Namalo ba with all humility accept you were nasty. You had just too many shortfalls and nasty happenings. Namalomba accept you had just too many nasty things gs as if you do not know, the moment you want to run away from your own bad things you will never see the Malawian vote. Be warned
Namalomba akuyang'anisisa Carthy mauridi kkkkk III koma pomwe Pari mnthu wamwamuna ndi nkazi ndipovuta kkkkk Koma Shadreck Namalomba you are the best and strong to DPP 😂😂😂.l like your answers
Brian always I follow you guys, but what Namalomba said it's true, I don't have more to say but the Truth is MCP it's useless ended.
DPP woyeeeee! 2025 professor muboma
No matter what people say, DPP is the next government come 2025. APM pfeeeeeeeeeeee (in Zim terms)
Never if u will not alone but agogo out
Apm my vote
Ichi ndi chibomaaaaa bravo namaloma
Namalomba umakwana❤
What was the root cause 0f demonstrations in dpp govt if their leadership was people centered?
Namalomba ndikatundu koma ndaseka eee😂😂
Ntchito zinapezakopo liti ku Malawi guys.. Coz for 30 yrs now we hv been struggling while few of u leaders are getting rich.
Koma Dpp inalephela kukonza misewu...Chilungamo amachisiya bwanji anamalombawo?
Apm my vote with my family
Namalomba ndi katundu
More 🔥🔥🔥 fire😅😅😅 my vote
Brian 😂😂😂you are the best
Kkkkkkkkkkkkkkk mmandifunsilanji nangaaa😂😂😂😂😂😂
Koma ma lubino musiya kuwapha? Brian ndifunsileko funso limeneli. Coz ndili ndi m'bale wanga wa chalubino amati dpp samayifuna ayi.
Ayi akanakhala kuti ma albino amaphedwa ndi Dpp wina atamqngidwa panopa nkhai imene ija siyaing'ono. Koma inu muyembekezele kulowa kundende pokupha chilima
Uthandzra ngat ndan?
Ku malawi ndikokoma kkkkkk
Tikufuna ndife anthu osa ti Peter,malingandi mavuto omwe amalawi akumana nawo,enawo ndi adyela
Funso lina tikhalire kuphana kodi?????
Never DPP again in malawi
Good job
Where was Mr Ndevu Zamwayi
Kkkkkkkk, Namalomba wandisekesa, ".........kulimbana nibouncer uyu.........?" Kkkkkkkkkkkk
Voto samatha kuyankha mafuso namalomba koma kupwa ntima
Namalomba umakwana
Sopuni Phiri army commander anali wakuti. Osamalankhula ngati munthu ochenjèra. Munkapha anthu inu
In short we call him Namalo, thumba la mchenga onyowa😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊Moreeeeeeeeeee fireeeeeeeeeeeeeeee👍👍
The 50+1 will be crucial no party will make it alone
Munatuluka chifukwa cha arrogance.
This is arrogance.
Mfondo zopepera simulowaso muona
The same old politics these people are just useless Malawi will never develop, same mind and same thinking capacity aaaa
Mumamenya anthu Inu ,kupha Issa njaunju ndi Robert chasowa. Munapha anthu 22 kumpoto Nthawi ya mademo Inu
Zonsezi ziri ndiumboni ogwirika
A Brian nanunso mumabalalika kwambiri.Inuyo ngati mukudziwa kuti nkhani ya Paul Gadama ili ku court bwanji mumamufusa Namalomba kuti ayankhulepo?
Namalomba chitsiru cha munthu, wayiwala muja munkatibula anthu. Boma sitikusintha.
Zako izo ifetizinda boma
Uziti xiukusintha momwe ukuyankhuliramo ulipo ndi ndani ???
Afunseni kuti amalawi azatetezedwa za ana adadi zija zidzatha
Ndadzikonda kwambiri fundo make kuluyi
Ndipotuu zooona ikulowa diii mbona
😂😂😂😂😂😂😂 DPP in my vein
Sakuyankha funso. Nchani chomwe aMalawi angafune kubwekera ku DPP. ZZoipa za DPP zomwe ankachita adzachita bwanji
Kunene zoona dpp kupha malobino zasiyeni ndithu
Oyamba ndi zikhale ngoma wa sokha nawo ine nda ingalura basi
Abanda anvetseni anamalomba vuto tinali ife atione zina apapa taphunzila ndipo ndithandize kulapa anamalomba tachimina ndi mcp
😂😂😂
Km shadiliki😊
Boma APM
achithina nimafunso chiyankha za panti yawakazi ake iyu
voti poti numbuli kom dpp adzayivotele nichitsulu
Mwalapa ndekut chan koma mafunso enawa
Choka namalomba. .mbava.
Mudzamalize malubino dpp ndiyoipa
Osawasokoneka zitukuko ndiza boma siza dpp
❤❤kkk
namalomba utisokoas tachoka apa
Zoona namalomba
Waboza uyu
Koma brian
DPP WOOOYEEEEE 2025 BOMA
Apm boma 2025
Namalo ba with all humility accept you were nasty. You had just too many shortfalls and nasty happenings. Namalomba accept you had just too many nasty things gs as if you do not know, the moment you want to run away from your own bad things you will never see the Malawian vote. Be warned
chabodza ichi
Mbava za DPP izi
Namalomba amuchosepo pamupandopo Samardziwa kuyankhulila chipani
Namalomba ukali wako
Namalomba akuyang'anisisa Carthy mauridi kkkkk III koma pomwe Pari mnthu wamwamuna ndi nkazi ndipovuta kkkkk
Koma Shadreck Namalomba you are the best and strong to DPP 😂😂😂.l like your answers
😂😂😂😂😂
Namalomba ndikape weniweni
Useless DPP
Malawians of sound minds will never never vote for dpp
Amayi ndi abambo ako ndiomwe sadzavota zofoila basiioi
Iwe sioyippa koma iwe?
Nkhaniyo njoona
But vote for who?
Apm my vote