Muli uthenga mu nyimbo iyi. Ndipo ndi zoonadi ena amatikonda chifukwa akupindula kuchokera kwa ife. Ndipo zikatibvuta samaonekanso. Dziko ili eesh ndadutsamo, amayamba kukunyoza ndi abwenzi nyengo zikatibvuta zinthu.
Sometimes life is hard that we don't have a place where to go. Our relatives ,our friends sees us as nothing. They have put a full stop that it shall not work ... But God is alive and He loves us without conditions.... Jesus is our friends He will never left us alone. He makes impossible to be possible. Ask God about ur situations things will change because prayer is a powerful weapon. Someone may translate better😊
He tries to do in all areas but nothing and he has insulted by the neighbors, only Jesus who will never leave you alone and He makes a way just call His Name because prayer is the key, which situation you are passing through and he has further say let's continue praying to God.he said don't waist time with our friends who mock us are not the one who created us last season change nothing else is permanent bad
Nyimbo iyi ikundikumbusa komwe ndachokela chifukwa ndinali ndabwenzi koma ndina kumana ndi bvuto ose anandithawa nzoona amakonda mnthu ngat zikukuyendela Nyimboi nthawi zina ndikamamvela ndimangolila😂😂😂😂😂
When you are in hard times that is when you're friends run away so it's only Jesus Christ because everything for God is possible
Thanks for the good song ,may Mulungu apitilidze kukuvumbulusirani uthenga winanso wabwino Kuti mupitilidzenso kugawana nafe
❤❤ nyimbo imandikumbutsa komwe ndikuchokera chifukwa abwenzi ambili amabwera zikakhala kut zikukuyendera. Much love ❤️
Nyimbo iyi ndi mbambande. Ikumangilira ambiri.... ndithu man of God
Ambuye alemekezeke kwambiri
God bless you guys you nailed it very well❤❤❤❤❤
My late dad's favourite song RIP😢 I wish I a have the chance to ask him why he loved it so much.
😢😢😢 sorry 😢😢😢😢
Nyimbo imandikhumbuza my brothers , may you soul rest in peace my brothers. Nyimbo yabwino❤
May you rest in peace too...Evance and me are still alive
Good work nyengo zingasithe bwanji sinditaya mtima🔥🔥🔥🔥🔥
Gramei do desenho do vídeo.
Força meus queridos
Koma ndizowona ndipo tuziwonadi😢😢😢😢
Indeed it is only God who cares about you when you in trouble but friends will run away
What a song and with a powerful message mmmmh
Wonderful and powerful song for someone to be mindful of this life.
Nyimbo iyi imakhala ngati yatuluka dzulo.
Ndikakhala kwandekha ndimalira ndikamvera nyimboyi.
Ndipo siimakwanayi ataaaah mmmmmmm anapha anthuwa ndia sound zedi mmmm❤❤❤
Touching song, and encouraging to stick to God. God bless you.
😢😢christ is the only hope
Amen, be blessed
Mbambande bwana timafuna uthenga wamphamvu ngati uwu mulungu apitilize kukupatsa lutso komanso moyo wathanzi pano ndikunthawi zonse
Amen powerful song
My best song❤❤❤
Muli uthenga mu nyimbo iyi. Ndipo ndi zoonadi ena amatikonda chifukwa akupindula kuchokera kwa ife. Ndipo zikatibvuta samaonekanso. Dziko ili eesh ndadutsamo, amayamba kukunyoza ndi abwenzi nyengo zikatibvuta zinthu.
My favorite song ❤❤❤ichi ndi hit
Thanks 🙏
Nyengo zovuta pamoyo wamunthu
Nyimboyi imandilimbikits ❤
In love with the song even though I don't know wat the song say from🇿🇼🇿🇼🇿🇼🇿🇼🇿🇼🇿🇼🇿🇼🇿🇼
Sometimes life is hard that we don't have a place where to go. Our relatives ,our friends sees us as nothing. They have put a full stop that it shall not work ... But God is alive and He loves us without conditions.... Jesus is our friends He will never left us alone. He makes impossible to be possible. Ask God about ur situations things will change because prayer is a powerful weapon.
Someone may translate better😊
He tries to do in all areas but nothing and he has insulted by the neighbors, only Jesus who will never leave you alone and He makes a way just call His Name because prayer is the key, which situation you are passing through and he has further say let's continue praying to God.he said don't waist time with our friends who mock us are not the one who created us last season change nothing else is permanent bad
Inshort when the days are dark friends are few
Only God can understand what we are going through.
My lovely song it inspires me more
Amen man of God
Mumakwanitsa❤❤❤❤❤
This is my favourite song of all
Praise God
Indeed. And there is also m'busa wanga
Iyi ndi hit unbeatable
Amen
Well nown as Eva an Bon nice song
Nyengo ndizongodusadi
Very inspiring for sure
Nyimbo iyi imandililisa chifukwa nde ndizowona abale amakuthawa
my best song
Apapa boiz munkaimba,
kuimba moikira mtima AMEN
What a song
Nyimbo yanga
Thanks 🙏
I like this song it reminds me something
My song ❤
5:47
Nyimbo yoopsa zedi iyi Anthunu munapha
❤yamikani
Nice song ❤
So nice
Nyimbo iyiyi ineyo mmhm!
Eish nyimbo iyi alw2i repeat to listening
This remind me my brother in law RIP 👆😭😭
It is well...Amen
Nyengo zowawa misozi yokha yokha
❤❤❤❤❤mumatha
Nyimbo iyi ikundikumbusa komwe ndachokela chifukwa ndinali ndabwenzi koma ndina kumana ndi bvuto ose anandithawa nzoona amakonda mnthu ngat zikukuyendela Nyimboi nthawi zina ndikamamvela ndimangolila😂😂😂😂😂
God is good 👍
nyimbo yolimbitsa
uku nde kunali kuimba
Amen
Amen 🙏😭😭
Nyimbo imanditsitsimutsa iyi
Koma nyimbo iyi munachedwapo ndinthu nyengo iziii eeeee
Nyimbo iyi imanikumbutsa munyengo zomwe ndadutsa
Muli uthenga umu
Nice song
Amene
Mwatisisimusa
Nyimbo ya chilimbikitso
Amen 🙏
Amen 😢😢😢😢
Osamangot zandale apa tazimuka
Ine sindiyimva za ndaletu
Amen
Guys mwaiswatu ndaikonda zedi
Iyi nde munatchaya kugwetsa
Hahahahahaha
😂😂😂😂😂😂Anatchayadi zedi 😂😂💪🏿💪🏿💪🏿💪🏿💪🏿
❤❤❤❤❤
😊
This song mmmm gays
nthis is my favorite song Mr born kavalatsanza banda ndipo ndikayimvera misodzi ikutuluka amen
Ameen🙏🙏🙏
Amen🙏🙏🙏
Nice song
❤❤❤
Amen
Amen
❤❤
Amen