ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
More thanks to flora suya for brilliant idea ❤ I really love you're team, keep it up, May God bless you pipo.
Good nice and I can't wait for the next
Flora Suya, you are great on creativity, and all the actors are great❤! The story lines are excellent as one can never predict the next episode actions.
Kkkkkk I can't wait next Amulelemba akukana mafunso ambwelela komaso Sasoka akumuthuzitsa kuti azipaga zake
😂😂😂😂😂 Koma guys mumaoanga ma comedy koma iyi yokhayi mmmm munaikonza mbambande guys limbikirani ,,,,ine LUFEYO WAALUFEYO from south Africa LIMPOPO
Wachibwibwi ali bho wabwera ndi fire.mai shokoshoko ur number one kkkk
Kkkkk Bengaz yomweyoooooo kuno Shoko Shoko and Khwini
I love it
Kmtu ku compaund kwa mdyangu mmmm kuli zochitika 😂😂😂😂 shokoshoko kumadyetsela mozemba bnji proud of you guyz kutimvetsa kukoma
Mmmm I love the whole team of mdyangu ,you are the great.
😂😂😂mulelemba ndiwetu wa phokoso,keep up good work guys watching from durban
Guys mdyangu ndi 1 mumativesa kukoma keep it up good job watching from R S A 🙏🙏🙏🙏
Filipe form Moçambique tete tsangano sasoca waziona mukutivetsa kukoma kwambiri
It's nice and I love it. Keep it up guys
Everyweek after watching this show always good for laugh 🥂cheers 🕊📖.....✍
I am addicted to mdyangu & mfumukazi...all directed by Flora Suya.
Much love guys mumatha koma I miss chiphwanya please come back
😂 😂 😂 Sasoka muli mtopola wonga wa Mlelemba 😂🤣🙌
Mulelemba😂😂 umandmvesa kukoma❤
Ati machimo akukwanani mpaka mwafika pomutukwana mulungu kkkkkk
Mulelemba sakazi ako awoo aliyese akwadziwa😂😂😂😂😂mulelemba sazathekaso basi❤❤❤
Ati mkatikati moyankhula mpaka muluzu😂😂😂😂 sasoka ase
Wachibwibwi wabwera ndi Moto😂😂😂😂😂
😂😂
Kkkkkkkkk aaaa queen mimba ndiya chokochoko eeee akangodziwa mai shoko shoko uzionatu queen azakusamusa ccta wako
Great work!
🔥🔥🔥🔥🔥🔥koma Friday likubwelari kuvuta hvy kkkkkk mumatinvetsa kukoma🔥
Kkkk mulelemba #1
Mpaka sasoka wanyowandi eti????? Mecry waitchotcho yolakwika uku 😂😂😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤😂😂❤❤❤❤❤ I love this
Excellent films.
Lululuuuuuuu moto buuuuuu n'dyangu nkhani yosekesa ndikumvesa chisoni ndiyoti queen momwe wakongolera kulephera kupedza mamuna wake wake mpaka nkumathana ndi alamu awo ? Mpaka mimba kodi zitha bwanji kusogoloko?
The Best one
Kkkkkk mulelemba umakwana iwe umandiwaza
😂😂😂 Kma sasoka please l need chimphwanya mmm
Much love sasoka and mlelemba mumakwana 😂❤❤
Mayi shokoshoko ndi moto, Sasoka waziona
Kkkk chiphwanya abwela ndiyotani Kwa kwin 😂
Wachibwibwi akuitha 😂
Mnyanyiwa batchala kwa dyangu. Ashokoshoko ndi mecy samalani.
