A person who has gone to school should be seen with his/her actions en fruitful.we salute for you chief.stay blessed with your wisdom so that we too can be blessed ❤
Thank you brother mwatisegula mutu. Only thing I discovered kumalawi Kuno kuli anthu a nzeru ndithu koma sapasidwa mpata muzotukula ziko chifukwa cha anthu andale. But this is powerful message thank you again brother
Thanks Mr we respect you and we just wanna give you respect about what you have said, you didn't just go to school without a reason. You speak truly congratulations Mr.
Mwayankhula modekha ndi motambasula simunagamule mwangotiunikira nkhani yachitikayi ikufanana kwambiri ndi zomwe zimachitika ku Mwanza munthawi ya ulamuliro wa kamuzu kumene kunafa anthu anai a Gadama a Sangala a Matenje komanso a Chimanga ananamizira ngozi ya galimoto lero anamizira ndege eish!!!!
Mcp imapha, ndi yadyera pa mphamvu za boma, ndi ya nkhanza kumbali ya ndale. Anapha anthu amene aja ndi mcp, mzimu wokupha sunawachokere, they are all murderers. Mcp yomweyo yaphanso vice president eeeeh
Thanks brother zamveka bwino kwambili, ambuye apitilize kukupasani dzeru ❤
A person who has gone to school should be seen with his/her actions en fruitful.we salute for you chief.stay blessed with your wisdom so that we too can be blessed ❤
Brother thank you God bless you 🙏
Thanks u my brother koma mchenjele angakipheni ndi mumene mukulongosolelamu
Thank you brother mwatisegula mutu. Only thing I discovered kumalawi Kuno kuli anthu a nzeru ndithu koma sapasidwa mpata muzotukula ziko chifukwa cha anthu andale. But this is powerful message thank you again brother
Wow
Allah akbar my brother thanks potitsegura zeru my allah guide and protect you all the time 💔🇲🇼🙏
Thanks my brother God bless you...
Good explanation in vivid details 👌
Thanks Mr we respect you and we just wanna give you respect about what you have said, you didn't just go to school without a reason. You speak truly congratulations Mr.
Amen, ndipo akulu inu mukulongosola monveka bwino kwambiri. Chakwera sanafune kuusiya udindo wa u President, koma MCP! Niyolimba mtima.
Thanks very much brother
Mwalankhula mwanzeru brother💪
Thank you brother ALLAH bless you
So touching and educative. Malawi must really understand this assassination analysis.
Keep it up bro
Wonderful explanation
Amen broz ambuye akudalitseni.
Thanks brother
Ilike this man this was an assisnation indeed
Umakwana Loya. Ukuwaimiirira achina Kasambala aja ndi onse aphedwa aja. Komanso chifukwa cha uthengawo wa m'buku lopatulika, zanveka bwino kwambiri. Ambuye elemekezeke ❤🙏.
Mpaka kulowa mmalemba?bravo!!!
thank you bro izi ndizoonadi ndithu
Very powerful ndipo ambuye akudalitseni
Amen mulungu simunthu akuona ndithu
Thanks sir for the explanation Koma nkhani ya Davide yo mwayiphonyako pang'ono mukayiwelengeso.
Nice explanation sir thanks
Mwayakhula mwa deep big respect 🙏
Powerful massage brother 🤝
You are right
Thank you so much brother
Wow nice talk
WELL ARTICULATED SIR
Thanks apa ndithu maso atseguka mwatitsegula
Thanks for your enlightenment
Great bro,
Well said
Thanks Elijah
Well explained
Thanks
Beautiful analysis on both aspects biblical and legal
Beautiful analysis
Well put. Keep it going!
well analysis
God bless you...
That's pple we need in this country!
Mmmm ndakuvulira chipewa bro respect
100% perfect word Bro's
God will provide us brother ! 💯 BC people they say until today we still say theys no secret under the sun kungatalike chotan truth imbwela ndithu
Salute
Kutanthauzira malamulo mwamphamvu, bola kumakhala mosamala bra. Coz dziko lathu likudana ndi achinyamata ozindikira.
Mwabaya big ichi ndiye ndi chilungamo
You what you talking My brother thanks for giving us the tip of Low
Well said😢
That's true
Wise man from the east
God bless you bro
Good words
Very impressive
We love u br
Keep it up bro
🔥🔥🔥❤
Very clear
Amen
The is sensible and wise analysis Bro
Blessed brother
Apa ndie ubongo wagwila ntchito yake respect boss
Wise words chief🔥
Inuyo ndukatundu pankhani za kafukufuku i'll follow you from now
God bless you bruh
His Excellency David 😂
Osaopa broo!
no no no!!! Anthunu tikhale srs kwa amene waona photo ya chilima atagonekedwa ntchire opanda even trouser kuvulidwa malaya kutsala ndi kabudula ekha munthu wamkulu ngat amene uja ndi ngozi yamtundu wanji ingapange zimenezo,zikuvuta pati kungovomereza kuti mwamupha mesa ndizimene mumafuna kt zitelo ukuganiza kuti uzakhala pampandoo mpaka liti?
Iweyo ndiye wankhula za nzeru
Insight
Muthu wankhani apa chakwera wapanga chipongwe chokupha chilima & onthers ppl
Fact
Ndakuvani brother achakwera amumphera dala chilima
Thanks brother kkķkk wina mundiuza kut kulibe nso ophunzila ku Malawi relo siizi hahaha zidziwika mu dzina la YESU soon
❤❤
Let's be buddies man, you are such a person I need in my circle
💪💪💪
2 Samuel 11:1-27 ❤
God bless you richly
Great
it was the warm heart of africa till it turned bitter…
Genius
🎉
Thats true story bro
❤
Uku ndiye kuyankhura
Zikomo boss 🙏🙏
Brilliant ❤
Very intelligent
Zimnvere muntolo ...apa mwayankhura chief ulemu wanu
Wel narrated thanks brother. Yes parachutes anali kuti
May God amplify your voice
Yeah ndanvesa
Ukundiye kufotokoza kwabwino mwandisegula mmaso😢😢
Mwayankhula modekha ndi motambasula simunagamule mwangotiunikira nkhani yachitikayi ikufanana kwambiri ndi zomwe zimachitika ku Mwanza munthawi ya ulamuliro wa kamuzu kumene kunafa anthu anai a Gadama a Sangala a Matenje komanso a Chimanga ananamizira ngozi ya galimoto lero anamizira ndege eish!!!!
Mcp imapha, ndi yadyera pa mphamvu za boma, ndi ya nkhanza kumbali ya ndale. Anapha anthu amene aja ndi mcp, mzimu wokupha sunawachokere, they are all murderers. Mcp yomweyo yaphanso vice president eeeeh
Mumakwana ❤❤❤❤
Wise
Chisanzo cha bwino cha Bible tanvesesa 😢😢😢😢
Zikomo ichinde chilungamo wadzellu wamva koma MCP dzidzatheka basi yamagadzi iyii