Wandikumbutsa zigoma waimba bho nyimbo anthu inu akut ndi ndalama koma kulakwila mlungu tonse ndife anthu amodzi god keep you safe big luso lanu ndilofunikila kwambili
Zimenezi mukuzitenga kuti? Bwanji kudana ndi zinthu zopanda pake? Linotu ndi dziko let them live their life happily. Mwinanso asatana mukhoza kukhalanso muli inu nomwe
mmm ndinali ndisanayinvele eee ayi nfana umatha wamuposa Dan lu nice song ❤❤❤ upitilize
Wandikumbutsa zigoma waimba bho nyimbo anthu inu akut ndi ndalama koma kulakwila mlungu tonse ndife anthu amodzi god keep you safe big luso lanu ndilofunikila kwambili
Nyimbo ya bwino kwambiri yatanthauzo, ndayibweleza mpaka 3 times yoooh ndalira kwambiri 😢😢😢
Nyimbo uabwino kuposa ya Dan lu✊✊👍👍
Ndipo zoti dpp imapha albino mmmmm i hope amangowaipisira mbiri..
Nanga uyu tiziti adaiwala???
Long live APM 💙💙💙
DPP 💙💙💙
Ndipo umatha zed ndakhala nawe chidwi saname❤❤
Lulululululululululululu big man nice song wow ❤❤❤❤❤
I love this song 💞
Very nice song keep it up brother
Dolo 🔥 kwambili 😊
A MCP amanga nyumba za albinos kuti akaluza azizawaphela momwemo azizati DPP MCP muvutika
❤❤❤❤❤❤ more 🔥🔥🔥🔥 kenani yatikanika yikuwawa
Chinyimbo akwapula ichi even masapota a mcp akumaikondaso heavy 😂
Azifuse. Kuti akuimbayo. Ndialubino kapena ndani
Eti eti
Anaimba ndi albino and I know him personally
I love this song❤❤❤❤❤❤❤
Dolo❤❤❤
Boma ndiromweri ❤❤❤
Amen mulungu ayankha
DPP woyeeee
Mbambande iwendiye umantha
Boma ililllllllllo boommmmme dpp my votes
Mbamva zigawenga zoipa mtima ngati manyi, chakwera chikangawa president wokumpha
Congratulations sir
Nice song❤❤❤❤❤
Dan Lu anathawa chi nyimbo chimenechi.Anadziwa kuti wachepa sangamake
Moto kutiybuuu
Nice nice tune
❤❤ u bro
Nice song.
Spirits 🎉🎉🎉🎉
❤
Ayi zikomo achimwene, nyimbo yabwino. Sitilira ndithu.
Nyimbo iyi ndimayifuna full mutu wake ndi chan komaso zina lake ndani wayimbayi
🎉 sharp ❤
❤❤❤ wayimba bwino,
Nyimbo ya bwino kwambiri umatha ayise
More fire 🔥 !!!
Good song vry meangful osati za A Dan olankhula nanga tiziti kumene Kuja ndi kuimba?
DPP woyeeeeeeeeee
Brilliant ❤❤❤
Ichi ndiye chitsiru cha albino uwona ngati pamenepo akuonera mokodwa agogowo Kalena mwina vampire sumamudziw eti ungodekha umuvotere kae uwone zomwe adzakupange udzatafunidwa ndi mafupa omwe iwe ngt sukudziw owooooh! 😂😂😂😂😂
Iwe mwana wahule eti ukulankhula ngat wadya manyibwnji uli bii ngat bibii plus panyapakonso
Chitsilu ndiweyo aise
We have got talented people in Malawi. Albinoism is nothing bro we are all humans. That is just a genetic complication. Do more music.
Ulemu wako km umatha kuyimba bro upitilize fundo zako zabwino zokhazokhazo🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏
Uyu ndiye wamenya kuposanso Dan lu muli mfundo zothyakuka DPP muziyenda ndi ameneyu basi
Mcp mapwala anu mesa mumati nthawi ya dpp malobino amaphedwa uyu ndindani
Nyimbo yi lri bhobho
Kod nyimboyi ndi ya ndan?ndimaona ngt ndi pat c
Nyc
Nyimbo yabwno kwambiri.
Title chan nyimboy
Umatha ulemu wako broooo
Nice One
❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉
Abale anthuwo mkanawapatsa ma uniform pls akuyimba bwino kwambiri
Nice❤❤❤❤❤❤❤❤
Kuyimba kwabwino uku achimwene inuyo mumatha kuyimba
Nice song
Mbambande
What's his name thiss guy😊
Kodi iwe wayimba nyimbo sukuwadziwa omwewawayimbira nyimboyi ukapanda kusamala akupha akuoneka ngati akukonda osayiwala kuti amadana ndi inu abale athu aChalubino mukudziwa zimenezi?
Zimenezi mukuzitenga kuti? Bwanji kudana ndi zinthu zopanda pake? Linotu ndi dziko let them live their life happily. Mwinanso asatana mukhoza kukhalanso muli inu nomwe
Tinasokera
Osati za Dan lu
Dikila iwey dzayambila kupha iwe😂😂😂😂
Sitinafike tikubwerera basi abro inu mumakwana
Kamajekete chikangawa ndi chikatumba mukayankha
Koma iyiyi nane ndimaifunadi bwanji munthu anayimba bwino
❤❤❤❤❤❤
Uthenga wa mphabvu
apa nde tasokeradi bs ambuye tikumbukireni
Mphechepeche mwa njovu sapitamo kawiri awa ndi achitsiru
Grey daundi
👍
Komatu mwinad tasochera
Eshiiih sorry m'bare ndinaiwala kt paja ukakhal pa bwino poipa pamaitana kuzolowera takaponyani vote tidzakuoneran poti mwat mukukhar mothawathaw mudzakhala mwaufulu osadand bola enanu tisakakuiken opanda mafupa zot stage wakwerayo ndrama zake ndi mafupa a zako uja waiwala eti, okay chabwino tienazo😢😢😢😢😢
you've no proof my brother just keep your mouth zipped to avoid embarrassment.
😂😂😂😂😂
Nanu inu dan lu nisataniki muzingoona ni zina rake iro kuti dan lu zina rapasi pa nyanja iri
DPP chipani cha fuko
Getting away nonsense
Umakhala kut ase?
Nice song
Nyimbo ya bwino kwambiri yatanthauzo, ndayibweleza mpaka 3 times yoooh ndalira kwambiri 😢😢😢