AMUNG'ALURASO MANGANYA NDIPO MUNTHU AKUZIONA UYU ZINA UMANGOONA WAZIYAMBA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 11 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 124

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 หลายเดือนก่อน +11

    Ng'alulayizeshoni at its best 😂😂

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x หลายเดือนก่อน +15

    Manganya ndiopusadi zadi Ndi Chakwerayo zonse nduzitsiru zichoke

  • @user-lp8wj3vq4x
    @user-lp8wj3vq4x หลายเดือนก่อน +12

    Sure DPP my vote

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz หลายเดือนก่อน +10

    Zitsiru za anthu iziiii chomwe akudziwa Iwo ndi kubaaa basiiiii mxiiiii

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 หลายเดือนก่อน +13

    Koma anthu takwiyatu 😅😅😅😅😂😂😂😂sitikunyengelera malankhulidwe

  • @Alicia-ns5ho
    @Alicia-ns5ho หลายเดือนก่อน +7

    Amanganya afera zaeni ajijilika kwambili,bola nnakakhara mbali ya utm anthu bwez atakulemekezani

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 หลายเดือนก่อน +10

    Apm ndi munthu wabwino lero anthu mukuona

  • @AubreyWilson-j8w
    @AubreyWilson-j8w หลายเดือนก่อน +9

    Ndipo live dyera manganya

  • @gracemaluwa4674
    @gracemaluwa4674 หลายเดือนก่อน +8

    Adad omwewo kuti waaaaa

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs หลายเดือนก่อน +7

    Zayambika Mesa 😂 😂😂😂 malawi pano idazindikira

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope หลายเดือนก่อน +7

    Ndinu ozindikira kwambiri

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w หลายเดือนก่อน +7

    Koma chikangawa chakwera zomwe amalankhula Anthu amanva.
    Mmm koma chikangawa unalakwadi kupha anthu aja. Pakuti nthawi nkachiphwisi , nthawi yanu ikudzanso mosakaika, musaiwale

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya หลายเดือนก่อน +1

      Ngati zamamva,omuzungulira ake ndiomwe amamudziwitsa....in short amamva kkkkk

  • @fosternyirenda-wo4eb
    @fosternyirenda-wo4eb หลายเดือนก่อน +9

    Oh!yes,kulankhula kwa mphamvu ndithu.am touched.

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i หลายเดือนก่อน +8

    Mau amphamvu kwambiri,ndipo eeee kulankhula Kwa nzeru

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 หลายเดือนก่อน +8

    Thanks bro

  • @francismungu7749
    @francismungu7749 หลายเดือนก่อน +2

    We need people like you brother. Thank you for massage

  • @user-uc6jk6pr9r
    @user-uc6jk6pr9r หลายเดือนก่อน +8

    Manganya ndi kape_ sadziwa chomwe akumayankhula

  • @ChrisjuZiyaya
    @ChrisjuZiyaya หลายเดือนก่อน +5

    Amambala awa akangoti achoka m'boma onse akonzeke wa ku maula prison

  • @HestingsZiba-d6k
    @HestingsZiba-d6k หลายเดือนก่อน +5

    Mawu mawu awa good message

  • @AnnieKwisanja
    @AnnieKwisanja หลายเดือนก่อน +3

    Ambuye timveleni mapemphero athu🙏

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 หลายเดือนก่อน +5

    Good massage my brother keep it up

  • @UnicekapachikaHanzwell-zz8te
    @UnicekapachikaHanzwell-zz8te หลายเดือนก่อน +4

    Nice point 🎉

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v หลายเดือนก่อน +8

    Ndipodi uku ndekuyakhula kuopa mulungu zoonadi peter muthalikaa sanatumeko munthu kukamusaka kunja koma iziii tikuzionazi ayi

    • @WilliamBandaWili
      @WilliamBandaWili หลายเดือนก่อน +1

      Koma boss mwala khula zikomo wakumva wamva mcp ilimumadzi bac

  • @MikeKanyaza-bm5tp
    @MikeKanyaza-bm5tp หลายเดือนก่อน +8

    I agree with you comrade

  • @user-co6sc8om5n
    @user-co6sc8om5n หลายเดือนก่อน +5

    Chakwera ndioipa

  • @victormaluwa6710
    @victormaluwa6710 หลายเดือนก่อน +2

    I like all you have said,,,, koma Peter Mutharika wakula it's time for the old man to enjoy his retirement.

