Chiphwilikiti mu Nzinda wa Limbe

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 20 พ.ย. 2023
  • Chiphwilikiti mu Nzinda wa Limbe
  • ตลก

ความคิดเห็น • 64

  • @BenissoneErnesto-eh6zs
    @BenissoneErnesto-eh6zs 8 หลายเดือนก่อน +2

    Apolice matama ati iwooo audindo watching from Mozambique

  • @LeonardPetro-ky6dq
    @LeonardPetro-ky6dq 17 วันที่ผ่านมา +1

    Koma kumalawi ndichani? Nanga Anthu adya chani😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @Elizabethshaibo
    @Elizabethshaibo 8 หลายเดือนก่อน +3

    😂😂😂Malawi 🇲🇼 tikapuma kumwamba

  • @vitumbikocobysinyiza-5116
    @vitumbikocobysinyiza-5116 8 หลายเดือนก่อน +3

    Apalice ndizitsilu akuthamangisaso atola nkhani

  • @user-nw6ie3xx8b
    @user-nw6ie3xx8b 8 หลายเดือนก่อน +2

    Palipose kumayala zinthu zogulisa musite

  • @user-dn7he4tb1f
    @user-dn7he4tb1f 8 หลายเดือนก่อน +5

    Next time, wear a highly visible identification as press.

    • @finchiadriano
      @finchiadriano 8 หลายเดือนก่อน +1

      very importance ,

    • @Midy265
      @Midy265 8 หลายเดือนก่อน

      I support the idea. Otherwise it could have been a front page story. Osamawapatsa zochita a polisi.

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 8 หลายเดือนก่อน +2

    Ndakunyadilani a reporter ndi team yanu apa boma linganizile anthu,apatu zizikuyendaaaa

  • @memoryyusufu
    @memoryyusufu 8 หลายเดือนก่อน +2

    Agendedwe zeni zeni chakwerayo awone ndinthu

  • @matiascalimbe1106
    @matiascalimbe1106 4 วันที่ผ่านมา

    Ziko langa ndi chiyani?

  • @gradsonmayira9336
    @gradsonmayira9336 8 หลายเดือนก่อน +1

    Dynamic leadership

  • @folamitowing238
    @folamitowing238 8 หลายเดือนก่อน +2

    Make sure kuti ma ID anu ali ready mukachotse mneneri onyengayu Chakwera 2025.

  • @user-cm5pv8dn7k
    @user-cm5pv8dn7k 8 หลายเดือนก่อน +1

    Agedendwe agalu awo kuphatikiza galu wawo chakwera

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr 8 หลายเดือนก่อน +1

    1000 job ankanena kuti apereka ija ndiimeneyi? Achinyamata, a Malawi tikuvutika akuti atani anzawo eeee Lilongwe city l see you coming 😂

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 8 หลายเดือนก่อน

    Ah! Zayambika, Chakwera woyeeeeee! President wa bodza ngati uyu.

  • @JamesChipande
    @JamesChipande หลายเดือนก่อน

    Tizikadya manyimba mwanu?

  • @user-ji4ed6dl3i
    @user-ji4ed6dl3i 8 หลายเดือนก่อน +1

    vendor ndi mwini tsika 😂😂

  • @alinafeanderson3065
    @alinafeanderson3065 8 หลายเดือนก่อน

    dziko muno mavuto achuruka even apolice wo mavuto wa akuwadziwa nde mtendere ndi ovuta ngt dziko muli mavuto ochuruka marephera kumvana ndipo izizi zangoyamba zikhala zikuchitika

  • @user-hs5xv6bk2f
    @user-hs5xv6bk2f 8 หลายเดือนก่อน +1

    Chakwela woyeeee 2025

  • @Charlieelieq
    @Charlieelieq 8 หลายเดือนก่อน +2

    Boma ili likufuna liphe anthu

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd 8 หลายเดือนก่อน +1

    Inu aside ndnu dzitsilu mwava

  • @kondwamlungu8384
    @kondwamlungu8384 8 หลายเดือนก่อน +1

    Nankha amalawi titani

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd 8 หลายเดือนก่อน

    Acity ngat chakwera wakutuman inuyo ndnu dzitsilu mwa adzitsilu nonse

  • @alicehananiya
    @alicehananiya 8 หลายเดือนก่อน

    Gayez mukanaotcha galimoto yaoyo agaluo akakhuta eti ? Zinthu sizikuenda bwino moti iwo sakudziwa

  • @vinc8359
    @vinc8359 8 หลายเดือนก่อน +1

    eeeeh kwakoma ndi kuno

  • @user-yj6gs3gx5v
    @user-yj6gs3gx5v 7 หลายเดือนก่อน

    Ngat isathe ma guy mumatha ......

