Our president Dr chakwera is fully matured in politics. He knows people's needs , wanthana ndi cyclone fredy, COVID-19, and other disaster. He construct many infrastructure like njanje . Akukonza zinthu zambili.
Hmm u mbuli musamaphatkize ndi zinthu zabwino bwino tamangolembani ma comment yosangalala osati kumataya nthawi ndi kunyoza ena zikupindulirani chani??
Ine ndilindi mfondo yimodzi a dpp anthu ambiri amakukondani koma ngati mukalowa m'boma 2025 phuzilani kukwanilitsa zofuna za anthu kuti asazatayeso chikhulupiliro malonjezo ndi zomwe zizakukhazikani mu boma mpaka kalekale
M,tsogoleli adzikhala ovetsa kukoma ine ku m,tima mbeeee❤❤ adad omweo kuti wawawa
Koma akanavomela kuti omwe tikukhala kunja kwa ziko la malawi kuti tivutelo tikufuna tifuna Peter apeze 90 plus please atiganizileko
Zoonad brother
Adad ❤ bomaaaaaaaaaaaaa! Ilooooooooppppppppp!
Makhosana TV your doing all the best serious we are really appreciated believe you me
Tears of joy in my eyes chipani chidzipatsa ntendele
Dpp boma I watching TV on cape town south Africa more 🔥🔥🔥
Ndungowona ngati tivota lelot
Watching live from Durban under u APM my vote
This is so wonderful ,APM a man of vision
Brian and your team ur the best media team...relevant questions plus easiness
Our president Dr chakwera is fully matured in politics. He knows people's needs , wanthana ndi cyclone fredy, COVID-19, and other disaster. He construct many infrastructure like njanje . Akukonza zinthu zambili.
Adad woyeeeee moto kuti buuuuuuuuu we love Dad may the almighty God bless you, protect you and give you long life❤❤❤ watching from Cape town
I wish all the best for convention DPP u show good behavior to another party's and good example that's good
Adad Adad Adad woyeeeee ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Watching from Capetown ADADI WOYEEEEEEEEEEEEEH!!!!!
Very nice convention of Dpp, beautiful beautiful
Kkkk komatuu Brianna mukhalikee with your teammm mumativesaa ku komaa heavyyy
Ndipo mtendere wakewo😂😂😂😂😂❤
Chaka Chino ndivoter for sure ,❤
My vote ❤
From Lilongwe..adad omwewo Moto Kuti buuu❤❤❤❤
MCP 🔥 our votes 2025 untill 2070
Chakwela munyaaa nazo adad moto kuti buuuuu❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Zako izo ife mcp mn
Iwe not ife 😂@@PreciousBandah-l2r
Ndale zophana zidatha kale adad wooyeeeeeeeeee❤❤❤❤❤❤❤❤❤
APM APM Bomaaaaaa ilooooo❤❤❤❤❤
More 💥💥💥Adadi inutu mulowa ndipo amalawi tiona kusintha.... 💥💥💥💥💥💥Buuuuuuuuuu!!!!!
Respect Arthur Peter muthalika we trust you 🙏 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
APM my vote not chikangawa,,munthu oipa kupititsa SKC kumanda coz of udindo ,, doesn't make sense
This is real Government what more malawians need
Koma makaka okhawa ndimapeleka ulemu anthuwa amatchena nawo palibenso nsalu yokongola ngati iyii kuzipani zonse number 2 Pali ya afford bas
The message should dwell on how better will serve Malawi than their last term....kuvomerezaso the wrongs not so bad!
Catherine, she's talkative lady, why she talk about beer?
Jona amandiwaza heavy😂😂😂nkochenjeratu.Maphang'ombe ndi andevu mwawasiya kuti??collab yachabe
Ine ndiye sindingayerekeze kukamba za chakwera chikangawa mfiti uja.adadi motooooo!!!!!!
Kkkkk Bryan at timakamba mkhan ya bungete😂😂
Adadi omwe ooh kuti wawawa 🇲🇼🇲🇼
I watching from binoni south Africa
Nankhumwa chisilu cha munthu ukumva bwanji kumene uliko mbuzi iwe
😂😂😂😂😂😂 ndipo ndiline khoza kuzipha
😂😂😂😂😂@@MemorySambani
@@BrightZiongaakupezekela kuti nakhumwa
Kkkkkkkkkkkkkkk Nankhumwa adapanga mistake yaikulu kwambiri😂😂😂
DPP woyeeee💙💙💙
Azimayi a dpp amanva kukoma osana watching from pritoria
Brian naye akati aipatse moto kkkkkkkkk umakwana BB
Adad omwewo asakufuna akakolope nyanja hehehe chakwera chikangawa mpaka kusegura mimba mwa kamwazi monga mwa chipani chako cha magazi uziona taona azako okondedwa chakwera wanyerebwa uku
Hmm u mbuli musamaphatkize ndi zinthu zabwino bwino tamangolembani ma comment yosangalala osati kumataya nthawi ndi kunyoza ena zikupindulirani chani??
