Repent mama before is too late it will be the same way the day u will departure. The Agel of God adzawerenganso chimodz modz kut munayikira umbon wabodza. Kamba ka ndalama
Zomwe awa akupanga sakudziwa let them do zopusa zawozi trust me Allah always give back ntchito Zako issue iyi siyongoti aitenge mwachibwana like the way she's doing
Namiwa saw this coming and he just stepped aside informing the nation of Malawi that the commission of inquiry will not be independent instead it is being funded and influenced by some top officials. But Time factor is a very stupid thing , the same time will judge us all. It is very difficult to get rid of the truth.
Uwu ndiye uchiteiru..ngati munali ndi umboni bwanji osakapere k a agalu be in me mwakhala mukusaka be chakwera.Chilima anali wa kwathu ku Ntchewu..musanamizire kumukonda ..Minamuzuza Ku DPP
Not only Angoni but the whole nation this death was more than I there is also other people we are related with our sister the pilot from Thyolo we will miss her the rest of our life
No way the report is not clear somewhere. Mrs chilima already told his housband that she will not attend the funeral because she had an assignment to submit hence she needs to concentrate on that. This time when Mary chirima was responding to his housband chirima had not booked for the jet! So how would then the report say Mary chirima was going to the funeral later she changed her mind because of the same assignment? That necessitated kumuuza chimwendo Banda kuti yazaza yet madam chirima decided not to go before Jet being booked. Chirima booked the jet after nkazi wake atatena kuti sapita that's when he changed his mind kuti ndipita ndekha then he started making ma logistics according to the report so we still have many questions There are still many answers you will need to tell us for us to understand and be confident in the report.
Namiwa anapempha kuti kafukufuku azichitika live osati mobisa Koma zinakanidwa,Lero mukubwera kuzafotokoza live ku public cholinga zioneke ngati pali HONESTY?? MUDIKIRE NTHAWI YA CHILANGO CHOCHITIRA UMBONI ONAMA MONGA MWA MALANULO NKHUMI AMWINI CHILENGEDWE CHONSE.
Ine ndingoti amene anatengapo gawo pa ifa ya anthu 9 aja nawoso adzafa ifa yowawa mulungu ndithu achite nawo anthu amenewo 2025 isathe anthu amenewo alipo
The weather report was provided by the German company and you saying "the weather was bad" is not evidence. Si umboni. You can google the weather that day.
Repent mama before is too late it will be the same way the day u will departure. The Agel of God adzawerenganso chimodz modz kut munayikira umbon wabodza. Kamba ka ndalama
Pplppppppppppplppppppppppppppppppppppppppppppppppppppppplppppkkkkllppphjp0
Only God knows the best 🎉🎉
Mumakambirana mobisa mumakama kupangira pa live tv..apa mukubwera pa live tv...kuti bwitika amalawife ndibodza... anthu olimba mtima kwambili
Ndipo anthu awa alibe nzeru kwambili anakaululaso mobisa momwemo kaaaa
Zomwe awa akupanga sakudziwa let them do zopusa zawozi trust me Allah always give back ntchito Zako issue iyi siyongoti aitenge mwachibwana like the way she's doing
Adziyakhuratso muchichewa nanga akuwauza ndi eni Malawi
GOD is watching you all
Mulungu analiko kuchikangawa::komanso akuziwa zobisikazo
Watching from very far Zambia, just waiting 2025 when we shall know the truth
Monseugnor Thawale is apriest of high integrity cannot be corrupted
Zitsiru izi zinakambilana kale.Ndege yokwela 19 people who told chimwendo kuti yadzadza?Nomse mwadya ma millions
Dzitsiludi
Agalu mulibe manyazi.
Kumwamba ndiomwe kuli ndi Ma yankho enieni popeza kwa mulungu kulibe chobisika 😢😢
guys apapo palibe chazeru tingopasira mmanja mwa mulungu bas osewa Amafunaso ndalama
chilungamo ndichovuta 😱😱😱😱😱😱😱
What surprising me is that who told Chakwela that the plane reached Mzungu as it was not like that.
Namiwa saw this coming and he just stepped aside informing the nation of Malawi that the commission of inquiry will not be independent instead it is being funded and influenced by some top officials. But Time factor is a very stupid thing , the same time will judge us all. It is very difficult to get rid of the truth.
Mukamaliza muyankhulekonso CHICHEWA,nawo akumudzi amveko.
Ndipo zoona , sindimaona chifukwa chomwe amalimbikira English coz ndi ochepa omwe amamvesa chizungu , ngakhale ku parliament anayenera kumalankhura home language momwe amachitira maiko amzathu
Where is black box?
