CDEDI PRESS BRIEFING (Malawi)

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 30 ก.ย. 2024
  • #malawinews

ความคิดเห็น • 60

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 7 วันที่ผ่านมา +3

    Mr namiwa you are comrade namiwa Allah azikuyang'anirani thawi zonse

  • @TimexKaufa
    @TimexKaufa 2 วันที่ผ่านมา

    Khaniiyi muibweretsa bwino kobasi tikyyamikileni. Mlungu akudalitse I. Koma tipephenao sizoti mulandile thumba lokutsekani pakamwa pakamwa. Yendetsani chilungamo

  • @AllieJonassi
    @AllieJonassi 9 วันที่ผ่านมา +2

    Ndipo musasinde maganiso mr namiwa maso patsogolo bas mulungu ali nanu limodzi patsogolo panu osawopa

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc 2 วันที่ผ่านมา

    Iyi sithawi yocheza amalawi tikufuna ufulu, izi tizimange chilili chipanda apo ibuke ibuke, sitikufuna chinyengo achakwera zinthu mnalephera kare siife koma inu nokha,

  • @KinziWindasoni-h4b
    @KinziWindasoni-h4b 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mukapeleka masiku akatha simukuchitapo kanthu .kulankhula kokha ndinu akatakwe .koma kuchita

  • @FelixSomba
    @FelixSomba 2 วันที่ผ่านมา

    Alonda ,amuchikangawa ,akutipo chani pankhaniyi,kodi mesa munkhalango ,muja muli alonda?

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc 2 วันที่ผ่านมา

    Msatitenge ngat siife amalawi, tipanga ziwoneselo konse konse sitikufuna zausilu tonse ndife amalawi,

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc 2 วันที่ผ่านมา

    Ndipo talimba ntima china chake chichitike basi tionesana pa imfa yii, ndife okwiya ngat simukuziwa

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 4 วันที่ผ่านมา

    Namiwa umakwan ndpo osadzalandra ndalam zamagaz Mulungu adzakukantha bravo Namiwa always u hit the nail proud of u auncle

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc 2 วันที่ผ่านมา

    Ndipo palibe chopyatira anthuwo ali limoz wonse atule pansi udindo wonse

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 4 วันที่ผ่านมา

    Nthawi ya DPP kunali human rights vuto ali mbali yasatana mzao paja asatan amayenda asatana okha okha ndye Namiwa wabwera kudzaika poyera chilungam

  • @JulietLizziePhiri
    @JulietLizziePhiri 2 วันที่ผ่านมา

    Koma ma feedback akumabwera? 14 days ija sinathebe kodi?

  • @MatthewGhondwa
    @MatthewGhondwa 7 วันที่ผ่านมา +1

    HRDC yasowa chifukwa analandira ndalama

  • @ChimsyUlemu
    @ChimsyUlemu 6 วันที่ผ่านมา +1

    I remember in RSA period like this in parliament they put the president in front n question him direct

  • @PeterMlowoka
    @PeterMlowoka 6 วันที่ผ่านมา +1

    Ngati tinachotsa Dr, Banda Pali chani tisiya bwanji kulankhula sitikuziwa chinachitika iwo Ngati akuopyeza which means akuziwapo katho

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc 2 วันที่ผ่านมา

    Namiwa tapanga changu 14 days yachuluka 5days imakwanila

  • @JaphetYohane
    @JaphetYohane 6 วันที่ผ่านมา +1

    Atiuze chilungamo za imfa ya beyeni

  • @SalimGrey
    @SalimGrey วันที่ผ่านมา

    Ndichifukwa chake otsutsa sapeza mpata

  • @DaveDambo
    @DaveDambo 4 วันที่ผ่านมา

    Please boss pitilizani kupanga zinthu zofunikazi

  • @SolisterChagunda
    @SolisterChagunda 2 วันที่ผ่านมา

    Anamiwa musamamize anthu. Ose omwe amasankhindwa mipando mukunenayo eg speaker amakhala andale komaso Richard Msowoya adakhalapo speaker panthawi yomweyo Ali first speaker wa nyumba ya malamulo ndipo sadatule pasi

  • @DigleDafter
    @DigleDafter 6 วันที่ผ่านมา

    Cdedi inuyo munabwera kuzatimirira❤

  • @DaveDambo
    @DaveDambo 4 วันที่ผ่านมา

    This man hmm very important person ❤

  • @JosephKwimbayani
    @JosephKwimbayani 3 วันที่ผ่านมา

    Namiwa 💪💪💪🙏🙏💯💯 ndiwe dolo Activist

  • @NancyBanda-g2j
    @NancyBanda-g2j 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akwanati masiku 14

  • @geofreydzinyemba6107
    @geofreydzinyemba6107 วันที่ผ่านมา

    Nkhani ya bwino iyi😊

  • @NicolasKamunga-rv9vr
    @NicolasKamunga-rv9vr 5 วันที่ผ่านมา

    Ine kuno ndikuona kuchedwa ndi demo

  • @OssmanAbubaker-w3x
    @OssmanAbubaker-w3x 3 วันที่ผ่านมา

    Zoonadi Mumatiimilira

  • @MlecheFatch
    @MlecheFatch 3 วันที่ผ่านมา

    Anatilakwira koma

  • @Davie-y1l
    @Davie-y1l 5 วันที่ผ่านมา

    Cidet woyeeeee

  • @OrisChitseko
    @OrisChitseko 4 วันที่ผ่านมา

    Mumakwana big...

