ไม่สามารถเล่นวิดีโอนี้
ขออภัยในความไม่สะดวก

ZAMANYAZI COMMUNITY POLICE KUBA CHIMANGA MOGWIRIZANA NDI T/A BVUMBWE AGWIDWA..KANGAUDE PA MIBAWA TV.

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ม.ค. 2024

ความคิดเห็น • 43

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 6 หลายเดือนก่อน +6

    A khansala awawa amatha kuyankhula ndipo udindowu wawayenera zedi ndipo DPP ndimbambende siitsunga kape❤❤❤❤❤

  • @dannymangawa7511
    @dannymangawa7511 6 หลายเดือนก่อน +3

    Mr. Pombeya the legend, odala ndi anthu amene ali mmudzi mwake mkuluyu

  • @rashidsaid2232
    @rashidsaid2232 6 หลายเดือนก่อน +1

    I l❤ this man for standing for the truth keep it apolice akuba Kennedy Nkombeya God protects u ameen 🙏

  • @CholapitsaSamson
    @CholapitsaSamson 6 หลายเดือนก่อน +1

    Keep up the great work no fear

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 6 หลายเดือนก่อน +3

    T/A BVUMBWE ndi ngoni si mulomwe

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w 6 หลายเดือนก่อน +3

    Pombeya ntchito yabwino osayang'ana nkhope mwaimilira anthu ambiri ndithu

  • @HenryGulani-fq5js
    @HenryGulani-fq5js 2 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂👏👏👏👏 ulibho kwambili

  • @HenryGulani-fq5js
    @HenryGulani-fq5js 2 หลายเดือนก่อน

    Awachita bho Akudzolomwela Amuchotse tsatanayo

  • @user-fm5io8xj2b
    @user-fm5io8xj2b 6 หลายเดือนก่อน +1

    Tikudikira tiku timve kumapeto kwa nkhaniyi

  • @user-cw7bb7lc5o
    @user-cw7bb7lc5o 6 หลายเดือนก่อน

    Komtu mwadula mau mr mphombeya nthawi inaacheoela kk

  • @ConfusedAtv-bs4gc
    @ConfusedAtv-bs4gc 6 หลายเดือนก่อน

    Machendeako akuwauza Kuti chimangacho ndichaulele Mesa ifetu timalambula misewu ena ena amakafesa mbeu yamitengo kunanzale ena amakadzala mitengo mphepetele mwamisinje ndiye ukakhuta nkumaphwisa mpweya wako wonunkhawo kumene uliko nkumati chakwela akutipasa chimanga sichaulele kwathukuno

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 6 หลายเดือนก่อน +1

    Mukuba ndi mafumu etiii.,omvetsa chisoni😢 TA kumene adzimveka ndi mbiri zoipanzo..zomvetsa chisoni...

  • @blessmarleystech5712
    @blessmarleystech5712 6 หลายเดือนก่อน +1

    Congratulations

  • @user-rk3gq7gd8f
    @user-rk3gq7gd8f 6 หลายเดือนก่อน +1

    Amateyu musamangokhala kudalila za u TA zilimani osamangokhalila manja please pepho langa kwa TA phombeya asakhale dani wanu phombeya ndiwazeru kuposa asogoleli ambili ena onse kuphatikiza TA mateyu kupha athu ake omwe shem

  • @user-gd6zb2bv8f
    @user-gd6zb2bv8f 14 วันที่ผ่านมา

    Nawonso a chitetezowo andindidwe kkkkkkk

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 6 หลายเดือนก่อน +1

    Ndimadabwatu kuti MCP ingapereke zaulere agalu amenewa akutipha amalawi zedi

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 6 หลายเดือนก่อน +1

    Thyolo North eeeeee ndiyovuta kwambiri

  • @user-vs7ou8ni7v
    @user-vs7ou8ni7v 6 หลายเดือนก่อน

    Kwabvuta! koma I would love chilungamo chitayenda bwino

  • @user-ws4ue7tf6j
    @user-ws4ue7tf6j 6 หลายเดือนก่อน +1

    Apolic ndimango waona ose kuti ndi mbava iyaaa

  • @Owen88887
    @Owen88887 6 หลายเดือนก่อน

    Phombeya simunthuwambadi😂

  • @KuangKinghzao-ju5xy
    @KuangKinghzao-ju5xy 6 หลายเดือนก่อน +1

    Atule pasi udindo

  • @MtenjeHassan
    @MtenjeHassan 6 หลายเดือนก่อน +1

    Abel zulanga umakwana .koma watilakwira ife timadikira tione nkhumba yokanika kufa ija...

