Koma Chisale😂😂😂😂 ati akhakhakha,abwampini,abwande,agulukunyinda😂😂🤣🤣🤣 ku Dpp kudzangochoka Chisale nd Suleman eeeeeeeee zinthu sizingayende. Dpp my vote ❤️❤️❤️
My vote is for Apm osati chisilu tili nacho lelo chingoziwa kuyankhula .....galu iwe watibwelesela mavuto omwe sitinayembekezele Kwa munthu wopusa iwe kwambili
DPP is good but chisale is a dangerous man he’s MCP in one, the other main problem is the cadets just like UDF had young democrats cadets are the reason every party is hated.
Koma Chisale😂😂😂😂 ati akhakhakha,abwampini,abwande,agulukunyinda😂😂🤣🤣🤣 ku Dpp kudzangochoka Chisale nd Suleman eeeeeeeee zinthu sizingayende. Dpp my vote ❤️❤️❤️
Ndipo zoona anthu olimba mtima ambuye apitilize kuwapatsa mphavu
😂😂😂😂Mcp tilibe mzeru ingowonjezera mkwiyo wa anthu pa zomwe zikuchita dpp woyeeeee moto kuti buuuuu❤❤❤
Akhalitse suleman 🔥🔥💙💙💙
Mkaladi wathu wathu 😁💪💪💪💪
😂😂😂😂😂 Koma ali bho and is a hard worker
Fighting for aur freedom thanks adadi
A man with no fear 💪💪
Seleiman ndiwe big awuze chilungamo osabisila chakwera muthu oipa kwambili
Auze chisale
Body gaurd wathu
Iweyo palibesoooo
Moore fireee
This team is strong enough tiyenazoni guys chakwera sakugonananu turo nanga azitigendaso anthu tikugona ndinjara daily ndare zauchikangawa basi😢
Powerful speech
Adad my vote
Amalawi tatopadi mwandisangalasa ♥️♥️♥️♥️♥️💃💃💃
APM 2025 my vote
Suleman🙌🙌🙌🙌umatiimilira chonde musasiye kutiuza chilungamo😅😅😅😅😅
to say the fact guys DPP fanz yamb akuikonda kwamb ,even ineyo mmaikondaso hvy 💯💯💯💯💯
Kkkkk akuti eti mwina Mulungu akawakhululukirani kukachisi konko
Kulibetu chiguru chawoyimbatu uku koma anthu okhawo njuchi. Ndi pamene mudziwe kuti kuyendetsa boma ndi serious business, si zamakape izi. Munachita kulanda simunawine ngati MCP panokha.
Dpp my vote
APM my vote
My vote is for Apm osati chisilu tili nacho lelo chingoziwa kuyankhula .....galu iwe watibwelesela mavuto omwe sitinayembekezele Kwa munthu wopusa iwe kwambili
MCP vote yanga ...
Mawu mawu Mr s ❤❤❤
My vote 🎉❤❤❤❤❤
Chakwera zamukanika
Sadziwa kuyendetsa boma...abwerere ku mpingo wache
Tiuzen zomwe mudzapange,Ife tikufuna anthu amasomphenya.
DOLO KAPWIIIII 🔥🔥 sulemani
Chomwe ndikuziwA ine ND DPP💙💙💙💙💙💙🔥☝️🇿🇦💍
Katundu omanga ndi mawaya uyu🎉🎉🎉🎉
Chimwendo banda ndi john tembo wachiwili yemwe akumakonza ziwembu osati masewela .....munthu woti amavala nkhwaila mmbuyomu lelo wamanga ma lodge 10 mu zaka 5 zokha .....munthu wokuba koopsa
Bravo DPP
Dpp ndi chiyembekezo cha a Malawi 🇲🇼 guys 🇲🇼 👦 Apm pls coming back to take care about your peoples 🙏 we need you Adadi 🙏 ❤️ 2025 boma dpp woyeeeeee
Sulemana 🙏🙏🙏🙏🙏
A p m my vot
Ineso basi ndikulowa dpp
Baba ❤
🎉🎉🎉
Koma chisale sizinthu ndithu😂😂😂😂
Mumatiimila bwana
🔥🔥🔥🔥
Bigy Bigy Suleiman
Opanda nzeru yekhayo ndamene angatenge side
😂😂😂 komatu Suleman
Boma ilooooooooo 🙏🙏🙏💙💙💙
Good speech yabho
Sure
Chakwera mdi chisilu cha munthu .....timaona ngati tavotera munthu osaziwa kuti tavotela chibekete cha munthu
Sama suleman amalakhula
My voti
Nzowonadi big sulemani
Dzanja la lemba a chikangawa
Ndipo chilima anachokadi bwino bwino ku dpp, koma MCP manyazi bwaaaa kuganiza mwa uchisiru.
Boma❤
Gangata apweteka anthu munthuyu ali ndi chikoka kwambili
Sitikufuna chikangawa
Suleman katundu
Inu chanu mulibe 2025
DPP is good but chisale is a dangerous man he’s MCP in one, the other main problem is the cadets just like UDF had young democrats cadets are the reason every party is hated.
Akulu mukunama kwambili chisale ndi wa Dpp weniweni
Chimwendo ukumva bwanji kumeneko kkkkk
Koma ineyo chisale ndi sulemani amandimvesa kukoma olo data izitha ndimakagula basi
Katundu waboma big man DPP woyeeeee
Abweleledi m church sukunama suleman
Pangolin
Mcp ndi salu zanu za red zo muzaziwotcha one day
Boma siilo koma ndiili
Panyapako ndi Boma lako lopendamali ......ndi Bomanso limeneli
Zilibwino😊
Koma Mai ayankhula kumapetowa muli ndale no wonder dpp 2025 is coming back
ndpo live ndale mai amenewa amazidzwa kwamb kmso eee kunena zoona boma ililo laonjeza kwamb its too much
Umakwana mzungu wathu
Akumangani ndipo Boma ili😅😅
Boma Koma ili
Abwelere mkachisi ameneyi ufumu wawo walephera a MCP
Saeed Mussa
Kumeneko
Kuswakuswa
Komatu munasowatu bigi
Mfunso langa kwa mcp njakuti, oyimba angati mukuwaona pansonkhanowu? Dpp ndi chipani cimene mlungu anacikhadzikitsa kuti cidzalanditse a malawi mkanwa mwa ng'ona za cikangawa mukuona bwa? 2025 APM boma! DPP Oyee!
Kma😂😂
Pafikapaa aliyese a jame yake
Jama yako 2024/5
MCP mboliyamake
Boma langa ilo 2025
Dpp Yomweyo basi
Boma ndilomweri
Sukunama kape iwe
Kkkkk km macadet udzinamizatu uku mchinj simuidzwa ndipo muzakhumudwa
Kagwere uko zoba
Dpp ungo utaya nthawi kuno ku mchinji dpp never again.
Kape iwe ukhala chonch😅😅😅😅😅😅
@@Belinda-c6e Wawa nikuuzani zoona mchinji singavotere dpp chipani Cha tsankho.
Kodi central region ndi mchinji yokho .....mmalawi muno ndiye mbuli ndi zambili .....iwenso ndi mbuzi bwanji
Suleman katundu