MPINGO WA BANGWE UKUTI UDAKAFALITSABE ZIKHULUPILIRO SDA. ATSUTSA MALIPOTI AMBIRI.

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 4 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 53

  • @VeraChirwa-c5n
    @VeraChirwa-c5n 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bangwe anakonza 🙌🙌

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 3 วันที่ผ่านมา +4

    Log ya seventh day Adventist sisitha,ndipo sidzasitha,ndi omega ndi alefa ngati president wa mpingo angachite, zimenezo,akhristu muli ndi mphabvu,yoletsa,tisatsocheletsedwe,ndi aliyese pomwe choonadi tikuchidziwa.choonadi,chidzakupulumutsani,ine kungoona ku mpingo kuli ine kazanga,ndi ana anga tidzidzapephela, nyumba mwathu.khalani,ndi chikhulupililo mwa inu nokha,log ya chikasu si log ya SDA.khalani,ndi log yeniyeni, SDA ndi today tomorrow for ever.si,sitha,log,ndi zochitika,ndi zozo.bangwe,tidzayiyendela,tipephele nanu Amen.

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 2 วันที่ผ่านมา

    Congratulations My Church members

  • @VeraChirwa-c5n
    @VeraChirwa-c5n 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    The best way akanangoyambitsadi wao kkkkkkkkkk nkusithanso dzina

  • @beinhardkausiwa7107
    @beinhardkausiwa7107 วันที่ผ่านมา +1

    Inuyo mukukakamilako chani?osachoka bwanji mukayambitse wanu wachoonadiwo?

  • @TenganiObety
    @TenganiObety 3 วันที่ผ่านมา +2

    Yehova akulimbikitseni

  • @BlendahChikopa
    @BlendahChikopa 3 วันที่ผ่านมา +2

    Bangwe SDA is doing her best. Mdima umadana kuwala.

  • @bangwesdachurch
    @bangwesdachurch 3 วันที่ผ่านมา +2

    IN JESUS CHRIST WE TRUST

  • @VeraChirwa-c5n
    @VeraChirwa-c5n 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zinazi mmmmm kumaoneka ngati angelo koma zigololo zosayamba aaaaaaa

  • @malapuramnkosi
    @malapuramnkosi 3 วันที่ผ่านมา +1

    Odala Iwo imwe azayima chiyimile osasutha, pa mau Ake. Imwe Yohova ndiye m busa wao

  • @malapuramnkosi
    @malapuramnkosi 3 วันที่ผ่านมา +1

    God is with us

  • @malapuramnkosi
    @malapuramnkosi 3 วันที่ผ่านมา +1

    Mwayamba kulowetsa ziphuzitso zakubabulo mchurch chifukwa Cha I, mwina A pulezideti anthu ampingo inu, nanutso za kudya zosekelesa za k u abulo ,mulungu akuoneni inu, ana anjokaq

  • @malapuramnkosi
    @malapuramnkosi 3 วันที่ผ่านมา +1

    Akuthawa kulalikila za uthenga wachirombo, ndi chinjoka tiyeni tikafela pa dzina kavYohova mulungu wanthu, tizaka ziphuzitso ndi zakudya za chilendo ngati Daniel ku babulo

  • @malapuramnkosi
    @malapuramnkosi 3 วันที่ผ่านมา +1

    Wanthu mulungu mulungu ndiyomweyi dzulo, lero ndi mawa, ndipo sazatsitha mpaka kale kale

  • @malapuramnkosi
    @malapuramnkosi 3 วันที่ผ่านมา +1

    Tiyenela kuvala ngeti ana a mulungu osati ngati jezebele

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 3 วันที่ผ่านมา +1

    Malamulo a mpesa aliyense akuwadziwa moveka bwino nde ngati pali wina akupanga dzosemphana ameneo si wa mpesa. Ndicifukwa manganya amuchotsa ku utm chifukwa amaphwanya malamulo a utm.

  • @FefieTenisha-du7ge
    @FefieTenisha-du7ge 3 วันที่ผ่านมา +1

    SDA is trying to evolve for the better...these conflicts will sanitize their religion...

