ไม่สามารถเล่นวิดีโอนี้
ขออภัยในความไม่สะดวก

PROGRAM YA TIVENSE YOMWE AMALAWI AKUSUSANABE YA KU MBC MWAZINA AKULAKHULAMO PROGRAM YO

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 18 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 64

  • @LionNzunga
    @LionNzunga 2 หลายเดือนก่อน +2

    MBC mwayiwala Kuti Radio station to ndimisokho yathu nosenu bwelela chakwela ndi wakupha and he must step down now

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892 2 หลายเดือนก่อน +2

    Mmmxxx dziko lino lilindi makhuluku ambiri

  • @wonganimwase9881
    @wonganimwase9881 2 หลายเดือนก่อน

    To be honest, the main thing is that "wolira samutseka pakamwa". In most accidental deaths there is a tendency to be blame games. When in shock, emotions are high.
    If the search was made in time things might have been different. A radius of 10km can't take over 10hours. Why did it take over 4hours to announce the missing plane to the nation?
    Let's put ourselves in the position of the bereaved and not concentrate on damage control.
    Have you not seen a person being attacked when breaking back news? It's all part of disbelief, shock, grief and confusion. Let's put politics aside and look at facts.

  • @karimshaik4485
    @karimshaik4485 2 หลายเดือนก่อน +1

    We watching you kasakula

  • @user-ul5hh3cz8z
    @user-ul5hh3cz8z 2 หลายเดือนก่อน

    We are after you mbc u tolk noses mwakuta mutonjani afiti inu simukufuna zabwino Kwa Malawi

  • @PatrickChiromo-qq7xy
    @PatrickChiromo-qq7xy 2 หลายเดือนก่อน

    Mukupusitsa ndani a Kasakula? Mulibenso umboni wa zomwe mukukamba,,,akudziwa chilingamo ndi Mulungu ndi Angelo kumwamba basi musanyoze ena chifukwa cha ndalama,,,what a shame.

  • @arafatMtyala-bo8ev
    @arafatMtyala-bo8ev 2 หลายเดือนก่อน

    Azibambo inu musazitukwanise ayi mwakula ndithu ndipo mbc mukuyakhulilayo ndi yaife tonse amalawi, mbwelera zanuzo muzikakamba kuchipani kwanuko osati radio yathuyo ayi, mabatile any nosenu

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 2 หลายเดือนก่อน +1

    Wosekeni matongo.yinu Chakwela you mast go

  • @Alliechamolie
    @Alliechamolie หลายเดือนก่อน

    Dzisilu dzikukukanikanikaso kuyakhula dzikutiwawatu agalu inu

  • @elijahmsesa8048
    @elijahmsesa8048 2 หลายเดือนก่อน

    George kasakula pachipwi pako kanyimbi fetseki

  • @user-vl8uw8mc3u
    @user-vl8uw8mc3u 2 หลายเดือนก่อน

    Amalawi onse anaziwa kale kuti mwamupha ndinu chilima.basi inuyo mwatha ufumu wanu watha😂😂😂😂

  • @renardmapemba9859
    @renardmapemba9859 2 หลายเดือนก่อน

    😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊

  • @DafterChitema
    @DafterChitema 2 หลายเดือนก่อน

    Nzeru mulibe ndipo mukuona ngati Malawi ,,sinaone zimene mwapangazi,,,,,nthawi ino SI ya make dzana ayi yoti ndikumanamiza anthu koma chilungamo.chili chete ai ,,zopusa basi,,,,muziuza ana Anu zimenezo,,ndi azibare Anu,,

  • @MikeMerecah
    @MikeMerecah หลายเดือนก่อน

    Ingopephani akuthandizan mukurakhurazo sizikuveka zikuchita kuveka kuti sizooona ,anaanu aenera kuti sakuverani fundoless phiri, Malawi wake siamenei uyu mwazi mukhetsa kuti ziende,

  • @user-bl6km6kx7n
    @user-bl6km6kx7n 2 หลายเดือนก่อน

    mwataya line adzibambo bwanji kod mukuyima mbali bwanji mukuziwa kathu musamaime mbali azibambo zamulungudzi ndiye ziti mungauze amalawi

  • @user-fd2su4ig1f
    @user-fd2su4ig1f 2 หลายเดือนก่อน

    JB chifukwa amangokutukwanani agalu inu

  • @MorganBanda-oc2jx
    @MorganBanda-oc2jx 2 หลายเดือนก่อน

    koma mungamagone pa live ngat apa??? kod anthu ngat awawa mukuwasungiranji ma office wo?? akulatu awo....

  • @michealchaomba9761
    @michealchaomba9761 2 หลายเดือนก่อน

    Mcp ntchito yake ndikupha kuba ndi kuononga
    Matenje ndi gulu lake mwaisilizira chilima ndiye muti chani apa

  • @ChristopherKawilam
    @ChristopherKawilam 2 หลายเดือนก่อน +1

    Kasakula pathako pako in sure

  • @karimshaik4485
    @karimshaik4485 2 หลายเดือนก่อน

    Ague man

  • @bisweckchimphamba8497
    @bisweckchimphamba8497 2 หลายเดือนก่อน

    Izi ndiye sindionera mkuonera komwe bolani ndizimvera Limpopo FM yomweyi

  • @Moffat-oi4yx
    @Moffat-oi4yx 2 หลายเดือนก่อน

    Akasakula ndi anzanuwo mitu yanu sikugwila ndinu mumamukomedwetsa mtsogoleli ngati zinthu zikuyenda inu simukuona nokha kuti anthu akukukanani mbudzi zawanthuinu