@@AishaChibwana-b8o usova
APM our vote
The government in waiting
Adad number one ❤❤❤❤❤
Adad woyeee♥️♥️♥️
Ndikumva kukoma kkkk
More 🔥
From durban adadie my vote
Chakwera wanyanya wakuba anabwera alibe nothing lero is a millionaire nyani chikangawa
Pangani alliance inu ndi zipanizo zabwela
Akanati anthu azivota monga kuno kuno ku jonz,I would have vote for APM DPP
Ine ndilindi mfondo yimodzi a dpp anthu ambiri amakukondani koma ngati mukalowa m'boma 2025 phuzilani kukwanilitsa zofuna za anthu kuti asazatayeso chikhulupiliro malonjezo ndi zomwe zizakukhazikani mu boma mpaka kalekale
I like ur comment.Mau amphamvu💪💪💪💪
@@FosterChakanga thanks brother 🙏
Apa ndiye DPP 2025 yadutsa na ndichikangawa scandal mcp down.... Kagwere
Wsh u all the best pm
chipani koma ichi❤❤❤❤
❤❤❤❤❤ lovely.......
Ine ndikuva kukoma 🤸🤸❤❤
Watching from UK
Dpp❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Agwirizane basi aliombole dzikoli we need peace not chokangawa😂😂😂😂
Go go my party
Chete kwa dad ife❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
All de best
Wa mcp apse mtima bas
Koma kwachema😂😂😂 dzipani Zina mwati koma chingawa komwe uriko ayi zikomo zimu achima ukukathe galu iwe
Times always good
Brian musamalese anthu kufotokozera zinthu mukukonda kuwaimisa kuti ai tikambe za DPP koma kwina kuja amalankhula moyerekezera zipani zina mumawasiya kuti alankhule zakukhosi.
Chakwera munthu woyipa iwe uziona mbuzi ya munthu . My vote is for Apm .....chakwera azimangilala kumene uliko .....panyapako chakwera
Khope Za athu zikuoneka Za chimwemwe aliyense chipan cha mtendere.
Boomma illooo❤❤
DPP 💙💙💙
Cathy ntchito amatha
Tv yanuyi sikulongosokaso iyaaaa!!!!
Dpp ❤❤❤❤❤
Koma ndye mtimamu ngat talowa kale adad usongoleli wabwino mwangoona zinthu mmene munazsiya muja lelo tili mavuto ife ana anu tinthandizen adad
Times best TV
Nafenso omwe tili kunja kuno atipatse mamvote next year
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Koma kwachema🎉🎉🎉❤❤❤❤❤
Kkkkkkk ATI ndimangofuna kusindika kkkkkkk tinamvatu kkkkkkkkk😂,
Adaad a tivutatu ukuuuu
A Malawi tikondwa ngati atamakambila zipani zimenezi kuti agwetseletu MCP, yatikwana kwambiri.
Koma ndye ndi kuzimva ngati dpp ya lowa kale m'bomatu
Adad woyeeee
Mi vote for DPP is unshakable
My vote dpp
A deputy mayor mumakwana dpp woyeeeee?
Koma Brian 😂😂
Azimai a DPP amadziwa kuvina 🔥🔥🔥🔥osati ma gogo aja a mcp
Zantchito Brian and Ca
Times much thanks .Dpp chipan chomvetsa kukoma anthu
If you not careful iwe pitala uthazakozonse zomwe unaba mulamuliro wako. Ukanasunga uzidya ndizidzukuluzako, m' phechepeche mwa njovu salowakawili.
Chikangawa bp yafika pa 99
❤❤❤❤❤❤BOMA 2025😅😅😅
Ine kuno ku Newcastle kuva kukoma ndiliphe❤
DPP apa yandilimbitsa mtima heavy
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Dpp woyeeeeee waboma uyu ulendo
Mcp chipani cha nyela sanayitane azawo chifukwa chanyela ndikuzikonda
Chikangawa party mmimba mwatentha😂😂😂😂😂