KOMA AKWENI PATRICIA KALIATI NDIOKULA MTIMA MPAKA KUFIKA POYANKHURA IZI PAMENE ADAKALI KU NDENDE?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 26 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 60

  • @MacdonaldMuphuwa
    @MacdonaldMuphuwa 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Akweni more fire more fire ❤❤❤ I love masten Monday mukupita ku nyumba

  • @MarcyKamaga
    @MarcyKamaga 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    ambuye akudariseni mam ndipo ndikukupephererani kuti mukhare mwambuye akutetezeni pamene mkudutsa mnthawi zamayesero amen

  • @PelajiaKwitanda
    @PelajiaKwitanda 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Akweni what a courageous.woman you are ! Bravo.❤

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 2 นาทีที่ผ่านมา

    May God see mai kaliati through and give her victory.

  • @AbdulrazaqHussain
    @AbdulrazaqHussain 3 นาทีที่ผ่านมา

    That's really mother's love, n your children will continue to fight n praying for you on the outside.

  • @ErnestMangani
    @ErnestMangani 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    We pray for you mum

  • @faithKwakwasa
    @faithKwakwasa 55 นาทีที่ผ่านมา

    God will take care of you mama😍😍😍

  • @FlorencePhalula
    @FlorencePhalula 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    My Strong woman with wisdom
    Olo ndima ukulele bwanji kunja kumanga basi
    God is watching from a distance
    It is well

  • @ShamimaCosimo
    @ShamimaCosimo 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    We need strong mom like u we are together with u ❤

  • @ADAMSONGONDWE
    @ADAMSONGONDWE ชั่วโมงที่ผ่านมา

    We love you madam Patricia kaliat God be with you

  • @LumbaniPolowani
    @LumbaniPolowani 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Noble woman God protect you naba

  • @JamesChingombe-l4l
    @JamesChingombe-l4l 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Your courage even transform me we will win indeed

  • @JosephHill-fy1bb
    @JosephHill-fy1bb 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    You can create a page and employ the manager ..

  • @ElizabethMulinde
    @ElizabethMulinde ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Yesoooooo mum we are 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @AbdulrazaqHussain
    @AbdulrazaqHussain 43 วินาทีที่ผ่านมา

    This party's vision was to work with the youths, n us the youth we are awake n ready to transform our country

  • @RoseThindwa
    @RoseThindwa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    God will take care for u Mama

  • @PriscaMasala
    @PriscaMasala 7 นาทีที่ผ่านมา

    Allah bless u akweni

  • @DelipherMtekateka
    @DelipherMtekateka 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Chipululu simofera, mulungu simunthu

  • @ErnestChansa
    @ErnestChansa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zose izi ndi manganya ndi chikangawa chakwela ponyelela pa manganya ndi chakwela
    Mama kaliyati worry not mulungu aliko kumwamba
    Manganya ndichakwela ndi manyi aanthu alangika posachedwa apa UTM 🔥🔥🔥🔥🔥🔥moto moto🔥🔥🔥🔥🔥mutuluka mayi wanga

  • @ruthkundwe7448
    @ruthkundwe7448 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    God is there

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 23 นาทีที่ผ่านมา

    Expect this to happen mom poti muyenda mapazi a SKC zomwe amaziona SKC muziona ndipo pamenepo nchiyambi chabe,but zabwino zili kuseri kwa lawi lawiko inuyo Mulungu ali nanu akumenyerani nkhondo Yehova anthuwo sakuziwa zoti alumenyerani campaign

  • @ostinchadika600
    @ostinchadika600 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Cosiyasi & conscious are different. Can you try to read these before recording. I noted yesterday you were say mp is still investigating. It's malawi police (MP) en u need to say it in presentation even if it has been abbreviated 😢 in writing

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Osaopa .osafooka .osaopa..viva akweni

    • @MarcyKamaga
      @MarcyKamaga 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Amen

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Be strong woman

  • @DavidWayilesi
    @DavidWayilesi 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zingatheke bwanji kupanga Post zithu oti munthu analandidwa phone ndiye mukutiuza kuti akupanga post zinthu ndi apolice amene alindi phone yawowo. Amalawitu penapa munawoneka ngati mituyanu simagwila ntchito bwinobwino .nomwenu mumatiuzakuti analandidwa phone pano mukutiuza kuti akupanga post zinthu which is which

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iweyo ndiwabodza phon ayitenga kuti ukuwona ngati ose ndiopoyi aliposo anzelu akudziwa kt kunena bodza phon amalanda ofuna kuwaffuza apolcewo atiwuze

  • @JamesAlinafe
    @JamesAlinafe 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Be strong mama