  • @user-my9op9et7z
    @user-my9op9et7z 8 หลายเดือนก่อน

    mwagwesa kwacha lero mukumenya anthu kodi chomwe mukufuna kt munthu achite ndichani

  • @user-im3gn6bp4e
    @user-im3gn6bp4e 8 หลายเดือนก่อน

    Nawo a city ngat atumidwa Afela za eni chifukwa.malawi watopa kwambiri

  • @Alinafe615
    @Alinafe615 7 หลายเดือนก่อน

    Kugulisa malonda munsewu ndizosaloledwadi zoona, koma ndi mmene likuyendera bomali anthu awaleke azipanga ma business awo, chuma chikazayamba kuyendano bwino ndi pamene azasate kayendesedwe kamalonda munsewu.koma kutero panopa ndikuzikonda

  • @PeterChikwakwa-xk1kr
    @PeterChikwakwa-xk1kr 8 หลายเดือนก่อน +1

    Shaaaaaaa

  • @graciouschimamba1807
    @graciouschimamba1807 8 หลายเดือนก่อน +1

    Koma ndee kukaniza Mic 2😂

    • @hunmadise8656
      @hunmadise8656 8 หลายเดือนก่อน

      Kuchito kumenya nkono😂

  • @tapiwakamanga2330
    @tapiwakamanga2330 8 หลายเดือนก่อน

    Eish mmmm

  • @PeterThawi-jc7zl
    @PeterThawi-jc7zl 8 หลายเดือนก่อน

    Boma la MCP...lafika ponyasa...Ife sitika vota 2025.bolanso Adadie

  • @gregben7657
    @gregben7657 8 หลายเดือนก่อน +1

    😮

  • @gabrielmaluwa1038
    @gabrielmaluwa1038 8 หลายเดือนก่อน

    Akujaila acity

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 8 หลายเดือนก่อน +1

    Zovutatu vendor ndiokwiyatu

  • @matolaandiochi1199
    @matolaandiochi1199 8 หลายเดือนก่อน

    Zikuti bwanji kod

  • @realsu7816
    @realsu7816 8 หลายเดือนก่อน

    Payatandaga

  • @catherinekatherere6949
    @catherinekatherere6949 8 หลายเดือนก่อน

    Kodi mmene mwagenderamu chimene mwakonzapo pamenepo ndichani? Umbuli basi zaphatikizana ndi kupepera

    • @whitethamangar2950
      @whitethamangar2950 8 หลายเดือนก่อน

      Ndiwe chitsiru kobasi umafuna anthuwo angothilidwa teargas ngati akapolo

  • @promixphotography8056
    @promixphotography8056 8 หลายเดือนก่อน

    Kodi moto ukumasowa

  • @AnastasiaChakwiya
    @AnastasiaChakwiya 8 หลายเดือนก่อน

    Ochakwera Amalawi akwiya

  • @YupaulYusuf-fg7lp
    @YupaulYusuf-fg7lp 8 หลายเดือนก่อน +2

    Sellina anakodza umatha kuyakha

  • @user-yg3hb7jh1q
    @user-yg3hb7jh1q 8 หลายเดือนก่อน

    Kodi venda mukamukaniza ku gulitsa malonda mudziko lake akakudyelani kuti Malawi wafika panyasi

  • @user-ex7zc3sg5e
    @user-ex7zc3sg5e 8 หลายเดือนก่อน +2

    boma.ili ndilolephela maboma.wonse. apita.buyomu.amapanga.zithu. zolondola.koma awa. Akufuna.kubwezelesa.za.kamuzu.kulanda.katundu.wa.mavenda.kodi. akufuna. Amalawi. apange.chani.ndimene zavutilamu.alibe.chisoni.ndi.a Malawi. Akufuna. Anthu.onse.afe.ndi ye.amalawi.mukafuna.zija.ndizimenezo.amuluzi.anayankhula.kuti.mcp ndichipani chankhaza ndizimenezi

    • @frankkassim1254
      @frankkassim1254 8 หลายเดือนก่อน

      Abale ingomuphani chakwela tipeze mtendele ife

  • @user-rl1hb2lc3u
    @user-rl1hb2lc3u 8 หลายเดือนก่อน +2

    Vendor pamalo pake😂

  • @trynessmwenda4950
    @trynessmwenda4950 8 หลายเดือนก่อน

    Koma Driver wagalimoto yagendedwa kwambiri yo ali moyo???

  • @user-ek4xw7yf1e
    @user-ek4xw7yf1e 8 หลายเดือนก่อน

    Kom sakulingalila kut panopa athu tnachulukana motan choyamba akamblane Kaye chmenecho oky

  • @alickdouglasp3493
    @alickdouglasp3493 8 หลายเดือนก่อน

    Vendor yeeeeh malo ameneu

  • @EniyaBanda
    @EniyaBanda 8 หลายเดือนก่อน

    Koma abale

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr 8 หลายเดือนก่อน

    Mibawa 2023 Abel Luwanga, 🎖🏆

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p 8 หลายเดือนก่อน

    Chiyambi

  • @MacdonaldMisomali-lt4wu
    @MacdonaldMisomali-lt4wu 8 หลายเดือนก่อน

    Boma lofoyila lingoziwa kuthamangisa anthu bs awaphe bs

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 8 หลายเดือนก่อน

    Umbuli

  • @user-hs5xv6bk2f
    @user-hs5xv6bk2f 8 หลายเดือนก่อน

    Achakwela mavenda mumawamenyela kanpeni wanu wonama kuti zizawayendela aja lelotu ndiamenewa samala azakukwapula amenewa 2025 muno