  • @SambulaniMaliki
    @SambulaniMaliki 3 วันที่ผ่านมา +2

    Musalole kutsata ziphunzitso zachilendo, amai sakuloledwa kulalikira pa guwa molingana ndi bible or atakuchosani mu kaundula wao sangakwanitse kukuchosani mbuku lakumwamba musadabwe tili mmatsiku otsiriza, simuli nokha ambuye ali nanu musamapembeze zofuna munthu opani Yehova mverani iye sungani malamulo ake

    • @VeraChirwa-c5n
      @VeraChirwa-c5n 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Mukuti ndinu achoonadi koma zigololo zili thoooooo mmmmm very shame

  • @LivielMabvuto
    @LivielMabvuto 3 วันที่ผ่านมา

    Ndinkona ndimapemphera pandekha nkhan zake zimenezi logo ya mtanda ozondoka wo ndiwa sataniki mot anthunu muli mtulobe mpingo wu unagulitsidwa ku midima mnthawi ya amfune president more fire bangwe

  • @charitymhone9983
    @charitymhone9983 2 วันที่ผ่านมา

    Inu abangwe amani njii pamaso pa Yehova olo akuchosen zilbe ntchito..Abweletsa zonyasa zaku babulo ndikusintha log ndi President watsopanoyo TY nyirenda paja anakwakwazidwa kale ali ku satanic ndi bwenz la papa ndi chakwera😮😮

  • @malapuramnkosi
    @malapuramnkosi 3 วันที่ผ่านมา +1

    Mwayamba kale kale kukayima mmisokhano ya ndale ndopa mene tinaziwa kt mpingo wapatikana ndi boma, ndinu osirhasitha ife ayi, ndembe Ya Angelo atatu, yiyime chiyimile

  • @malapuramnkosi
    @malapuramnkosi 3 วันที่ผ่านมา +1

    Logo ya moto mkabweze kumene mnakate nga chonde kampaseni, mwini wa logo iyo, mka m uze ife ndfe ana a Yohova mulungu osati ake

  • @ChibaleKunsamale-si8qf
    @ChibaleKunsamale-si8qf 3 วันที่ผ่านมา +2

    Kwangotalika ndimafuna zikapephela kumeneko poti dima umadana ndi kuwala

    • @EmmanuellKajawa
      @EmmanuellKajawa 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Ndipo zoona atsogo

  • @NormanChilewani
    @NormanChilewani ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Log sidzapulumutsa munthu

  • @Mavisbunny346
    @Mavisbunny346 4 วันที่ผ่านมา +5

    Following

  • @PromisNtaba
    @PromisNtaba 3 วันที่ผ่านมา +1

    Kodi logo mwasintha chifukwa chani nanga chiyambile cha mpingo wa seventh day logo mwasintha kangati nanga akhristu monga mudawadziwitsa awuzeni anthu kuti mpingo mudagulitsa chilungamo ndichofunika mpingo wa bangwe uyime pawokha basi

  • @stanleymabuku9749
    @stanleymabuku9749 3 วันที่ผ่านมา

    Camera simajambula bwino video,

  • @GeorgeLipenga
    @GeorgeLipenga 4 วันที่ผ่านมา +3

    Mmasiku otsiliza ambiri adzataya chilungamo ndikutsata zina, koma inu MULUNGU NDIOPA MBANA OSACHEUKA MASO PATSOGOLO NDI CHILUNGAMO CHANU MULUNGU ALI NANU. NO MORE turning BACK

  • @lewisdicksonmlozi130
    @lewisdicksonmlozi130 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndipo ine sindikumva kukuveka phokoso kwambili pansi pansipo

  • @mphatsolupiabanda6910
    @mphatsolupiabanda6910 3 วันที่ผ่านมา +1

    Ndimakhulupira kuti padziko timakhala komanso zovala ndizichito chito zambiri nzaoipayo zimafunikira chikhulupiro cha iwe mwini ndikulimbika mmapembedzedwe ako kuti ukapulumuke otherwise the rest nzosala..nde tisadane kamba ka mipingo sidzitipindulira kathu

  • @mphatsonyirenda7981
    @mphatsonyirenda7981 2 วันที่ผ่านมา

    Kusowa kwamafuso kuchoka kwa atolankhan zikuonetseratu kuti zithu sizili bwino

  • @NormanChilewani
    @NormanChilewani ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zovuta masiku otsiriza

  • @JeremiahHunga
    @JeremiahHunga 3 วันที่ผ่านมา +1

    Nanenso ndifunse m'mene mwachotsedwera mukharabe mukugwiritsira ntchito mabuku a SDA monga totaled, nyimbo, ndi mabuku a Spirit of Prophecy?

