Excellent discussion. Ine ndine muKristu koma ndaphunzilako zambiri chifukwa chakukambilana uku. A Goba is a very good interviewer and the Sheik knows his stuff. Thanks a lot
waoo so nice.from all this interview I have seen that God is one though some quoters say not,whether you pray 5 times a day,face which direction during prayers,or don't work on Sunday but still God knows better about what he said that could you wait until the Sabbath is over to rescue your donkey out of the pit.ndiye sizoti bwanji asilam simulipatula lonse tsikulo,coz even the seventh day Adventist they are having so many alternatives about working in sabbath
MashaAllah powerful bayani❤❤❤😊
Ooooooh hallelujah Amen mtumiki mwayakha mothandidzidwa ndidzimu wa Mulungu Ooooooh yes
Excellent discussion. Ine ndine muKristu koma ndaphunzilako zambiri chifukwa chakukambilana uku. A Goba is a very good interviewer and the Sheik knows his stuff. Thanks a lot
+Isaac Thomas Thank you for your comment
Wallah nkhani iyi ilibwino kwambili ndipo sheikh awa akufunika kukumana nawo mwa pafupi pafupi muli ubwino mwa iwo mulungu awalipire zabwino
Ameen
That's a powerful message, it's a message that can bring peace n unity btwn Islamic n Christianity religions thanks so much God bless u !!!!!!!!
Masha Allah ndikanakhala okondwa koposa nditakumana naye sheheyu
Ma shaa Allah.... Beautiful message
waoo so nice.from all this interview I have seen that God is one though some quoters say not,whether you pray 5 times a day,face which direction during prayers,or don't work on Sunday but still God knows better about what he said that could you wait until the Sabbath is over to rescue your donkey out of the pit.ndiye sizoti bwanji asilam simulipatula lonse tsikulo,coz even the seventh day Adventist they are having so many alternatives about working in sabbath
Mashaallah......❤❤❤❤
Am enjoying the message
❤❤❤❤
maa sha Allah sheikh asakusokoneze ameneyo
agness ndiganiza ndiwe opusa nkhaniyi ndiyabwinobwino ukusokonekera ndiweyo and ukuoneka ochenjera opusa ife taphunzirapo
Mashallah
mashallah
Maa nsha Allah
This shehe number one
Mashallah sheikh
برك الله فيك
AMEN
Namu sheeh
SHEKHE ALLAH AZIKULIPILANI ZABWINO
E-mail
Good massage
Namu
My
Naam shelk
sheikhe mukulankhula zomveka
Chilindi magomelo
Mufziweni yesu asilamu inuu ndipo mukuyenera kumulandira
Ukuthanthaudza chani.ukati A silam amudxiwe yesu.mesa udziti A Christu mumudziwe yesu..
Aslam amadziwa Yesu kuposa akhristu
Koma mukuvetsa koma kkkk.. akuti yesu sizathu ujayu ndi oremekedzeka
Nthawi mudayika yochepa next time,mudzaike nthawi yokwanira,