KOMA MWATI IZIZI ZIKUCHITIKADI? PROGRAM YA ZILI PATI YAULURA IZI NDIPO UYU ZINAMUCHITIKIRA NDI MBONI

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 36

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 16 วันที่ผ่านมา +5

    Mfiti iza fanso kumango khala kuzi vuta kumaloza kapena kupha mzako palibe chosatha pa Dziko Lapansi,kunali koyenera tonse kumalemekeza Yehova, Koma masiku akusa ziwa Mulungu adalekerera mphavu Za satana pa Dziko Lapansi.

  • @PercyRoos
    @PercyRoos 16 วันที่ผ่านมา +3

    Mmmmm 🙌 🙌 🙌 🙌 🙌 🙌 🙌

  • @JumaDevelopmentnetwork
    @JumaDevelopmentnetwork 16 วันที่ผ่านมา +4

    Bola nzimayi ankapanga program iyi uja ankabebetsa.

    • @osbornleman2500
      @osbornleman2500 14 วันที่ผ่านมา

      ndipo achembonera sakuitha program iyi eishhh ikuwavuta ndthu ndikachibwibwi kake kaja kkkkkkkkkkkk

    • @louisbonongwe8537
      @louisbonongwe8537 10 วันที่ผ่านมา

      Chemkope ndobalalika🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣machine anali adha anapita ku times aja

    • @EmmanuelNtago
      @EmmanuelNtago 10 วันที่ผ่านมา

      Komatu program anayamba ndi chemkopei mai uja asayambe konse

    • @EmmanuelNtago
      @EmmanuelNtago 10 วันที่ผ่านมา

      Komatu program anayamba ndi chemkopei mai uja asayambe konse

    • @EmmanuelNtago
      @EmmanuelNtago 10 วันที่ผ่านมา

      ​@@louisbonongwe8537Koma adayamba program ndi iyeyutu adah aja asanayambe ali ku times aja,,atachoka ameneuja ndipameneno kunabwera mai uja

  • @elizabethziba1652
    @elizabethziba1652 15 วันที่ผ่านมา +1

    Nkhani zopanda mutu zosowa poyambira😂

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 16 วันที่ผ่านมา +4

    Aaaaa...basi chinthawi chonsechi yathera pamenepa???.. za ziii

  • @abwinoamatani4921
    @abwinoamatani4921 16 วันที่ผ่านมา +1

    Alomwe akati awonjezere nkhani. Koma palibe chikumveka

  • @CharlesSanudi-f9t
    @CharlesSanudi-f9t 10 วันที่ผ่านมา

    Zakuvuta kulongosola aaah

  • @Stranger_265
    @Stranger_265 7 วันที่ผ่านมา

    Part 2 ilikuti nanga

  • @IsaaAkila
    @IsaaAkila 11 วันที่ผ่านมา

    Ndechan ichi

  • @JailosiKaphuka
    @JailosiKaphuka 15 วันที่ผ่านมา

    Next time dzaesetseni kujambulila malo aboh

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 16 วันที่ผ่านมา +2

    Aaaa chenkope sudziwa kufusa

  • @BenedictChikaoneka
    @BenedictChikaoneka 5 วันที่ผ่านมา

    Palibe chazeru apa.

  • @LuciaJames-k4p
    @LuciaJames-k4p 16 วันที่ผ่านมา

    Mmmm

  • @EllinaTausi
    @EllinaTausi 12 วันที่ผ่านมา

    Jesus

  • @abwinoamatani4921
    @abwinoamatani4921 16 วันที่ผ่านมา

    Mwatisiya m'malere

  • @JoanaMalekwa
    @JoanaMalekwa 15 วันที่ผ่านมา

    Komatu nde siinamveke bwino yopandanso poyambira

  • @RoseMathews-x8b
    @RoseMathews-x8b 15 วันที่ผ่านมา

    Program sili bwino next time zapangen zadongosolo

  • @bandakelvin4601
    @bandakelvin4601 16 วันที่ผ่านมา

    Koma mwanao akusokoneza aaa

  • @VioletMbale-o4y
    @VioletMbale-o4y 15 วันที่ผ่านมา

    Ndipo kale zimabeba pano I don't understand

  • @bandakelvin4601
    @bandakelvin4601 16 วันที่ผ่านมา +1

    Palibe ndatolapo kanthu

    • @MikisaSure
      @MikisaSure 11 วันที่ผ่านมา

      Ine ndikugovamo anfumu

  • @AdelinaNong-ow4dg
    @AdelinaNong-ow4dg 16 วันที่ผ่านมา +1

    Mmmm everyone is right according to themselves, koma kwaineyo it doesn't make sense

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 16 วันที่ผ่านมา +2

    Nkhani iyi siikuveka bwino zikuphatikizana mutu weniweni siikuziwika

  • @EusébioLucianoGaiondo
    @EusébioLucianoGaiondo 16 วันที่ผ่านมา

    Hii

  • @EnockMvula
    @EnockMvula 16 วันที่ผ่านมา

    ufiti uriko muzinamiza anthu kuti ufiti kuribe koma aboma inu ufiti uriko ineyo umboni pankhani naiyiyi yafiti tagwirapo ambiri naine

  • @MereenahCustom-yq4mv
    @MereenahCustom-yq4mv 11 วันที่ผ่านมา

    Sizikumveka bwino

  • @NaduMbewe-zz6iw
    @NaduMbewe-zz6iw 16 วันที่ผ่านมา

    Koma

  • @acklenmalawimovies9496
    @acklenmalawimovies9496 15 วันที่ผ่านมา

    Not making sense