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o 29 วันที่ผ่านมา

      Zoona akanasankha munthu wina bola

  • @user-lk8kj9zv6x
    @user-lk8kj9zv6x หลายเดือนก่อน +6

    Auzen

  • @PRECIOUSMKUTE
    @PRECIOUSMKUTE 26 วันที่ผ่านมา

    Kung'alura At Its Best 😊😊😊😊

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 29 วันที่ผ่านมา

    Respect one another is needed u r a grown up man amene ukumutukwana ndi kholo lamzako ngat iweyo ,kut naweso akupaseso udindo sungayendese

    • @user-hm9nc7lz6e
      @user-hm9nc7lz6e 28 วันที่ผ่านมา

      Mmmm kholo likakhala lopanda nzeru akutukanidwa ndi ana omwe

  • @HoseKatsekera
    @HoseKatsekera หลายเดือนก่อน +4

    muzen avetse ameneyo

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 หลายเดือนก่อน +4

    Ndipo ndizowona chisiru

  • @EdwardZuze-r7w
    @EdwardZuze-r7w 28 วันที่ผ่านมา

    Mr Ussi, izi za ndalezi mungoyaluka nazo, muli ndi ma source of income, zoti munkhoza kumasangalala ndi mabanja anu, tangosiyani zandalezi,

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm หลายเดือนก่อน +4

    Boma ili Malawi atopa nalo

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 19 วันที่ผ่านมา

    As Malawians, we have power to fire out this stupid president of MCP,
    Enough is enough , we don't like another mistake on 2025

  • @ThokoLungu-tq6pw
    @ThokoLungu-tq6pw หลายเดือนก่อน +3

    Ahahaa usi ndiwamadramatu 😂😂😂😂😂

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 หลายเดือนก่อน +4

    Ndiwe chewa ozindikira kwambiri

  • @LiyayaNyamula
    @LiyayaNyamula 19 วันที่ผ่านมา

    Zufunika anthu ngat inu big up

  • @EliasOdala
    @EliasOdala 29 วันที่ผ่านมา

    Big up comrade!

  • @RossanaMitha-tl9in
    @RossanaMitha-tl9in หลายเดือนก่อน +2

    Auzeni amwetsetse 🤗

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz หลายเดือนก่อน +4

    Usi ndi kape

  • @AnnaPhiri-b8t
    @AnnaPhiri-b8t 27 วันที่ผ่านมา

    Apm my vote

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 หลายเดือนก่อน +1

    Mposo Apm only hope for Malawians ❤❤❤❤❤

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน +2

    (Moses Kumkuyu+Mkaka+Chimwendo+Chakwera+Zikhale+Chithyola) ndi combination ya ufiti.

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c หลายเดือนก่อน

      Chikangawa crew

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w หลายเดือนก่อน +3

    Usi ni odwala nthawi ilionse apegelatu

  • @Gamazul
    @Gamazul หลายเดือนก่อน +1

    Ng'alulazetion

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto 28 วันที่ผ่านมา

    Very good❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-ld8gb9xm7v
    @user-ld8gb9xm7v 23 วันที่ผ่านมา

    Kuzitama ndi kupempha 😂😂😂😂 chitsilu manganya

  • @ErnestChansa
    @ErnestChansa 23 วันที่ผ่านมา

    Munthu woyipa kwambili manganya Wana panga zithu zopanda zeru zomwe waza panga regret 1 day manganya

  • @SamuelChiwere
    @SamuelChiwere หลายเดือนก่อน +2

    Ineso l was asked for myself kuti kodi why akumapita in working places kumakawafusa kuti what time what time, and my poor mind kuti Kodi if you're a father or a mother is it makes sense to ask your children what are going to eat while you. Parents you didn't having food to gives them. And Manganya was busy to toxic people what time did you starts to work how, by then yet workers they didn't getting their paid and even though ku Chipatalakoso medicine kulibekoso for me to be honest this was a full of Nonsense 😢