Who told chimwendo that the plane is full????
Chakwera chikangawa adapha chilima.
Ndipo asamachiteso mkuvutika anthufe timadziwa kale zinaoneka kale ndenge itagwa chipogwe chomwe anapanga nzawo kumusiya muthengo
Uwu ndiye uchiteiru..ngati munali ndi umboni bwanji osakapere k a agalu be in me mwakhala mukusaka be chakwera.Chilima anali wa kwathu ku Ntchewu..musanamizire kumukonda ..Minamuzuza Ku DPP
Nanga Black Box,ilikuti?
Angoni tiyeni kunseu timatche biyeni wathu ndiathu Ena 8 ..izi sizoona aiii😭😭😭
I blame HRDC kulanda boma mwauchifwamba kupereka kung'ona izi 😢
😭😭😭😭😭😭😭 nkhopezo zikuchita kuzitsutsa zokhakut pakamwapo pakunenaboza eee koma zikoili linatembeleledwa ndithu
Agalu inu leave the guy to keep on resting 😢
Let's leave it in the hands of the Almighty God
NO SECRET UNDER THE SUN.MUNTHU AMAPHEDWA ALIKO EKHA KOMA ZIMAULULIKABE SO MWABISALA MU MBATATA ACHAKWELA NTHAWI IKUBWELA MUONA NKWIYO WA MULUNGU.
Ubwino wake andalenu mulibw chinsisi tikasintha boma 2025 muz 8:55 anenanso nokha kuti umboni weni weni ndi uwu
Osaiwalatu paja tinauzidwaso kuti black box ilipo munayitanisaso black box kuti zinveke zamenemoso ngat ?
aaaa makolala aubusa nanga mwapereka report lachilungamo😢😢😢😢, Ambuye akuoneni athakati inu
You must have to know that the Government can change all the enquiry team you will be questioned.
She is reading emphasizing points to support their narrative.
Zazii zenizeni
Nde ngati anafera mu ndege then who removed the close and shoes...... 😮
Meaning that Mr sikwese is the one stopped Mr chimwendo to board an aeroplane
Rest well Raph kasambara
Ngakhale azungu ndiodabwa😢😢😢😢
Peter atulutsenso report la commission of inquiry la 2019 za Alubino killings
That's offside Sir
God is watching
God knows it all .
😢😢u sunu zanyoko nonse azakulangani
Where is interpreting for chichewa vision abi
I want know why chikangawa he didn't go
Khope za anthu omwe ali mu room sakusangalara coz akuziwa kuti zonse ndi zaboza😢
Angoni Musavomeleze zopusazi wake up Andi fight for truth chakwela his a Deval
Not only Angoni but the whole nation this death was more than I there is also other people we are related with our sister the pilot from Thyolo we will miss her the rest of our life
Nosese vomerazani kuti kuli ifa
Or imfa ya kasambala mukuyivetsesa inu?
Imeneyo si report.
Zachamba zanuzo musake owauza musamatinamize ,,we know this was a long project God knows ,,,rest well Bhiyeni
2025 Malawian will answer this
Koma muzinena zoona chifukwa mwini wake akukuwonani chilima
Know that there is God in heaven
They must underline your words, bro
No way the report is not clear somewhere.
Mrs chilima already told his housband that she will not attend the funeral because she had an assignment to submit hence she needs to concentrate on that. This time when Mary chirima was responding to his housband chirima had not booked for the jet!
So how would then the report say Mary chirima was going to the funeral later she changed her mind because of the same assignment? That necessitated kumuuza chimwendo Banda kuti yazaza yet madam chirima decided not to go before Jet being booked.
Chirima booked the jet after nkazi wake atatena kuti sapita that's when he changed his mind kuti ndipita ndekha then he started making ma logistics according to the report so we still have many questions
There are still many answers you will need to tell us for us to understand and be confident in the report.
Akubanja apapa akuwaputatu 😅😅
Ambuye akukhululukileni amai inu popeza simukudziwa chimene mukuchita mwava
He wanted to go by road- someone might have opted for him to go by air in order to see him off to Bahamas Eish
Zazii
Zidzadziwika chilungamo Chakwera akachoka pa mpando
Tizapanganso commission of inquiry yanthu 2025 nonse muli apa tikazapeza zoona zake muzayankha mulandu
Where is black box
Zachibwana
Mwalandila masaka ngati Adalama , mulemera ndi dziko la MCP kuti phimba maso
😢
Izi zaugalu
Chakwela ,from President to Prisone just now
Umboni uwu after moyo wina muzakayankha idzi yehova akuona zonsezi
Amakufunani kuti mukapelekele umboni simunanene lelo muzitsutsanzo eish muli mvuto
Wa mike please awasiseko..
