This episode deserves an award for sure. Big up guys. You are improving in each episode. I'm casting my flowers to the whole crew starting from the camera handlers 🎉🔥💯
Nkhani ya kobwe yokhayo ngakhale ine nditha kulowa fast yosafunatu until khobwe athere2 mnyumba 😂😂. #pat#Gan# Ngozo achita kuthawira2 serie yonse osaonekako kuzemba ndiwo khobwe.❤much love from South Africa guys mumatha.
Tili apaaaaaa mesa Cheteeeee kudikilira kut Gani nanga Patricia and Mtebede aza zanji osaiwala Langwani NGAUZOOOOOOOO🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥USAUVER TO THE WORLD 🌍🌎
Ma fans a Ganizani tilikuti
pano hahahahh
🤙
We here
Ife pano amathu
Ife Pano 😂
Let's gather here for ganizani 🔥🔥🔥🔥this dude is so protective 🙌
Ndimunthu wamkulu
What do you mean protective kapena you wanted to say Proactive??
🤣🤣🤣🤣🤣
Super mumakwana
Amene timayembekezera kut hyphen amupezelera mkazi wake ndi Mashasi tikweze manja😂😂😂😂😂😂😂😂
Ndipo ine pano thought ali munyumba momo
😊
Kkkkk koma Gani guys wandikumbutsa kale ndithu .... Mpaka Tonde .... Nyooo
Inde ife tikampanga zimenezo 😂😂
Sangie ndi vibe kwambiri🙌🙌🙌. Sungaonere part yoti pali sangie munthu osasekai. Ahhhh bigup Sangie. Ahhh ndakutaira mitengo yonse🙌🙌🙌🙌
🙌🙌🙌🤸🤸🤸
Ndipo chomwe chandisangalatsa pa Usauver ndichoti yayambira pomwe inathera 5 ndipo muzitero guys keep high high
🎉
Nane ndazikonda
Kkkkkkk guys mmatha
Patricia and Ganizan acting ili good heavy, big up guys🙏
Kkkkkkkk koma ziboo amixsa boo m,tchana
Best comedy ever 🎉 koma muja anapangira MPUGWEPU kuopseza a shadow asadzabwerezeso fukwa ineso ndnachita nawo mantha 😂😂😂😂
Aaaaa ndiwausilu amene uja bwanji ,nanetu ndinazizimuka kkkkkkkkk!
😂😂😂😂😂😂
Atha kukhaladi sing'anga weniweni. Zizimba
Ndipo anatutumusa gulu😂
Mzimu unathawamo nane hahahaha
Ganizani ndi actor mbambane mmmmmm uyu anakonza
This episode deserves an award for sure. Big up guys. You are improving in each episode. I'm casting my flowers to the whole crew starting from the camera handlers 🎉🔥💯
Ine Gani amandiwaza😂😂😂. He is so calm koma zimayankhulidwazo🙌🙌
Ganizani akhale ambassador # take care for young girls
Kma sangie🤣🤣🙌 nde it's the song for me and I like ganizani too, he is a natural
Iyi nde best ever eeh yachuluka fans bwino....
Nice, good camera balancing, nice camera angles, amathu amatha, nice effort.....
Emmie ya sugar Mamie akuyitha, sangie is just the best, Gani is very natural excellent. Keep it up guys and kamwana kaja kakuitha heavy
Keep it up guys camera kuposa tv ya bomatu koma ganizani machine ❤
I just love this episode 😍, hyphen adzafa ndi BP tu akangodziwa🤣🤣🤣
Amangozipezera mavuto okha okha..kk
Km Patricia wandsekesa pakat pa usiku ndipo ndmangobwerez pamodz pompo ' akaxi awo amenewo, akazi awo atsopano, akuziwan nd matious, 🤣🤣🤣🤣 nsaname keep the fire burning, moto kuti 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Kandiwaza kameneka😂😂😂😂😂😂
Coming every Friday to check for next episode to find nothing is boring 😭.
Koma Patricia ati muyende bwino ndikudziwana kwanu🤣🤣🤣🤣🤣
zipongwe🤣🤣
Gwamabodza Patr
😂😂😂😂ndipo Patricia iih
😅😅ndpo pat mabodza
Kkkk akuti tonde nyooo koma gani 😂😂 big up guys
😂
Amashas asalapang ono kuti onse akome ku den kwangozo ayambazii kkkk
takoma tonse..., in Ngozo's Voice
I saw Ganizani at Kamuzu stadium. Dazi lija ndizazenizeni eti, ndimaona ngati ndimu usauver mokhamu
😂😂😂😂😂
Uli ndi mwano adha
Kķk
Mucheza bwanji koma?😂😂
Mashasii eee mashasiii😂😂😂
Keep the fire burning magaye🤗
And the song at the end is so nice,simungatuluse
I like it too
I see great creativity in our movie industry in coming two years 🔥🔥💪
Patricia n Ganizani eeee u pipo😂😂,,,,, but the song hits so hard in my heart😢😢
Nkhani ya kobwe yokhayo ngakhale ine nditha kulowa fast yosafunatu until khobwe athere2 mnyumba 😂😂. #pat#Gan# Ngozo achita kuthawira2 serie yonse osaonekako kuzemba ndiwo khobwe.❤much love from South Africa guys mumatha.
