Osaopa...bros...sangakupheni...wachepa zed ndi ana awa dzelu zawathela manyadzi tsopano chifukwa chake angoyankhula popanda pake ngti mwana wa 2 years ........more fire osatopa ayi ayikeni pambala...mbanda agalu..amenewa...tikanadziwa agalu awa...tsitikanawapatsa...vote yathu ayi😢😢
God bless you gyz zenje lokumbila mzako umagwelamo wekha
Mmmmmm nkhaanga zawona nd namba one i salute u
Osaopa...bros...sangakupheni...wachepa zed ndi ana awa dzelu zawathela manyadzi tsopano chifukwa chake angoyankhula popanda pake ngti mwana wa 2 years ........more fire osatopa ayi ayikeni pambala...mbanda agalu..amenewa...tikanadziwa agalu awa...tsitikanawapatsa...vote yathu ayi😢😢
Iz Malawi a warm heart of Africa😢 or a God fearing nation😮
Don't worry brother or of you we are together with you Malawi ndiyathu iyi
Fire fire mabomba...keep it up
You are the best
Nkhanga zawona 🔥🔥🔥
May God bless and protect you guys, you always stand for the truth and fight for freedom for poor citizens, proud of you always 🔥🔥🔥🔥
Akulu akulu nonse omwe tamvera audeo iyi tiyeni aliyense payekha payekha timuthokodze mulungu chifukwa chakutuluka madgage amenewa
Muthokoza zichan amalawi moti simukudziwa be kut ndi ndindale zimenezo kkkkkkk amalawi
Akuluwa samakhala ku south Africa ndizambodza
Kumphamvu ya mulungu mwini kupanga moyo chiwembucho sichikutheka ndipo nkhati iweyo ng'oma pamodzi ndi chakwera mukufuna kupha anthu amenewo mutipha tonse dziko lamalawi chifukwa ngakhale nafenso omwe tiri osaziwika dziko lamalawi sitikukufunani.😂😂😂😂
Nice nkhanga zaona
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣more fire💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥
More fire 🔥
Moto buu❤❤
❤❤❤❤ nkhanga zaona
The following link and
Kodi zikhaleng'omA akuonangati dzikoli natuluka pa buyala mayiake pankholopakoiwe dzikhaleng'oma
Osadandaula a Malawi Chakwera ndi nduna zake si angelo komanso Yehova saangalore kuti anthu amenewa azunze a Malawi, posachedwapa Satan agonja
Kodi mukudziwa Kuti chakwera amadziwa kuvina vimbuzi mufuseni
😂😂😂😂 komadi kunali kamuzu pano anangokhala ntchende lonkha mmanda
Brother aululeni adZiweonkha
Malawi tiyeni tipephere .
🎉🎉
Mwaswela bwanji achimwene anga , Kodi nkhanga zilipo ?pitilizani kutipasila nkhani mulungu akusogoleleni nooonse
Malawi tipephere.zikomo.
Mofaya mthonyiwa iponde fadah.
Amalawi akudziwa kt ndiwe wambodza' munkati mwazidziwa kale vp asakha wakuti wakuti apa ndi uyu tikuwona a usi mukusochwlesa amalawi koma simuwatha amalawi tadziwa ndiwe wabodza ndi mzako emweyo akukupasa zambodzazo tikumudziwat ife akukupasa zamambodzazo
Title of the song pleaseeeeeee
Akupangilidwa ma passport wo achitenge chamwayi akasake ntchito ku S A ko coz ndizosowa mwayi oterewo
Kodi iwowo sadzafa
Tiuzeni ife tidziwe kuti kunjaku kuli motani timakunyadirani
😂😂😂😂 zikhale ntchende ngati njovu
Zikhale ng'oma ndiwoyipa khope ndi tima womwa Mmmmm shame on you
Anyamata openyesesa othudzula maso madolo anamanyonyoro ntanyuwa
Kkkkkkk koma zikhale ameneyi
Nkhaaaaaaaaàaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaangazaoooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooona mulibwanji kunse kumene muli Lelo 26
Ng'oma tikukuonatu
Inu ankhsnga zaona nonse ndinu anthu achabe, mchifukwa chiyani mumangoona zina komaso kungopeka zoipa zokha. Ndikuuzeni mosakunyengelerani, mwainu mulibe choonadi ndi chilungamo. Vuto lanu ndinu a DPP, ndiye ine komaso mmalo mwa amalawi ochulukai zedi tikuti mande anu komaso Nyini zanu. DPP yakhala ikuvhita zambiri zoipa bwanji simunena zimenezo? Kodi inuyo zaphedwa kwa alubino mu nthawi ya DPP bwanji simunena? Kodi bwanji simunena za kulephera kwa DPP kukwanilitsa malonjezo awo kwa zaka 6? Kodi inuyo pano tita muuze koma Kuna mangidwa Singapore yomwe amaliseche akumwera inatilonjeza ija mungatiuzw kuti ilikuti? Inu amane mukumaikaika ma comment, osamangoika ma comment pazithu zauchitsilu, the first thing is, kuzifusa kuti Kodi DPP inapanga chani chomwe lero lino tingaloze kuti chikupidulira amalawi?
Mmm zukuyenderani anthu akuvutika inu amalonjeza okha nthawi ya bingu umbamva unachepa, Kuba ndiye dpp yokha mmbiri ya zipani mmalawi inu mcp ndiyo kanika kuchoka kale
@@blandinabonaventure pepani pejiyi nja satanic amene akutukwana ndi ana asatana