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i 6 วันที่ผ่านมา

    CDEDI more fire 🔥 be strong guys 👦 chikangawa wachepa uyu we trust you guys more fire 🔥 again chakwera azaimenso next year pls 🙏

  • @MercymithieMithie
    @MercymithieMithie 3 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤❤

  • @AiwaMedia-sh6vx
    @AiwaMedia-sh6vx 7 วันที่ผ่านมา

    Pepani a CDEDI akuchita ngati kulankhula mwamwano koma am following every time you are online. Awawa apaneni MACHENDE mpakana aphulike
    Amongst all these concerned ministers bear 10 culpable homicide each.
    Chakwera sakupusisidwa ndi wina aliyense pa report yandenge, iyeyo mwini ndi mastermind hence he can't take any action to any suspected Minister. Two!!! Chakwera akuwopa kuti akangochotsa wina wake, atha kukhala pachiwopsezo chopangidwa EXPOSE
    Awawa chonde mwatonse tiyeni tiapane
    Ndathokoza a NAMIWA.

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 7 วันที่ผ่านมา

    Komatu mulungubwangoti phee kuonelera..ifika nthawi zobisika zibwera poyela..viva Namiwa..mudafooke😊

  • @qhwireless961
    @qhwireless961 6 วันที่ผ่านมา +2

    I salute you comrade. this is not apartheid time

  • @ronaldordinga6537
    @ronaldordinga6537 9 วันที่ผ่านมา

    Every government is having a strong independent organization that opposes the motion of the ruling government during DPP it was HRDC directed by T. Mtambo more power to these comrades

  • @MjombaMoosa
    @MjombaMoosa 7 วันที่ผ่านมา

    Achakwera ngakhale pang'ono osaganiza kukaonapo pamene panagwela v p nkhondotu iyi akuyiyambayi

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 7 วันที่ผ่านมา

    Komaso mcp kungowauza thawi kapena kuwauza siku lomwe munganene inuyo basi comrade auzeni basi

  • @shupiebeib
    @shupiebeib 6 วันที่ผ่านมา

    Mmakwana chief,big up"

  • @JosephIsaac-s1c
    @JosephIsaac-s1c 8 วันที่ผ่านมา

    Malawi akufunika anthu ngati inuyo Comrade mulungu akupatseni moyo wautali

  • @trifoniachilunda6263
    @trifoniachilunda6263 7 วันที่ผ่านมา

    Atiyankhedi anthu amenewa atikwana kwambili

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 10 วันที่ผ่านมา

    Namiwa is good Comrade same same Comrade Mtanyiwa ❤❤❤❤❤❤

  • @KentWilliam-r2v
    @KentWilliam-r2v 6 วันที่ผ่านมา

    Mumakwanila big

  • @danmbuzi
    @danmbuzi 6 วันที่ผ่านมา

    Mumakwana guys

  • @AllieJonassi
    @AllieJonassi 9 วันที่ผ่านมา

    Proud of you mr namiwa

  • @HestingsWilson
    @HestingsWilson 6 วันที่ผ่านมา

    Achoke watikwana

  • @MussahGilbert-lk5mn
    @MussahGilbert-lk5mn 6 วันที่ผ่านมา

    Chakwera achoka basi

  • @MacsJafali-d1m
    @MacsJafali-d1m 10 วันที่ผ่านมา

    kwaolaaa

  • @BillyBentryMunthali
    @BillyBentryMunthali 10 วันที่ผ่านมา

    Bwanji nthawi ya DPP sided kunalibe koma kungobwera chakwera bas cided ya bwana nanga cholinga chawo ndi chian?

    • @TakalaniGlenda
      @TakalaniGlenda 7 วันที่ผ่านมา

      Kudzudzula zolakwika are you against this organization? Are you also chikangawa?

    • @RosinaPatel
      @RosinaPatel 7 วันที่ผ่านมา

      Iwe ndiwe mbuli..ife imfa ya Chilima ikutisowesa mtendere

    • @RosinaPatel
      @RosinaPatel 7 วันที่ผ่านมา

      Useless person

    • @kingsleymsampha2260
      @kingsleymsampha2260 6 วันที่ผ่านมา

      This is the best time for CDEDI. Kunali HRRC lero ndi la CDEDI

    • @MussahGilbert-lk5mn
      @MussahGilbert-lk5mn 6 วันที่ผ่านมา

      Iwe sukudziwa ndiwe mbuli paja

  • @donexmakande5979
    @donexmakande5979 7 วันที่ผ่านมา +1

    Were together namiwa

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 10 วันที่ผ่านมา

    This Man called namiwa he's a really comrade

  • @steka-c3j
    @steka-c3j 7 วันที่ผ่านมา

    Mumatha guys