  • @blessmarleystech5712
    @blessmarleystech5712 6 หลายเดือนก่อน +1

    Acansara amatha kulankhura hevy

  • @anniewhite3497
    @anniewhite3497 6 หลายเดือนก่อน

    Pombeya Ambuye akudalitse chifukwa cha chichilungamo chako

  • @user-gd6zb2bv8f
    @user-gd6zb2bv8f 14 วันที่ผ่านมา

    🤣🤣🤣🤣 Zipwete kkkkk

  • @ConfusedAtv-bs4gc
    @ConfusedAtv-bs4gc 6 หลายเดือนก่อน

    Nkhani iyende Ngati madzi bornnnnnnn kalindoooooo mwela 29:38 sisunga makape Sibisa nkhani

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 6 หลายเดือนก่อน +1

    pombeya ambuye akuteteni

  • @user-gd6zb2bv8f
    @user-gd6zb2bv8f 14 วันที่ผ่านมา

    Phombeya akuyeneka atakhala msilikali guys

  • @tiacampbell1843
    @tiacampbell1843 6 หลายเดือนก่อน

    Ingowavekani omwewo ufumu basi ziyenda bwino😊

  • @user-uf1tz7bp5q
    @user-uf1tz7bp5q 6 หลายเดือนก่อน

    Mr phombeya mulungu akudaliseni

  • @user-frasernamaona14
    @user-frasernamaona14 6 หลายเดือนก่อน +2

    Awanso ndiza personal che Kennedy wa ndatha kuwona

    • @lacksonsiyadi943
      @lacksonsiyadi943 6 หลายเดือนก่อน

      Ndipo live

    • @HaroonSaidi-jv3ek
      @HaroonSaidi-jv3ek 6 หลายเดือนก่อน

      Chisiyeni chilungamo chiyende ngati imfa
      Khoswe wa John white alamulira bwanji makoswe black john

    • @chesterphiri7523
      @chesterphiri7523 6 หลายเดือนก่อน

      Kkkkk it’s personal for sure

  • @user-gd6zb2bv8f
    @user-gd6zb2bv8f 14 วันที่ผ่านมา

    Two feet kkkkkkkk Msilikari wankulu

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 6 หลายเดือนก่อน +2

    Kunyumba kwathu this is really bad picture eishiiiiii, Mathew Madala akotu moyo uwu analibe ndipo anali T/A wabwino zedi kunyumbaku kunkakoma limodzi ndi agulupu Anamaneya. Koma apapa mmmmmmmmm moyo uvuta zedi

  • @benitagrassman-windvogel5355
    @benitagrassman-windvogel5355 6 หลายเดือนก่อน

    Ufumu wathapo bac

  • @romsa4590
    @romsa4590 6 หลายเดือนก่อน +1

    😂❤

  • @Slyvia-uu3wc
    @Slyvia-uu3wc 6 หลายเดือนก่อน

    Onse amangidwe ndi A/T wo achisilu kwabasi

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r 6 หลายเดือนก่อน +1

    Adpp ndi zisilu boma likupeleka chimanga inuyo mkuba ndiye mkuyozaso mcp fokofo mkupha anthu anu womwe ndiye mzimtukwana chakwela .zisilu

  • @victorbanda9039
    @victorbanda9039 6 หลายเดือนก่อน +1

    Alomwe ndimbava

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r 6 หลายเดือนก่อน +1

    Akalindo mmangonyoza apa munenapo chiyani akalindo kwanutu uko