Mumatha watching from RSA
Welcomed Anzawo a Nkango 😄 🤣 😂 😆 😄 🤣 😂
Sindi wokatenga chiberekero uyende bwino😂Mumatimvetsa kukoma gyz limbikirani nonse
Mulelemba umakwana 🙏
Akutindibengazi 😂😂😂😂😂😂😂
mulelemba sakunama aliyese akhare ndi banjaa😂😂
Kkkkk km ashokoshoko muzitenge bwino ndi mulamu wanu kaya zidzakuthelani bwanji
Kkkk mulelemba kumfusa munyanyiwa ati mudayamba mwakhalapo ndi mimba kkkkk🤣🤣🤣🤣
Mdyangu ministries 😂😂😂😂😂 koma mlelemba sazatheka 😂😂😂😂
Kusatila mwachidwi Queen mimba yake ndibya mulamuBanja la Shokoshoko silili bwino ndithu pavuta hahhaahha amuthila madzi Sasoka
Frola never give up we are with you all the best
Mdyangu ndi one,,,Queen ND Sasoka ndye itiso imeneyo kkkkk
Waishosha kkkkkkkkk 😂🤣😂🤣😂
❤ Mulelemba number 1🤣🤣
umayitha mulelemba sanakhalepo ndipakati ameneyo😂
More fire 😂😂😂
Kamtchini kopanga munthu ndi mzimayi 😂😂😂😂😂😂 mlelemba suzatheka
Mulelemba kkkk,ndi sasoka
Waishosha , sasoka 😅😅😅, wakumana nazo
Miss Franco's family plz bring them back 🔥🔥
Ndipo ndimaona kuchedwa kufika Friday ❤❤❤❤nyc guys
Mbambande shokoshoko wayamba njengunje wayambapo kudyesela mimba bas😂😂😂😂 mercy nayeso wafikafikapotu amuna akusowad 😂😂😂😂
Sasoka eish 😂😂😂😂 mankhwala adzino ndikudya nzimbe 😂😂😂😂😂
Koma sasoka sazatheka ayi 😂😂😂😂😂😂😂 akut mercy abweresera oimba likweru
Tifane muphanye mercy yo wakuonjeza😂😂😂😂
Km sasuka plz 😂😂😂😂😂😅
Queen ndi mercy mumakwana
Mulelemba ndi zose momo
Nzake wamwana wankango alibho...chibwibwi
😂😂😂😂😂koma mulelemba ndi machine
❤❤❤🎉🎉 mumandimvesa chisangalalo mbweeeeeee ❤❤❤❤
So Queen mimba alinayoyo ndi shokoshoko😮😮😮
Mulelemba😀😀😀
Komatu queen ndi ashoko shoko mukuziwana
Mumativetsa kukoma muzangosowa❤❤❤
Koma guys mukuithatu keep it up koma mundisungile queen yo kapena mercy😂
Wachibwibwi ali bho wabwera ndi fire
Shokoshoko kudyetsela mimba mamuna wabwino kwambiri😂😂😂😂😂
Zafikapo kwa shokoshoko
❤❤❤❤
I love you so much 😂😂😂❤
Shokoshoko ndi queen mantha nyumba mwanu momwe 😂😂😂😂
Please improve on sound especially that bell ringing ......
Munyanyiwa
Ya pa 30June yandidutsa mwezi uno wosandiiwala😢
Munyanyiwa😂😂😂😂
Nice 😂
Sasoka 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Gre
Much love for Queen Shokoshoko Mercy and Sasoka❤
Much love indeed, Flora Suya 🎉and your creativity that dazzles!
😂😂❤Shoko wamwa wa mkaka
Komatu a mlemba 🙌🤣🤣 human factory
Abusa a mlelemba mumakwana moto kuti buuuu
Kwa mercy kwabwel alendo😅😅😅😅😅
Chiphwanya please
Tifane iwe 🤣🤣🤣🤣🤣🤣 zofunda za Blue
Human husband ndi azimayi kkkkkkkk koma mimba ya queen ndiya mwana WA nkango 🤣🤣🤣🤣🤣
Eshi chibwIbwi wabwela iweo
Wachibwibwiyo wabwera bho❤
😆😆Nice
Mulelemba umakwanira
Zilibwino guyz pitilizani kutisangalatsa
Koma wachibwibwiyu wabwera ndi moto kkkkkkkkk
Sasoka wayishosha 😂😂😂
😂😂😂 Koma Mulelemba ayi fenkis
More thanks to flora suya for brilliant idea ❤ I really love you're team, keep it up, May God bless you pipo.
Good nice and I can't wait for the next
Flora Suya, you are great on creativity, and all the actors are great❤! The story lines are excellent as one can never predict the next episode actions.