I don't see her face kuno...
Maybe ndine wamfupi
M 2
Nonse amene munali mu inquiry muyenera kuzayankha mafuso before your master Chakwera
Amayiwa akuchita kuoneka ochenjera ndiposo oti sangakane chibanzi
chionongeko chanu chayandikira
Death at the Funeral.... SKC MHSRIP....😭😭😭😭😭😭
Achipani cha mcp bwanji sanakwele nawo ngege? Kd a Chilima amagwira ntchito ndi a opposition okhaokha
R l P 😭😭😭😭
Namiwa anapempha kuti kafukufuku azichitika live osati mobisa Koma zinakanidwa,Lero mukubwera kuzafotokoza live ku public cholinga zioneke ngati pali HONESTY?? MUDIKIRE NTHAWI YA CHILANGO CHOCHITIRA UMBONI ONAMA MONGA MWA MALANULO NKHUMI AMWINI CHILENGEDWE CHONSE.
Za nkutu mbuuuuu
Zausilu izi,,chilungamo tichiziwa 2025 mpamene muzaululane,,,ndipo ife amalawi sitizalola kuti mukakhale ku ndende tizakuwoshani moto bad people
Kaya
Mulungu ndiye akuziwa anthu oyipa inu mwalandila ndalama km muziwe kt mulungu sachedwa safulumila 1day chilunggamo chizaziwika
Black box adayibisa ku state house aliyiwala komweko akayipeza akukalowako chaka chikubwerachi tizava zose
Kodi mboni zikhale anthu anamwalirawo
Only god knows the truth
Amalawi anzanga mumatichitsitsa manyazi umbuli mpaka pa TH-cam ngati muli ndi umboni osakasuma ku khoti bwanji zaululika zaululika ndiye kuti chani?
Kenako mukutivutisaso ndka smartmatic kanu please tisiyeni tipume
What Mossad terrorist came to do in Malawi during the same period?
Please stop wasting your time Malawians are not fools.
Apa onse wakumoto ndayankhula chifukwa cha ? Muone khope zawo zikuoneka kuti chinyengo chalowapo
Mzimayi olimba mtima mfiti ya ikazi
Zopusa izi agalu inu anapha chilima ndi chakwela ndi gulu lake anthu oipa awa
Why u never come live B4
Mabodza okhaokha ogwidwa ufiti paja safuna msing'anga ndiye kukana kukonderedwa ndie palibe chanzeru mungatiuze ife timadziwa basi mmene zinakhalira mudzanena nthawi ikubwera.
God is watching from a distance
Takhonzeka ife anthu aku ntcheu kuchotsa agaru amene adapha chilima
Zaziwik
Aaaah panyoo pake mayiyu fotsake!
Ine ndingoti amene anatengapo gawo pa ifa ya anthu 9 aja nawoso adzafa ifa yowawa mulungu ndithu achite nawo anthu amenewo 2025 isathe anthu amenewo alipo
Even nkhope zawo zikuoneka za chinyengo
Zoonad
God never fail let us wet and see 😂😂
Koma ineyo za IMFA iyiyi only God knows
Zikundiwawa bwanji ndikamamva izizi
Koma zoseyenda
Chilichose chili ndi mathelo ,munachosa azanu miyoyo yawo mowawisa mitima yawo ,end pangatalike inuso muzafa ifa yowawa ,nose omwe mukuikila umbon zabodza.
Palije chazeru apa ndenge yikasowa mulenji usiku wose uwu wakarekerachi kuyisanga musimuthowa mura two wasilikali wakuchezera kugwira tchito icho chikapangisha murongozgi wacharo kurekesha wasilikali kupenja ndenge cthivichi ndipo chimwendo wakakhilirachi kutipusika yayi
The weather report was provided by the German company and you saying "the weather was bad" is not evidence. Si umboni. You can google the weather that day.
English cadet imamucheka ndiye sanganene chilungamo Cha report
Zoona zenizeni za report ya ndege ziziwika a Malawi akachosa boma lovundali pa Sept 2025
Ameneo ndimaganizo anthu sitikuziwa akubanja kut maganizo awo alipat
Afufuza bwanji popanda akubanja komanso opposition parties
Kongotenga MCP yokha yokha inquiry apanga bwanji omwenso anapanga chiwembu
Asatana inu mulibe manyazi chidzadziwika chilungamo pangatalike landilani ndalamazo
Palibe wambeu tonse paulendo,ndipo kuweluza ndikwake kwa mulungu
❤❤❤❤ that's true I agree with you