9:36 Useless cabinet how can he reconfigure the cabinet and yet they are the same people since 2020? Failed people they are the same in a cabinet so they want to change what? They want to recover what in 8 months a head of Tripartite General Elections and yet they have failed Malawians the last past 4 years nothing tangible we have seen on the ground?
Much respect to you guys 🙏
Atenga kuti adzatsutse nawo, nthawii yokonza dziko yatha anali kuti 5 years yonseyi?
Ulemu wanu gayz ,
First 11 imeneyi agwanayo kuyambira kochiyo anthu sitikumufuna chikangawa no chances
Atsukuluzi ndiy akunena zoona chitsulo kuno kumwanza sangamuvotele chifukwa amusankha u dept alemba mmadzi
Muuzeni DCccccc kalindo born abwere watisowa ife
Vote yanga iweluza pazimenezi nd2
Chikangawa achikewawoono nga malawi
Akufunika mapemphero apa Dela dela
Mulungu agobwerapo apa basi chabwino palibepo .
Chakwera wazibwana Malawi Ali mmavuto
9:36 Useless cabinet how can he reconfigure the cabinet and yet they are the same people since 2020? Failed people they are the same in a cabinet so they want to change what? They want to recover what in 8 months a head of Tripartite General Elections and yet they have failed Malawians the last past 4 years nothing tangible we have seen on the ground?
this government is eresponsible and the leaders we have can't bring any change because they don't care
Kabinetiyo akanangosiya palibe chabwino
palibe chomwe asitha kuma kuonjedzela uphawa
Chimwendo,Kamajekete ,Chithyola,Sam Kawale atsaliranji osachotsa bwanji
Galu wa munthu uyu
😂