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c หลายเดือนก่อน

      Zoba manganya

    • @vincentmpighu1080
      @vincentmpighu1080 19 วันที่ผ่านมา

      Leembani mofatsa fn ndi yanu boss

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 26 วันที่ผ่านมา

    Manganya panyo pako chakwela maphwala akenso anthu opanda nzeru agalu amenewa mbunzi za anthu

  • @EllenChimera
    @EllenChimera 28 วันที่ผ่านมา

    Auzeni akang'wing'wi ndi chikangawa party

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 29 วันที่ผ่านมา

    Usatinamize sunavotere tonse alliance iwe unavotera dpp kuyambira kale

  • @ItaiKafunse
    @ItaiKafunse หลายเดือนก่อน +1

    Exactly manganya ndiye mbuzi yen yen

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 27 วันที่ผ่านมา

    Chikhalamba cha zaka 62 ku Immigration and mnyamata wazaka 84 ku DPP. KOMA ANTHU ENAWA AMAGANIZA ASANAYANKHULE? KUKHUTA NAPWIRI ETI?

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r 23 วันที่ผ่านมา

    Manganya chisilu alibe zelu fundo alije

  • @StellaCharmer
    @StellaCharmer หลายเดือนก่อน

    Naturally I'm shy to beg koma wina akuti iye ndiye amatha zopephapephazi ayi mwatchukatu bwana manga😂😂😂😂

  • @johnlameck8366
    @johnlameck8366 21 วันที่ผ่านมา

    Uyu amandiwaza koma sindidziwa kuti ndi ndani or ma vn ake ndingawapeze bwanji

  • @user-ol1hf7ru1v
    @user-ol1hf7ru1v 29 วันที่ผ่านมา

    Ndipo mcp ikadzaluza anthu ambiri adzadzipha okha ndithu

  • @lyiemax
    @lyiemax หลายเดือนก่อน

    Powerful talking ❤❤❤

  • @ThomasMlowoka
    @ThomasMlowoka หลายเดือนก่อน +1

    🔥🔥

  • @NizigiyimanaChantal-c2p
    @NizigiyimanaChantal-c2p หลายเดือนก่อน +1

    Azayya kupanyoooo awa

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 หลายเดือนก่อน

    Ndipo Bakili Muluzi channel sikumvekanso panopa.
    Inquiry report ya kuchikangawa kuli zii.

  • @user-xo8ms5wh2s
    @user-xo8ms5wh2s หลายเดือนก่อน

    Mulikuti tikuoneni timafuna azibambo ngati inu oyakhula poyera panda matha

  • @user-rz8qp8tj8e
    @user-rz8qp8tj8e หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂koma ku Malawi anthu anatope yooo for give us Peter muthalika 🙏🙏🙏

  • @DoreenAllan-tg1dz
    @DoreenAllan-tg1dz หลายเดือนก่อน

    Mawu amphavu 👏

  • @DanielJuwawo
    @DanielJuwawo หลายเดือนก่อน

    Ndi amene adatumikira kupha chilima

  • @JonathanMtambo-w6e
    @JonathanMtambo-w6e หลายเดือนก่อน +1

    Things. are becoming. much. worse now

  • @CharlesChisoso2
    @CharlesChisoso2 หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂Koma muphana

  • @OmarBasheer-v7c
    @OmarBasheer-v7c หลายเดือนก่อน +1

    Ichi nde chilungamo mopanda kupyathila

  • @CHIWSABINYAMBOSE
    @CHIWSABINYAMBOSE หลายเดือนก่อน

    Kupandaso nzeru awa zawo ndi drama

  • @user-xo8ms5wh2s
    @user-xo8ms5wh2s หลายเดือนก่อน

    Ndipo usi ndichitsiru galu

  • @Christopher-xc2ey
    @Christopher-xc2ey 20 วันที่ผ่านมา

    True mmmmm

  • @AhamadAsina
    @AhamadAsina หลายเดือนก่อน

    Mwamuza.bwino.manganyayo.ndigalu.kwambili.waiwala.zonse.akapa GA.namanena.mmasewelo.ake.aja.ndichisilu.kwambuli.ndipo.alibe.nzelu.manganya afuna.kufa.basi

  • @WisdomMaseko-fi5sv
    @WisdomMaseko-fi5sv หลายเดือนก่อน +1

    Wina wadya za adadi

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c หลายเดือนก่อน +1

      Akulankhula chilungamo koma ngat wadya mwai wake

  • @gersommalama
    @gersommalama หลายเดือนก่อน

    Nsanje suudolo ayi.

