Support me by buying Titsitse Data Bundles through this link. bit.ly/Afropartisan Just tell them how much data you want to buy❤ These are their packages 500mb at MK400 1GB at MK750 2GB at MK1200 5GB at MK3000 10GB at MK5750 ALL BUNDLES VALID FOR UNLIMITED DURATION UNTIL YOU FINISH YOUR DATA UP TO THE LAST KB... I will receive a small commission 😊
Support me by buying Titsitse Data Bundles through this link.
bit.ly/Afropartisan
Just tell them how much data you want to buy❤
These are their packages
500mb at MK400
1GB at MK750
2GB at MK1200
5GB at MK3000
10GB at MK5750
ALL BUNDLES VALID FOR UNLIMITED DURATION UNTIL YOU FINISH YOUR DATA UP TO THE LAST KB...
I will receive a small commission 😊
Dk my vote❤
Alibho my vote ❤❤❤❤🎉
Exactly this man mr kabambe sogolo lake ndilowala ali ngati mumene analili chilima kukhala wachiwili mpaka wafela pa uchiwili wake omwewo
My choice ,my vote , history is a best teacher
Daliso Kabambe our next President of Malawi
He was just exercising his right by defecting to UTM . I don’t blame him. DK my vote.
Ndachedwa kubwera pepani😂 DK my vote
That's my observation too
Dk our hope
My vote
Mcp taiyesa ndi dpp tiyeni tiyeseko utm tione ko zina😊
With Peter Ageing and Chakwera loosing populality Kabambe is at good position of become President of Malawi...
Haaa big lie even he is old we r still supporting apm
Mulungu atipasa atsongoleri wabwino amene ali osatchuka osadziwika ozichepesa kupatula anthu omwe akhala akuba ndalama za amalawi kwa nthawi yaitali Mulungu alowa mumtima ya anthu azasakha munthui osayembekezeka ndipo tizadabwa ngt mene tikudabwira lero enawa azagwa awa
Kabambe naye ali ndi mwayi woti anthu Atha kumukonda chifukwa cha umunthu wake womwe akuwonesa kwa amalawi
Ubwino ndiwoti onse omwe akusogolela zipani Zina tinawaziwa kale kulephela kwawo ndimwayi kwa kabambe kuwina
Mbava iyi kudzikonda 30 thousand milion.kumadzilipira
Inu RBM governor aliense amalandila 18 mita osati zomwe anakunamizanizo
His salary was 18 mita uyu governor wa Chakwera akulandilanso 18 mita vuto ndichani, Salary samakonza ndima governor
Chachikulu akhale osaopa olimba mutima kuti anthu ena asamupusise
your beating about yhe bush
Too much
With Peter Ageing and Chakwera loosing populality Kabambe is at good position of become President of Malawi...