Apostle misheck you have the message keep up the good work. Good understanding its vital than memorizing. You are doing good work Mr misheck you really understand may the good Lord bless you and give you wisdom
Muchenjeletu bwino amisheki kuwelenga mwaphuma kapena akuchemeleleni bible ndi losusana ndipos Bible ndi buku lomwe linalembedwa ndi anthu ambili mbili amboni ali ndi lawo angirican aliso ndi lawo aroma aliso ndi lawo apostle aliso ndi lawo ndie mukanene kuti ndi mawu amulungu
Sheikh mwazan mau amulungu bas auzen choona sheikh mukuipatsa moto
Apostle misheck you have the message keep up the good work. Good understanding its vital than memorizing.
You are doing good work Mr misheck you really understand may the good Lord bless you and give you wisdom
BAIBULO lilibe chilema Amen Apostle
Quran ndbukhu losokonezeka,lilibe mfundo zenizeni
Adzabwer kudzamaliz zomwe sanapange paja musaiwale yesu anal batchala sanakwatirep nde akubwer kuzapez kake kangenge
Bible is powerful weapon
Misheck John sanachenjere bwino koma nthawi iyi ndiyabwino kuphunzitsa dziko lapansi
Asilamuwa koma mmm bodza ndithu kumakhota Dala.
Is good chehe
Apostle amawerenga 😂😂😂
Masha ALLAH
SHEKH yo Ali bwno
Koma ngati sheikhewo akunena zoonama malembawo akuwelenga kuti si baibulo momwe
salaam allaykum ... God will punish those who harden their hearts..
Koma apostoli ndi machine 😂😂
Sallamu wallekumu mukuchita bwino Koma QURAN IMAGWILIDWA ULI NDIUDU NDY SIKUZIWA KUT MUKUTHANDIZANA BWANJI PACHITHU CHATHUCHO
Mishek make sure u become a Muslim Tasiya izi zama Bible zakozi
Koma inu Sheikh angawo2 akulongotsola momveka bwino kwambiri
Mukugwira quraan mulibe udhu?
Good work 🙏
Korani nde lasimikizira bwinobwino kuti Bible ndili buku la moyo
Koma apositoliwo amawaziwa wau
Abusa chonde ife asilam sitikukhana kuti bible si buku lamulungu koma tikuti lili ndi mistake ambiri
Abusa bible lili ndi zilema chifukwa cha anthu osawopa mulungu anachotsamo mau ena pomwe Qur'an siyinasithidwepo.
Dzuwa ndi mwezi samakulozera ubwino wake
Quran ndi bukhu lopanda chokaikitsa ndipo linabwera kuzakwaniritsa zomwe zinachotsedwa bible.
Iwe onukha manyi tachoka apa ukasambe ndiposo ukavinidweso
Amen apositoli
Quran longofunika kuliotcha basi losokoneza limenelo
Zikuveka ndthu
Koma chomwe tidziwe ndichakuti.......amene azabwereso kuzatega olugama ndi yesu yeah basi ...no any prophecy never bt Jesus ll come bck
Qà😊à😊q😊
Onse okhulupilira Quran kulibe moyo
Muchenjeletu bwino amisheki kuwelenga mwaphuma kapena akuchemeleleni bible ndi losusana ndipos Bible ndi buku lomwe linalembedwa ndi anthu ambili mbili amboni ali ndi lawo angirican aliso ndi lawo aroma aliso ndi lawo apostle aliso ndi lawo ndie mukanene kuti ndi mawu amulungu
Bible ndi limodzi enawo anabwela kufuna kusutsana ndi bible koma bible ndi Mau a Mulungu enieni osati quran
Quran nambala 1amae
Adzabwer kudzamaliz zomwe sanapange paja musaiwale yesu anal batchala sanakwatirep nde akubwer kuzapez kake kangenge