Inu palibeso kulowa m'boma mukachitamo chiani poti mavuto onse tikuwaona lerowa source yake ndinu,lero mudzakoza chani poti all things has already destroyed by you,I was one of your supporters ,but once you have disappointed people in this country,those they know you very much ,you can't enter into the government.Thats true lie to say you are going to improve this country.
My vote 💙 💙💙💙
Congress party nje nje nje😢
My vote ❤
My vote too
Mbambande DPP amene ana choka ku DPP akunvakuwawa.❤❤❤🤸🤸🤸🤸🤸👍👍👍
Zamphamvu kwambiri ambuy akuze malire achipanu chathu 2025 boma💙💙💙💙💙💙💙💙 moto kut buuu🔥🔥🔥🔥🔥🔥
This is our beloved next boma
Chipani chokondedwa kwambiri adadi tikufunilani moyo wautali kuti musamale anawanu 💙💙💙💙💙💙💙💙
Akatundu achipani chomanga ndi mawaya cha dpp moto ku 🔥🔥🔥🔥🔥💙💙💙💙💙
Ndazikonda 🤞💙💙💙💙
My vote
Dpp my vote eeeeeeeee
chipani choti ukachipna. khawa kuthawa koma chikangawa kumafuna kugwa bp
Ndazikonda ndipo kumva. Kukoma
My voti
Chipani chafuko❤❤❤❤
😊
Koma nde anthu atchena koopsa chipani chosachititsa manyazi🔥🔥🔥
My vote 💙💙💙💙💯
Zthu zake kuposa zitsilu zili m’boma zija
Adadi ndi mbambande
Dpp my vote kkkkk🎉🎉🎉
Mcp ulendo bas Kwao dpp bomaaaa
I see Jane asah, beautiful 😂😂😂 masankho awa wakuba agwidwa ndithu 😂
Wao kumaopa ngongole coz enawa angongola zambili km aaa ngogula oyimba malo mwa mafuta avutawa eee kkkk
Wishing you all the best 🎉🎉
Mbambande
Adad woyeeee
Anthu tikumanena kuti Malawi tili ndinjara tivomeleze kuti njara tilinayo koma tisaloze chala boma chifukwa kunjaku mvura kunalibe sinagwe moyenera ngakhale adpp akanakhala mboma njara ikanakhalapobe chifukwa amagwesa mvura ndi namalenga dpp eshiii kubwelera mu boma Palibe chomwe angapange
Iweyo ndi munthu wopusa kwambili ...njala iyi ndiyochita kukonza ....taona feteleza wafika 120000 munthu wakumuzi angakwanise kugula feteleza
...chakwera akugwesa kwacha mwadalala ...panopo pamalawi mavuto ndiosayamba ...taona njala ndiye ndi imeneyi .....nanga kukwela Kwa katundu pa nsika tsiku ndi tsiku mafuta a galimoto kulibe .....mukamafuna kuteteza chakwera wanuyo muzichita manyazi .....pano akufuna timuvoterelenso koma tikamuvotela asintha chiyani ....munthu wopusa kwambili
Akufuna adzadyenso ndalama za a 🇲🇼🇲🇼 kubabasi Murali ndi chani bola a silikali alamulile izi zichitika
DPP not an option, too angry and hungry people
Ndibe class mate kkkkkk
Tikusapotani
Mcp katundu mpaka kusaukitsa DDp aDDp kd Mesa munabanso ndarama nanuso kd ndarama zakuba sizichedwa kutha nanuso MCP muchejere ndi ndarama mukubazo ndiye kuzankharaso kumangidwa
Achakwera anthandizeni aDDP cz tsiku Lina azakulembani ntchito kapena azikukhururikira pamirandu yonse cz big aaaa yalakwa ine Siwa DDp mayazi km
Koma mpaka chipani kusonkhelana ndalama aaaaa azathu chitani manyazi
Kulibe kulowa inu munayamba mavuto awa mumalawi
Akulu inoyu mumakhala kuti?
Mwandichimwitsa mxeeew
Kapena mwabadwa liti?pamene athu amagula feteleza patengo wabwino, mafuta akupeza ,ndalama yakunja ikupezeka,
@ElizabethMajiga osanamizana anayamba kusakaza Malawi Ni Peter yo mwamva atabwera apa palibe angazasinthepo kanthu Bola bingo
Ine nine wamkulu iwe ndiwe mwana
Inu palibeso kulowa m'boma mukachitamo chiani poti mavuto onse tikuwaona lerowa source yake ndinu,lero mudzakoza chani poti all things has already destroyed by you,I was one of your supporters ,but once you have disappointed people in this country,those they know you very much ,you can't enter into the government.Thats true lie to say you are going to improve this country.
My vote❤
My vote❤❤