Inu akabadza ndi amene mumamupasa chakwela mulali 2020 maka inu akuchigawo cha pakati lero mulungu akuphunzitsani phunziro wosamakhala ndi mtima wa jelasi pls lapani apa muona nyekwe mumaziona ngati mandolo inu akabadza aku lilongwe
Akanakhala Kuti akulamula ndi Peter bwenzi kuli mademo anyoooo pano mungoti Kakasi ndiye wakukhaulitsani chakwera no mlomo wakumangani mumasamba a satanism aka boma ndilomweli mukugagada wapansi shame on you Malawians.
Wina kupanda nzeru umuva boma ndilomweli 😢
Boma ndi lomweli tiapase ka term kena basi , kuti basi Manda azangokhala paliponse kufa ngati mwa ntchentche basi 🕺🕺
Ngati dziko tikudziwa dzativuta komano chomwe tikadachita ndikusankha anthu omwe akhoza kusintha zinthu monga cabinet ya new one posayang'anira mtundu omwe akuchokera kapena chipani .
Tipulumitse dzikoli.
Kudzichepetsa komanso chakwera ndi Usi ayime pamodzi alankhule kumtundu wa Amalawi atifotokozere pomwe palakwika ndipo onse apepese Kwa ife alolere kudzola manyazi alape pamaso pa Malawi ndikugwada ndipo tiwawone atapepesa kenako agwirane manja ndi vice yo ndikupemphera Kwa mulungu atikhululukire mulungu amamva zinthu zisintha. Dzichepetseni abwana muona mulungu asintha nyengo zathuzi.
Amen amen amen amen amen
Atha mavuto amenewa, palibe chosatha padziko
JOSEPH MKASA-Chakwera delivery, DAN LUU-Kutchaya kugwetsa uja ndiameneyi.
Agalu MCP koma kuba bas
😂😂😂😂 koma Malawi wathapo
Inu akabadza ndi amene mumamupasa chakwela mulali 2020 maka inu akuchigawo cha pakati lero mulungu akuphunzitsani phunziro wosamakhala ndi mtima wa jelasi pls lapani apa muona nyekwe mumaziona ngati mandolo inu akabadza aku lilongwe
DAMBWEEE NDILOMWERO
How I wish SKC was here
Kod sizingatheke pomwe takhala ma filling station wo ndikuyambitsa mademo achinyamatafe mademo okwiya coz izizi zafika pomvesa chison tisamangojambura better kupanga chiganizo mademo okwiya coz andale akumagwiritsa ntchito achinyamata omwewa ndy kut adziwe kut zikutibhowa komanso kut tatopa achinyamata titenge action komwe takhalako mma filling station MO aaaaaaaa
Alibe nthawi yosaka forex kom alindi nthawi yolimbn ndi DPP kupusa even kubereka kukhal kovuta azimun akugon ku filling station
apapa nde zafika poti tili kuchipendo ,,2025 idzipita kuchimbudziyo ndi munthu no eating anything,chakwera go out kukasiya akayambe kulamulir nyawu,
Cikangawa comwe akudziwa ndi kunyenga ku 49 mbuzi ya munthu palibe cicita iye.Nonse muli kudikilira mafuta tikakumane ku mademo mbuzi zimenezi dzicoke, mcp sikufunika mmalawi muno
Koma kumalawi zaonjeza kuno kuzambia kulibwino zinthu zasintha awonesa asunga ziko
Boma ili lazizilu
Pobwera amati tikuzakoza mavuto a DPP mpaka 4 years sadakoze?
Chomchi nkumakakamira kulamulanso? Mukanakhala ndinu anthu mukanangotula pansi udindo. Izi sizinayambe zachitika kwathu kuno. Boma losowa pokomera, chilichonse nyansi.
Mavuto wa satha ndithu
onse kuno tasanduk odikira pa meru
I don't know kuti campaign awanamiza chani amalawi, mcp
Akanakhala Kuti akulamula ndi Peter bwenzi kuli mademo anyoooo pano mungoti Kakasi ndiye wakukhaulitsani chakwera no mlomo wakumangani mumasamba a satanism aka boma ndilomweli mukugagada wapansi shame on you Malawians.
Ndpo zoopsa