BON KALINDO KU MALAWI SIKULI BWINO 🙌

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 12 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 34

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 19 วันที่ผ่านมา +3

    Lero ndatsimikizadi kuti Bon Kalindo Mulungu amamungwilitsa ntchito ndikudziwa ambiri simuvomeleza mudziti amapangira zimenezi ndale koma aiii ndithu Mulungu anamusankha Bon Kalindo Ngati momwe anachitira ndi Mose kwa iguputo kuti akatulutse ana Israel ( GOD BLESS YOU MR KALINDO🙏)

  • @phonexDaniel
    @phonexDaniel 19 วันที่ผ่านมา +3

    Kod athu ndinu otani Muthu akunena zabwino bwino.inu mukut chitsilu.zangozizo zimukumva.

    • @GiftJulius-gx2kb
      @GiftJulius-gx2kb 19 วันที่ผ่านมา

      Anthu enatu anangobadwa opusa amangoikila kumbuyo zilizonse.akuti sakuona vuto

    • @anicakandiado
      @anicakandiado 18 วันที่ผ่านมา

      Eti inu

  • @MercyChimaliro-fi6mv
    @MercyChimaliro-fi6mv 19 วันที่ผ่านมา +1

    Kuyambira lero boni Kalindo ndizikuyitana Mose wa Lero. Soka limugwera munthu odana ndi iweyo

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 19 วันที่ผ่านมา +1

    Simunaonepo mfiti? Wina aliyense amene akujijirika ndi MCP ndi mfiti. Achakwera anangobaya chidole chija ndi jakison ku Malawi kunachitika ngozi.

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 19 วันที่ผ่านมา +1

    dziko lamalawi eeeee panopa lafika poopsa kwambili

  • @PaulineKamwana
    @PaulineKamwana 19 วันที่ผ่านมา

    Ndipo inenso ngoxi zimenezi nduudabwa nazo ..Ambuye Mulungu alowererepo

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb 19 วันที่ผ่านมา

    Nanu a fire akumalawi amawelengela za anthu

  • @SilenceChepiano
    @SilenceChepiano 19 วันที่ผ่านมา +1

    Mmmm pakana 3days osapeleka what's going on

  • @michaelbulaula6444
    @michaelbulaula6444 19 วันที่ผ่านมา

    Ya 🔥 yinabwera

  • @Paworo-h5r
    @Paworo-h5r 19 วันที่ผ่านมา

    Satana woyamba ndi kalindo enawoakungomalidzitsa, munthu akuti akumenyela ma ufulu anthu wosawuka, anthu ake ati anapitako kukapempha kwa anthu andale ngati iyeyu? Ndili linen anayamba wakapelekako sopo Kwawosawuka akunenawo kalindo, bigiiiiii and smart develop usadyele pamutu pa amphawi moto waselufule ukukudikila

  • @FrancisStima-sc7zs
    @FrancisStima-sc7zs 19 วันที่ผ่านมา

    Chakwela amakatani kwa papa Francisco

  • @ChrisyMbewe
    @ChrisyMbewe 19 วันที่ผ่านมา +1

    Zoona.tipephele.amalawi

  • @LoyidKarebe
    @LoyidKarebe 19 วันที่ผ่านมา

    Ng'alulazation

  • @user-bl2kh5hd4m
    @user-bl2kh5hd4m 19 วันที่ผ่านมา

    Ameen

  • @Paworo-h5r
    @Paworo-h5r 19 วันที่ผ่านมา

    Big devil

  • @beatricenkhoma1109
    @beatricenkhoma1109 19 วันที่ผ่านมา

    Devil at work, let's pray for our country, iyi ndi mphulupulu ya dziko imene imabwera cifukwa utsogoleri woyipa wa atsogoleri adzikolo Mulungu amakhala kt wacenjeza, waunikira atsogoleri kumangovitabe zoipa as result, amalola oipayo alamulire nkwiyo wa Mulungu then mukupwetekesa anthu osalakwa

  • @Iwiszy-ht9ic
    @Iwiszy-ht9ic 19 วันที่ผ่านมา

    Today is 24 don't forget

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 19 วันที่ผ่านมา

    Chakwera ndi wa satanic aliyense amadziwa munthu woyipa

  • @RajhMatola
    @RajhMatola 19 วันที่ผ่านมา

    Ili ndiy bodza malamulo afiti sanabwele ler or chakwela anawapeza kamban zina awinik

    • @chilembwekanjirawaya4296
      @chilembwekanjirawaya4296 19 วันที่ผ่านมา +2

      Yamba kupemphela aisey nthawi yatha uchedwa nazo

    • @MercyChimaliro-fi6mv
      @MercyChimaliro-fi6mv 19 วันที่ผ่านมา

      Ndiwe mfiti iweyo komaso satanic.

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r 19 วันที่ผ่านมา

      Mudzazindikila but very soon. Choopsa chikudza

  • @ChrisyMbewe
    @ChrisyMbewe 19 วันที่ผ่านมา

    iiiiiiiiii.ndipo.zoophwa.kumalawi athungati.agalu.kufa.iiiii.ambuye.atithandizendithu

    • @kingsleymsampha2260
      @kingsleymsampha2260 19 วันที่ผ่านมา +1

      He says andale adayika malamulo woyipa not Chakwera. Listen again

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 19 วันที่ผ่านมา

    Choka iweee mbuli ya munthu

    • @FrancisStima-sc7zs
      @FrancisStima-sc7zs 19 วันที่ผ่านมา +1

      Wasala ndiwe usamale

    • @anicakandiado
      @anicakandiado 18 วันที่ผ่านมา

      Mbuli ndi iweyo amene sukumva kuwawa kwa imfa zikuchitikazi mpaka wina wakwanu atafa

  • @MaxwellSamuelChikapa
    @MaxwellSamuelChikapa 19 วันที่ผ่านมา

    Chitsiru

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 19 วันที่ผ่านมา +1

      Kagwere uko pedegu iwe 😢

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 19 วันที่ผ่านมา

    Chakwera ndi wa satanic aliyense amadziwa munthu woyipa