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr 2 หลายเดือนก่อน

    Koma mipando yopatsidwa chifukwa chothokozedwayi, KASAKULA wafika poyankhula NADZALAMPHUNO ngati amenewa lero? Ayi zikomo Mulungu akuona

  • @ChimwemweHenry-uw1bq
    @ChimwemweHenry-uw1bq 2 หลายเดือนก่อน

    Ngatbmwapasidwa ndalama zingodyani koma thawi yake izakwana yoti mubweze

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl 2 หลายเดือนก่อน

    Chifukwa mumadya naye chakwera koma nose muli opusa kwabasi chende Anu kuyakhura zopusa basi

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 2 หลายเดือนก่อน

    Nkhumba zimenezi mmene zakuliramu zilibe nzeru..
    No wonder waikakonso abale ake ku MBC...Ubulutu paliponse...idiots😮😮😮

  • @Alliechamolie
    @Alliechamolie หลายเดือนก่อน

    Kansakula kholo yamako

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 2 หลายเดือนก่อน

    Iwe muvula kasakula blessing nose muchokako uko ku mbc next year stupid Amalawi ife tose taziwakale zimene zinachitika chilima mwamupha ndinu ndi chakwela wanuyo

  • @YouzyJames
    @YouzyJames 2 หลายเดือนก่อน

    Munthu wina aliyense amagwila ntchto yaboma amakhala mbali yaboma .ndiye inu apa masatinamidze

  • @hassanpillow4251
    @hassanpillow4251 2 หลายเดือนก่อน

    Koma ichichi mukuti kasakulachi nchitsiru kwambiri one day udzachoka pamenepo

  • @patrickdamalekani9863
    @patrickdamalekani9863 2 หลายเดือนก่อน

    Koma ngat zolankhula ulibe ndibwno kukhala chete cz ndiwe munthu amene sukudziwa chomwe ukulankhula ukuganiza atakhala mwana wako chonchija ungalankhuleso Iziii?

  • @dyba-x9w
    @dyba-x9w 2 หลายเดือนก่อน +1

    Big empty heads

  • @Moffat-oi4yx
    @Moffat-oi4yx 2 หลายเดือนก่อน

    Mwakhuta nkhalamba inu measowa zoyankhula simungawauze amalawi zovhita. Anthu anakukanani kale olo mukomese bwanji munthu sangadinthe osintha ndi inu chifukwa mukulandila ndalama

  • @kondwanitruemanmatiki3248
    @kondwanitruemanmatiki3248 2 หลายเดือนก่อน

    kunali amzanu oziwa kuyankhula inu muti chani apa...

  • @RCFAKI-mx4dv
    @RCFAKI-mx4dv หลายเดือนก่อน

    Amvulanso mulibe nzeru kasakulayonso ndi wa mcp

  • @elijahmsesa8048
    @elijahmsesa8048 2 หลายเดือนก่อน

    inatipusisa ndi hot current yomwe ija palibe chomwe tingakuvele tiye uko kanyere

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 2 หลายเดือนก่อน

    Kasakula lero limenero ayi zikomo

  • @ChikumbutsoChiphaka
    @ChikumbutsoChiphaka 2 หลายเดือนก่อน

    Koma kodi anthu mukutsutsanu muli umboni, and ngati muli nao, kokanena kulibe? Usiyana kumatukwana,, I think umunthu wanu, suwonekera through phuzotu,

  • @abdulazeezchapita2159
    @abdulazeezchapita2159 2 หลายเดือนก่อน

    Akasakura amaoneka anzeru Ali ku Times atangochoka pano ndikanyimbi wachabechabe

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl 2 หลายเดือนก่อน

    Ndiye T V yimangorora chirichose inu simufunika apo ayi kupusakwanu

  • @CharityKangulero
    @CharityKangulero 2 หลายเดือนก่อน

    Kasakura mada faka

  • @Alliechamolie
    @Alliechamolie หลายเดือนก่อน

    Zinsilu nonse ndi bwanawanu wa abc

  • @karimshaik4485
    @karimshaik4485 2 หลายเดือนก่อน

    Nd you too will be accountable

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 2 หลายเดือนก่อน

    Akasakula ndimawona ngati muli ndi nzeru

  • @user-zo4yr9rx4u
    @user-zo4yr9rx4u 2 หลายเดือนก่อน

    Atilakwisa awa akasakula Mutu ngati Zungu lapachulu

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 2 หลายเดือนก่อน

    Mwakhuta mmalo mokalera dzidzukulu uko mmxxxx

  • @PatrickChiromo-qq7xy
    @PatrickChiromo-qq7xy 2 หลายเดือนก่อน

    Azizambo opanda nzeru inu

  • @KennyPhiri-zg1kr
    @KennyPhiri-zg1kr 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂

  • @karimshaik4485
    @karimshaik4485 2 หลายเดือนก่อน

    Kasakula you talking nosence

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 2 หลายเดือนก่อน

    Mmimba zonkhwepazo

  • @user-ql8nf2vb8s
    @user-ql8nf2vb8s 2 หลายเดือนก่อน

    Azinsilu awa

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 2 หลายเดือนก่อน

    Musatibowe

  • @ernestphiri5507
    @ernestphiri5507 2 หลายเดือนก่อน +2

    Just keep quiet if you have nothing to say

  • @elijahmsesa8048
    @elijahmsesa8048 2 หลายเดือนก่อน

    George kasakula pachipwi pako kanyimbi fetseki

  • @elijahmsesa8048
    @elijahmsesa8048 2 หลายเดือนก่อน

    George kasakula pachipwi pako kanyimbi fetseki