  • @JuvenileDebwe-bv8ow
    @JuvenileDebwe-bv8ow 19 นาทีที่ผ่านมา

    The way I know this is the to the presidency

  • @CharlesMussa-x6c
    @CharlesMussa-x6c 32 นาทีที่ผ่านมา

    Akweni more fire moto kuto buuuuuuu❤

  • @JonathanLimunye
    @JonathanLimunye 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nthawi zambiri mu ground ma players amalimbana ndi player yekhayo amene ali chiopsezo. Simukudziwa chimene mukulimbana nacho, ndinu mafana enieni

  • @LamseyLazarous-dl5qd
    @LamseyLazarous-dl5qd 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mayi mwapanga history yanu muzizayankhula nsogolomo

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 3 นาทีที่ผ่านมา

    Dziko lomwe lasowa usogoleri wochokera kwa Mulungu zimakhal choncho munthu sungasiye kutumikira Mulungu kenako kuyamba zadziko lapansi Mulungu tithandizeni Ambuye chonde

  • @ZioneMkwanda-y6i
    @ZioneMkwanda-y6i 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Za bodza izi! Mai kaliyati Alibe foni pano mafoni awo Ali mmanja mwapolice, akupanga post ndi amene atenga maphone amai kaliyatiwo osati mai kaliyati wake up guys, akupitiliza kumupezera zinyau kt ampeze zifukwa nanga bwanji sakupanga VN kt timve mai awo amai kaliyatiwo. Manganya ndaamene akulemba izi ku Facebook kwa mai kaliyati satana manganya ndi gulu lake la chikangawa 😅😅😅

  • @FlorencePhalula
    @FlorencePhalula 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kunja kumaçha basi
    Only God has the final say on this matter

  • @MillyKachepa
    @MillyKachepa 31 นาทีที่ผ่านมา

    Koma mesa akut awalanda ma 4n awo nde akulembera 4n yandani

  • @WelingsLongwe
    @WelingsLongwe 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiwe waboza ukulemba ndiweyo munthu analandidwa phone azilemba bwanji uzipusisa ena

  • @hagayichiluwe
    @hagayichiluwe 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Izii ndiye zaziiiiiiiiiii makosana mwasowa zopanga post😂

  • @Majorleman
    @Majorleman ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akweni akuyidziwa zofooka za mcp ,paja a mcp tu mitu yawo siyimagwira ntchito chilichonse amapanga ndi mkwiyo nkhanza that's why azikhalila yomweyo

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤❤

  • @ToweraMaviyo-g4j
    @ToweraMaviyo-g4j 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mulungu akuthandizeni mama

  • @AlexBenjamin-z7i
    @AlexBenjamin-z7i 58 นาทีที่ผ่านมา

    Gys andale amsmanga mzandale izi

  • @BersonChidziwe-yu9jb
    @BersonChidziwe-yu9jb 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chemwali mulungu akuyang'anireni

  • @SolomonMatola
    @SolomonMatola 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiye zikutheka bwanji poti maphone anamulanda komweko

  • @PeterNyongolo
    @PeterNyongolo 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mcp yapenga nanu mukatuluka mung'alura zonse

  • @SaukaniMbiliyawanda-ur7zb
    @SaukaniMbiliyawanda-ur7zb 18 นาทีที่ผ่านมา

    Maloto Munthu odzikonda wa mtundu ujawu ofuna zawo zokha ziziyenda mkumati mudzatenga BOMA ayi tili Mmalawi momwemuno bola osadzakomoka

  • @sodochimangeniChimangeni2
    @sodochimangeniChimangeni2 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Osaopa osafoka ambuye Ali pambuyo panu

  • @stephenchavula1162
    @stephenchavula1162 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    How come, using a phone in a cell? This case is going no where kuzikola kwenikweni uku,cheap propaganda

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Muzipusisa anthu opusa amene skukufusayo ndichitsilu

  • @KumbukaniMandala-h2j
    @KumbukaniMandala-h2j 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Amadya ekha apa wayamba kupindula

  • @ConfessMhango
    @ConfessMhango 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Amakuopani zitsiru izi

  • @nyanguoipa6996
    @nyanguoipa6996 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Munthu analandidwa zotheka bwanji?

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akuipanga post ndiwe yemwe most iweyo pakufunika Kumanga chifukwa ukugwirisa ntchito FB yamwini . kaliyatiyo alibe phone pakalipano munthu alamangidwa phone tima landa

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Simumati anamulanda foni....😂

    • @ShamilahSaizi
      @ShamilahSaizi 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kodi inuo mukt chani nanu????

    • @GetrudeBanda-sd1yf
      @GetrudeBanda-sd1yf 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Mumati alandidwa phone ndie awapasa? Ok page ndi yaodi
      Kom
      ?
      Wa pho

  • @JamesChingombe-l4l
    @JamesChingombe-l4l 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Eee mama golidi amaenela mung'anjo to be purified mudutsa my pa u president po

  • @faithKwakwasa
    @faithKwakwasa 56 นาทีที่ผ่านมา

    God will take care of you mama😍😍😍

  • @EdwardSimbi-l5f
    @EdwardSimbi-l5f 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    We need strong mom like u we are together with u ❤