Kkkkkk I can't wait next Amulelemba akukana mafunso ambwelela komaso Sasoka akumuthuzitsa kuti azipaga zake
😂😂😂😂😂 Koma guys mumaoanga ma comedy koma iyi yokhayi mmmm munaikonza mbambande guys limbikirani ,,,,ine LUFEYO WAALUFEYO from south Africa LIMPOPO
Wachibwibwi ali bho wabwera ndi fire.mai shokoshoko ur number one kkkk
Kkkkk Bengaz yomweyoooooo kuno Shoko Shoko and Khwini
I love it
Kmtu ku compaund kwa mdyangu mmmm kuli zochitika 😂😂😂😂 shokoshoko kumadyetsela mozemba bnji proud of you guyz kutimvetsa kukoma
Mmmm I love the whole team of mdyangu ,you are the great.
😂😂😂mulelemba ndiwetu wa phokoso,keep up good work guys watching from durban
Guys mdyangu ndi 1 mumativesa kukoma keep it up good job watching from R S A 🙏🙏🙏🙏
Filipe form Moçambique tete tsangano sasoca waziona
mukutivetsa kukoma kwambiri
It's nice and I love it. Keep it up guys
Everyweek after watching this show always good for laugh 🥂cheers
🕊📖.....✍
I am addicted to mdyangu & mfumukazi...all directed by Flora Suya.
Much love guys mumatha koma I miss chiphwanya please come back
😂 😂 😂 Sasoka muli mtopola wonga wa Mlelemba 😂🤣🙌
Mulelemba😂😂 umandmvesa kukoma❤
Ati machimo akukwanani mpaka mwafika pomutukwana mulungu kkkkkk
Mulelemba sakazi ako awoo aliyese akwadziwa😂😂😂😂😂mulelemba sazathekaso basi❤❤❤
Ati mkatikati moyankhula mpaka muluzu😂😂😂😂 sasoka ase
Wachibwibwi wabwera ndi Moto😂😂😂😂😂
😂😂
Kkkkkkkkk aaaa queen mimba ndiya chokochoko eeee akangodziwa mai shoko shoko uzionatu queen azakusamusa ccta wako
Great work!
🔥🔥🔥🔥🔥🔥koma Friday likubwelari kuvuta hvy kkkkkk mumatinvetsa kukoma🔥
Kkkk mulelemba #1
Mpaka sasoka wanyowandi eti????? Mecry waitchotcho yolakwika uku 😂😂😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤😂😂❤❤❤❤❤ I love this
Excellent films.
Lululuuuuuuu moto buuuuuu n'dyangu nkhani yosekesa ndikumvesa chisoni ndiyoti queen momwe wakongolera kulephera kupedza mamuna wake wake mpaka nkumathana ndi alamu awo ? Mpaka mimba kodi zitha bwanji kusogoloko?
The Best one
Kkkkkk mulelemba umakwana iwe umandiwaza
😂😂😂 Kma sasoka please l need chimphwanya mmm
Much love sasoka and mlelemba mumakwana 😂❤❤
Mayi shokoshoko ndi moto, Sasoka waziona
Kkkk chiphwanya abwela ndiyotani Kwa kwin 😂
Wachibwibwi akuitha 😂
Mnyanyiwa batchala kwa dyangu. Ashokoshoko ndi mecy samalani.
Mumatha watching from RSA
Welcomed Anzawo a Nkango 😄 🤣 😂 😆 😄 🤣 😂
Sindi wokatenga chiberekero uyende bwino😂Mumatimvetsa kukoma gyz limbikirani nonse
Mulelemba umakwana 🙏
Akutindibengazi 😂😂😂😂😂😂😂
mulelemba sakunama aliyese akhare ndi banjaa😂😂
Kkkkk km ashokoshoko muzitenge bwino ndi mulamu wanu kaya zidzakuthelani bwanji
Kkkk mulelemba kumfusa munyanyiwa ati mudayamba mwakhalapo ndi mimba kkkkk🤣🤣🤣🤣
Mdyangu ministries 😂😂😂😂😂 koma mlelemba sazatheka 😂😂😂😂
Kusatila mwachidwi Queen mimba yake ndibya mulamu
Banja la Shokoshoko silili bwino ndithu pavuta hahhaahha amuthila madzi Sasoka