Ndine Gardener Ku Statehouse - Samuel Lwara

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 21 ส.ค. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Mr Samuel Lwara talks about Ghost workers in Government with Leah Malekano on Zodiak Broadcasting Station (ZBS) Exclusive Interview. You can Catch the Rest of the Interview on ​⁠​⁠‪@ZodiakMalawitv‬ Once it has aired.
    Pa Nyasa VoiceBox, Mr Samuel Lwara akukamba zanthu amene amalandila malipilo ku boma koma ntchito yawo yeni yeni siwoneka ndi Leah Malekano pa Zodiak Broadcasting Station (ZBS) Exclusive Interview. Mutha Kupeza Mafunso Ena Onse pa @ZodiakMalawitv Akayamba Kuwulutsa.
    • EXCLUSIVE INTERVIEW WI...
    #malawi

ความคิดเห็น • 9

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 15 วันที่ผ่านมา

    Kwasala ndikutentha state house one day amalawi azakwiya ndithu one day this is the war anthu akumwalira muzipatala no medicine inu mukunjoya ndi ndalama za misonkho i pray that state house moyo uzayakamo

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 5 หลายเดือนก่อน +2

    Kkkkkkk koma ziliko🔥🔥

  • @chikukanyinji6873
    @chikukanyinji6873 5 หลายเดือนก่อน

    Zilikotu ziliko!!!!

  • @user-ud9wl8yg1t
    @user-ud9wl8yg1t 5 หลายเดือนก่อน

    Chakwela ndimbava yayikulu zedi ndi chifukwa chake chilima anati ichosedwe immunity kuti president aziyimbidwaso mulandu ngakhale akulamulila ndipo chakwela akalonjeza kuti ndikazalowa mboma ndizachosa phamvu Zina za president kuti azizayimbidwa mulandu ngakhale akulamulila atalawa Kuba anayiwalilatu nzose

  • @user-vo9ie2gv7o
    @user-vo9ie2gv7o 5 หลายเดือนก่อน

    Ndichifukwa chake kwapita ndalama zambiri ku state house ati zosamalira kapinga mmalo mongonena kuti ndizopangira phwando nthata zanjala izi zikungokama yoonda kale ng'ombe

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m 5 หลายเดือนก่อน

    Misonkho yathu mama nee

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 5 หลายเดือนก่อน

    Dziko laMalawiimenero chonchi tingathkuke .Tidzingolila daily Asaaaa atsogoleri wathu Dziko mukulupititsa kuti .kuba kumeneku bwanji?

  • @user-dd1qq5xq1k
    @user-dd1qq5xq1k 5 หลายเดือนก่อน

    Bargamoyo state

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r 5 หลายเดือนก่อน

    Chakwela mbava yahikulu Malawi