  • @KulinjiGoodsonnkhoma-o9w
    @KulinjiGoodsonnkhoma-o9w หลายเดือนก่อน

    😊

  • @shenwaahabdulhakim
    @shenwaahabdulhakim หลายเดือนก่อน

    Ka Usi ndikachitsilu ndi chakwera yemweyo akungofunika kuwaponya miyala

  • @FrankChimpango
    @FrankChimpango หลายเดือนก่อน

    Eeeee anthu amalusa kumalawi kwaipa🙌

  • @juliochiwalo
    @juliochiwalo หลายเดือนก่อน

    A chakwera ndi boma lanu la mcp mukuona koma mmene zinthu zilili mdzikoli anthu ndi okwiyadi kwambiri do you reason

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika หลายเดือนก่อน +1

    Eya zoona

  • @ChrisjuZiyaya
    @ChrisjuZiyaya หลายเดือนก่อน

    To be honest Amalawi ndalama zilipo koma zikungothera mmatumba mwa anthu MCP ndiutsogoleri wawo aliyese akudziwa.

  • @user-gm9xj1wc2m
    @user-gm9xj1wc2m หลายเดือนก่อน

    Fact up

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u หลายเดือนก่อน

    Usi omasanduka sanduka kukhala mkazi mpena akhale mamuna

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 หลายเดือนก่อน

    Mau mau ndithu chakwera usamale uli pa ngozi mbuzi abusa akusi kwa nyanja

  • @LiyayaNyamula-j3b
    @LiyayaNyamula-j3b หลายเดือนก่อน

    Koma dzikoli likupita kuti abale zuchitikaz izi mulungu akuon ndili

  • @NkosDysonNkosDyson
    @NkosDysonNkosDyson หลายเดือนก่อน

    Kuyankulatu mawu athanzitu anthu mudyadi katatu patsiku eti kkkk

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no หลายเดือนก่อน

    Anthu mukusapotera zopusazi , abwande adapenga yawa , inu mwapangapo chian pachitukuko chadziko

  • @OssmanAbubaker-t2i
    @OssmanAbubaker-t2i หลายเดือนก่อน

    Zoonadi brother simukunama MCP zonse ndi mbunzi anthu okupha

  • @BrunoChakukuma
    @BrunoChakukuma หลายเดือนก่อน

    Mwembe nganipepe😂

  • @IssahAluba
    @IssahAluba หลายเดือนก่อน

    😅😅😅 akuti ndine Dolo pa zopephapepha iiih

  • @MikeMwale-bw1xw
    @MikeMwale-bw1xw หลายเดือนก่อน

    Inuso za Peter zo zisiyeni naonso zidawavuta kale tikufuna tione Zina.A peter mphamvu zolamura alibe Pali tiwanthu tina tikubisala kumbuyo kwa peter sitikufunaso.

    • @samdiverson9733
      @samdiverson9733 หลายเดือนก่อน +1

      Iwe wa mphamvu chakwera akuchitapo chani?

  • @ChitumbukanaLoraine
    @ChitumbukanaLoraine หลายเดือนก่อน

    Kwawachi?

  • @ChitumbukanaLoraine
    @ChitumbukanaLoraine หลายเดือนก่อน

    Ka mbalisha wakuphalazga?

  • @VeroMaster-lo1mu
    @VeroMaster-lo1mu หลายเดือนก่อน

    Kudalila kupepha or manyazi

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili หลายเดือนก่อน

    Nkachitsiru kamanganya

  • @YamikanChirwa
    @YamikanChirwa หลายเดือนก่อน

    Auzen ave

  • @ClaudiaarmandoMafunga
    @ClaudiaarmandoMafunga หลายเดือนก่อน

    Zoona koma

  • @ChrisyMbewe
    @ChrisyMbewe หลายเดือนก่อน

    Zopanda.zelu.manganya.

  • @EstherBonga
    @EstherBonga หลายเดือนก่อน

    Mawu

  • @StechelectronicsRepair-qh5jl
    @StechelectronicsRepair-qh5jl หลายเดือนก่อน

    Osaopa