Tonde.... Nyooooo..... You have reminded our childhood😂😂😂😂😂
Kma a gani makwana much love from phweya's family
Wow 🎉🎉 sangie 🔥🔥🔥🔥
We miss Ngozo please
Koma sangre 😂😂😂 ndiwe wamabodza😂😂😂😂😂 applause for ganizani🎉🎉🎉
Am waiting patently am I really need to see this
Anthu inuy mukukita bwino nsaname much love you guys ❤
wow this is amazing
Ganizan you're now my favorite actor 🔥🔥🔥🔥
Kkkkkk tonde nyooo😂😂😂😂😅
Oyimiliraaa kkkkk eeeh adandidzidzimutsa manja Kuti gwiiii lol 😂
You never disappoint, keep it up!!
Nice guys,,today's episode was dope!!!!! Everyone was at high note,,, kuyambira wa Camera
😅😅😅 kma Gani,Tonde nyooo
Akt uzngt nyoooo😂usauver❤
Khobweyo akupeza akukudikirani kkkkkkkk
Komatu kamkaz ka hyphen sikanachenjele bwno😂😂😂
Sangie eeh iweyo Ai fenkis 🙌🤣🤣
Tili apaaaaaa mesa
Cheteeeee kudikilira kut Gani nanga Patricia and Mtebede aza zanji osaiwala Langwani NGAUZOOOOOOOO🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥USAUVER TO THE WORLD 🌍🌎
Very nice work guy's 👏
Kkkkkk koma ndee mulizipongwe😮😮😮😮😮😮😊😊😊😂😂
iyiy yzpangidwa premier pa ma tv kumalawi kuno zinangoyamba mwachibwana kma ❤❤❤
Kumakuwaaa 😅😅😅😅 Tonde .... nyoooo😅😅😅😅
Akazi a new one wa eh 😂
Nah man 😂😂😂 Sangie is too good🔥🙌
Waiting patiently 🎉
😂😂😂😂😂 kma Gan adha amakhala serious
Patricia will always be my favorite,she spices the show❤
shaaaaaaaaaaaa ndikuona kutalikatu eeeeeeeeeeeeeee
Tonde! Nyoooo😂
Ndee kuyankhatu eti ndakufusa maganizo ako evekere tonde nyooooo😂😂😂😂😂
Ili bho 👍
New follower 😄😄
Kmatu mashas 😂🎉🎉 wateraaaa😂
Waiting mwantintiii
😂😂😂😂 ati tonde uziti nyooo koma guys ndaseka. Gani ndi zina zake
Iiiiih Sangie iweyo ndi vibe❤🎉😂😂😂
Patiently waiting
Sekulu my boi .. kukonda zinthu
Gan my G✌️🔥🔥🔥
😂😅😂 and I quote dzulo dzana lero kumangolangizana chinzake chabwanji agani
Kma Patricia upole moto🔥🔥🔥🔥🔥 zoona nzako kumunena choncho
Ntonde nyooo! 🤣🤣🤣🤣
❤❤❤ sangie mundiitane ku ukwati pa wife material paja ndendende maturity yake ya mayi wa ana folotu scene iyiyi ndi yako basi big up
Kma Gani ndi katundu 🔥🔥
Gani wasandukatu akomesi😂
This episode was dope eeeh, guys mumatha inuyo
Getting hotter and hotter
Emmie umatha big up sis❤
Nyoooo😂😂😂
Tonde!! Nyoo!! 😂😂😂mwadza guys mukupanga zochitika guys kkk
Gani more fire watikumbutsa yakale kkkk
Sangie ndwe Dolo aseh❤😅😂😂
Tikudikilatu 🎉🎉🎉
A Gani next episode muwapephe alamu anu Juzi lanyowani
Keep it up!🔥
😅😅😅😅 Tonde nyoooo aaaaaa Ganiii
Iyiyi koma izituluka every 3 days ❤
It's always Sangie and the vibes she gives 😊😊😊
😂😂😂,you guys are the best
Gani simply man of the moment ❤
Kudos maguy ❤
Waiting 😊
😂😂😂aaaa Gani mpaka nyooooo
Nyoooo nyoooo😅😂😂😂
Aganizan amapanga zofoira Koma zibwana sama zifuna 😃😂😅
The song at the end it's giving ❤
I like the flow guyz hahaaaa
komano windows xp zamukhudza chani.. lol. Great job akulu akulu
Sangie😂🔥ai zikomo
Sangie ndi vibe❤
The nyoo vibe reminds me kalekale ndili mwana
The best mukauzane😂😂
Guys episode iyiyi nde mwayipambanitsa big up
Eeeeeh shoulder to shoulder 🤣🤣