ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
ine ndli pano kuvera inu a ntanyiwa yakhurani chilungamo chocho poti akuti boma ndi lomweli komatu akunama Achikangawa amenewa kodi akufuna chani? maka maka kom tu mulungu wathu salora ayi, ndiye kuti dziko lathu silo sawuka eti , nakha ndalama chochuluk chocho akuzetenga kuti, komabe akunama. ife tidalira Mulungu wathu bas❤❤❤
vuto ndilokuti yomwe mwaiyambai achikangawa simuimaliza muona nyekhwe ng”alura iwe ntanyiwa
Big up comrade
APM MY VOTE
awa dzeru alibe a mcp anthu sanapite ku school anatenga udindo mutu mulibe kanthu
,zikomo mtanyiwa titetezeni mung'anjomu ya moto
Akhalilayomweyo makape
Chikangawa yakwiya ndi mizimu
Yakwiya ndi mizimu yonse anaipha ija Anya adziwona
Komatu anthu amenewa ali ndi mvuto kwambiri
Vuto loika mbuli pampando MCP muli zidzete dzomwa madzi ometela ndevu
Kwaipa
Zachisoni amtanyiwa maboza anuwo mulungu azakulangani
Musamachure mulungu Malo osayenera kumuchula mulungu nanuso akukanthen Malawi akuvutika ngakhare mulungu ndi akuziwa atimenyera nkhondo ife tili chete
@@HappyAbyssinianCat-xt2bmndipo chikangawa apezeka bwanji kuno
Iweyo nanga osakamba chilungamo chakocho bwanj
MCP Ikuchoka iyambe ku pakila
Ndipo live😂
𝐀𝐳𝐢𝐤𝐡𝐚𝐥𝐢𝐫𝐚 𝐳𝐢𝐰𝐞𝐦𝐛𝐮 𝐜𝐡𝐨𝐧𝐜𝐡𝐨
Tilipo chete kunvetsela kwinaku tikudya nyika
Koma ndiye bodza mufukanazo kut poti mukupaga bunnssn
Zikomo❤
MCP ikhaula kkkkkkkk
Koma ukapsanalo.bodzalimenero aaaaa koma wadziwikatu takutulukila
Muthu wabodza osamataya thawi ndi kuvela ma odio ake ndithu napepe
🤣🤣🤣😂😂simunati
Mudakazionabe simunati
Maboza mtanyiwa, no vinjelu
Tiyen munthu wamkulu
Mabodza basi😂😂😂
Ndizitsilu zimenezi mesa amati akufuna kupha apm nde waphedwa pamtumbo pake ameneyu