    • @MelitaFrancisco-g7u
      @MelitaFrancisco-g7u 3 วันที่ผ่านมา +2

      We are Seventh day Adventist from the beginning of the church we will not change,
      Conference yatichosa pa maso pa dziko lapansi kma Mulungu sanatichose Tizakhalabe ana ake mpaka kale kale

  • @thokokaluluma
    @thokokaluluma 3 วันที่ผ่านมา +1

    Muli busy kupanga za mpingo osapanga za chipulumutso chanu bwanji? Chotani machimo anu dziyeretseni

  • @MtabeniMbuziyadula
    @MtabeniMbuziyadula 4 วันที่ผ่านมา

    Panopa maudindo a busa onse a SDA church ya mtanda muli ziwanda. Palibe mzimu oyera. Ufumu umodzi suukirana. Mmodzi Ali pa choipa. Iwe SDA wa makono taona chakuzungulira ndi chani kuopa ukuyenda mu njira yotakata

    • @tadalapatrick5914
      @tadalapatrick5914 3 วันที่ผ่านมา

      Ubwino wake anayambisa kuukila ndi white kuyambisa forum ya SDA nothing knew sometimes look back where is from

  • @malapuramnkosi
    @malapuramnkosi 3 วันที่ผ่านมา

    Mchose tose ,mwayamba kumene, mkuopa zomwe mnatumidwa kumisokhano yanu yaku babulo kt mchose ose imwe sakugwilidzana Nafe, ndiye mwayamba kuchotsa, chisani mthe tose, tizikapephelela ku ntchile, ena Tina yamba kale, smbiri atisatila, sitizayima kuziphunzitso za zidziko .

  • @JeremiahHunga
    @JeremiahHunga 3 วันที่ผ่านมา

    😂😂 koma sindikuvetsa Bangwe help ndamva dzoti azimai tsaloredwa kulalikira koma ndikumva mau kuyimba kwaazima kodi kuyimba it's not park of ulaliki ? Mwina ndine sindikumvetsa akati azimai akhare chete

    • @MelitaFrancisco-g7u
      @MelitaFrancisco-g7u 3 วันที่ผ่านมา

      Kuimba ndi kulalika ndi zithu zosiyana though zonse zimapereka uthenga
      But the issue is kulalikira pa pulpit and even mzimayi kukhala mbusa

    • @JeremiahHunga
      @JeremiahHunga 2 วันที่ผ่านมา

      @MelitaFrancisco-g7u koma Bible limati akhare chete ngati ali ndimafunso akuyenera kukafunsa amuna awo ndiye you don't see that you contradict yourself because there is no different preaching and singing it's all about preaching

    • @charitymhone9983
      @charitymhone9983 2 วันที่ผ่านมา

      Mkazi sangakhale mubusa Seven ya Mtanda ndi imene imachita zimenezo anazibweletsa kuchoka ku Babylon kwa papa

  • @Bbbbwesgtcjoug
    @Bbbbwesgtcjoug 4 วันที่ผ่านมา

    Or mutachotsa koma mu buku la kumwamba sumungawachotse zonse zomwe akunenazo ndi zowona koma mpingo omwe wasintha logo zimenezo sizilondola

  • @thomphalavi5027
    @thomphalavi5027 3 วันที่ผ่านมา

    Tiyeni tidzichotsana pansi pano koma ku Mwamba

  • @JosephMedson-q1l
    @JosephMedson-q1l 3 วันที่ผ่านมา +1

    Ya mtanda mwalowa chipwilikiti. Nde muchosa mipingo ingati??? Pangani manyazi. Nanga mamini mu church akufunamo chani?

    • @MelitaFrancisco-g7u
      @MelitaFrancisco-g7u 3 วันที่ผ่านมา

      Eti eti,

    • @EmmanuellKajawa
      @EmmanuellKajawa 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Ndipo zochititsa manyazi mmene zimavalidwa mmmmm

    • @JosephMedson-q1l
      @JosephMedson-q1l 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Ukadakhala pafupi akanandilandila bas, ndiopa ndani.

  • @ElizaMadiPhiri
    @ElizaMadiPhiri 2 วันที่ผ่านมา

    Following