Mbambandetu malawi first osati CHIKANGAWA ndi mbava zinzake nohani iyi ndi yapakanthawi koma CHIKANGAWA palibe chomwe amachitapo koma kuba ndi kupha ndi kumanga anthu ulemu wanu malawi first Ambuye adzikutsogolerani
Anthu a kuZambia A wemba ndi anthu a nkhaza kwambiri zikomo.kwambiri malawi first mwalowererapo apa zikomo @ Malawi First mulowererenso .kuti malawi peesident .chakwera asalolenso ngomgole ya I M F ndi world Bank omwe zimapatsa mohamvu azunguwa kupanga devalue malawi kwacha yomwe imàkhala njira imodzi yobera chuma chakumalawi. Cifukwa interest ya azunguwa imachuluka nkhani nkhani
Awa ndamene akuyimilira anthu kumalawi awa mulungu aziwadalisa kwambiri
Proud of you guys, may the Lord continue to bless, guide and protect you, proud of you always 🔥🔥🔥🔥
Dc my uncle me your nephew am proud of you uncle live in kenya
Awa ndi omwe akuima pachilungamo viva Malawi first
Viva Malawi first peoples first
Ndiamene asalamulile Malawi. Mawa likubwelali
❤❤❤❤❤❤🙏🙏🙏🙏
Mbambandetu malawi first osati CHIKANGAWA ndi mbava zinzake nohani iyi ndi yapakanthawi koma CHIKANGAWA palibe chomwe amachitapo koma kuba ndi kupha ndi kumanga anthu ulemu wanu malawi first Ambuye adzikutsogolerani
Proud of you 😊 the DC 💪💪
❤❤❤❤ the Malawi first people first we love you all
Viva Mr DC
❤❤❤
Nkhani iyabwino kwambili❤
We love you
Malawi Fest number 1
Zapamwamba ndazikonda kwambiri viva malawi first ❤❤❤
Tizafera mbenderaimeneyi 🇲🇼
❤❤❤thanks guys
Mulibho guys ntchito yanu ikuwoneka ndithu
Booooon kalindoooo ❤❤❤❤❤
The DC uremu wanu mukuyimirela malawi
Malawi first zikomo kwambili pa ntchito mukugwila
Malawi first ikugwila ntchito kuposa president wa mdziko
Booon ♥️♥️
Apolice ndi Amey tchito Yao ndikuteteza boma la chikangawa party osati amalawawi ayi ulemu wanu Mr boni kalindo ndi timu yanu mulungu azikudalitsani
Yeah ndichoncho ndithu
Ndinu anthu ofunikila
Malawi tadzuka iweh
Boma lichte manyaz mwaona kufunka kwa kalindo?mummangeso mwamva? dziko lidzakwiya
Anthu a kuZambia A wemba ndi anthu a nkhaza kwambiri zikomo.kwambiri malawi first mwalowererapo apa zikomo @ Malawi First mulowererenso .kuti malawi peesident .chakwera asalolenso ngomgole ya I M F ndi world Bank omwe zimapatsa mohamvu azunguwa kupanga devalue malawi kwacha yomwe imàkhala njira imodzi yobera chuma chakumalawi. Cifukwa interest ya azunguwa imachuluka nkhani nkhani
President not peesent
Wovala ma jekete abwino abwino sanakafike?
Koma bon ai mulungu akhale nawe
Inuyo ndi reporter kapena commentator? Tiuzeni zimene akukambiranazo
Kkkkkkkk ine uyuyu sindkumvesesa ka report lake limamvekaso kaya handiziwa
DC ndi katundu
That's ur job not zandale
Sapanga zandale komano amayimilira amalawi ngati penapake sipakuyende bwino they take an action
Inu ameneyu angapulumutse ndani ?mbuzi yamunthu ngati imeneyi
❤❤❤
❤❤❤