- 61
- 904 057
TIDZIWE TV
เข้าร่วมเมื่อ 20 ก.พ. 2023
This channel for TIDZIWE TV
วีดีโอ
KUNALI KUMANO WA MAMFUMU KUNYUMBA YA TSOGOLERI WAKALE A BAKILI MULUZI KU BCA HILL
มุมมอง 743หลายเดือนก่อน
Mamfumu akumachinga anayitanidwa ndi mtsogoleri wakale kuti vakawapase chiseka pakamwa kapena kuti ndalama
NKHANGA ZAONA _ DPP YAMENYA GALU NDIPO MBUYACHE WAONEKA
มุมมอง 11K10 หลายเดือนก่อน
NKHANGA ZAONA _ DPP YAMENYA GALU NDIPO MBUYACHE WAONEKA
BEN LONGWE WAYAMBA KUMANYOZA MITUNDU YA ANTHU 🇲🇼
มุมมอง 6K11 หลายเดือนก่อน
BEN LONGWE WAYAMBA KUMANYOZA MITUNDU YA ANTHU 🇲🇼
NKHANGA ZAONA- APOLICE AKUSAKASAKASO VICE PRESIDENT WA A BON KALINDO KUTI AMAGWIDWESO
มุมมอง 14K11 หลายเดือนก่อน
Tidziwe tv
NKHANGA ZAONA - MA PASSPORT ADINDIDWA KUTI AKAKHALE UMBONI PA KHOTI PA MULANDU WA FELEX MAGANGA🇲🇼🇲🇼
มุมมอง 16Kปีที่แล้ว
Tidziwe tv
NKHANGA ZAONA - ANTHU OMWE APITA NDI PRESIDENT KUNJA NDI 210 OSAMANAMIZA A MALAWI 🇲🇼
มุมมอง 7Kปีที่แล้ว
Tidziwe tv
NKHANGA ZAONA-APEZEKA KWA NSINGANGA NDI CHOVALA CHA MKATI CHA MNYAMATA WAWO
มุมมอง 76Kปีที่แล้ว
Tidziwe tv
KAMULEPO KALUWA KUYAKHULAPO ZA MALAWI FIRST
มุมมอง 10Kปีที่แล้ว
KAMULEPO KALUWA KUYAKHULAPO ZA MALAWI FIRST
LIMPOPO FM YALANDILA CHIOPYEZO KUCHOKA KU MALAWI FIRST🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
มุมมอง 22Kปีที่แล้ว
LIMPOPO FM YALANDILA CHIOPYEZO KUCHOKA KU MALAWI FIRST🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
BUNGWE LA MALAWI FIRST 🇲🇼 KULI PUNGWE PUNGWE PAKATI PA BEN LONGWE KOMASO BON KALINDO🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
มุมมอง 24Kปีที่แล้ว
BUNGWE LA MALAWI FIRST 🇲🇼 KULI PUNGWE PUNGWE PAKATI PA BEN LONGWE KOMASO BON KALINDO🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
THOMAS CHIBADE WA MWALIRA KUCHIPATALA CHA KAMUZU CENTRAL KU LILONGWE
มุมมอง 9Kปีที่แล้ว
THOMAS CHIBADE WA MWALIRA KUCHIPATALA CHA KAMUZU CENTRAL KU LILONGWE
KENNETH MSONDA WAPASIDWA NDALAMA KUCHOKERA KU MCP KUTI ADZITENGA INJUNCTION KU DPP
มุมมอง 16Kปีที่แล้ว
KENNETH MSONDA WAPASIDWA NDALAMA KUCHOKERA KU MCP KUTI ADZITENGA INJUNCTION KU DPP
NKHANGA ZAONA - YASALA MISIKA IWIRI KUTI A OTCHE ANYAMATA AKWA NSUNDWE
มุมมอง 13Kปีที่แล้ว
NKHANGA ZAONA - YASALA MISIKA IWIRI KUTI A OTCHE ANYAMATA AKWA NSUNDWE
NKHANGA ZAONA -ANTHU AMENE AKAOTCHA MISIKA MADELAMU APASIDWA NDALAMA ZAWO
มุมมอง 10Kปีที่แล้ว
NKHANGA ZAONA -ANTHU AMENE AKAOTCHA MISIKA MADELAMU APASIDWA NDALAMA ZAWO
NKHANGA ZAONA - AKUFUNA KUTENGA INJECTION KUTI HRA ISACHITITSE MADEMO
มุมมอง 8Kปีที่แล้ว
NKHANGA ZAONA - AKUFUNA KUTENGA INJECTION KUTI HRA ISACHITITSE MADEMO
MCP YAKOZANSO UPANDU OLEPHERETSA MADEMO OMWE MALAWI FIRST AKONZA
มุมมอง 9Kปีที่แล้ว
MCP YAKOZANSO UPANDU OLEPHERETSA MADEMO OMWE MALAWI FIRST AKONZA
NKHANGA ZAONA - TANZANIA YATI IKUFUNA NDALAMA ZAWO ZOMWE BOMA LA MALAWI INANGONGOLA ZA MAFUTA
มุมมอง 7Kปีที่แล้ว
NKHANGA ZAONA - TANZANIA YATI IKUFUNA NDALAMA ZAWO ZOMWE BOMA LA MALAWI INANGONGOLA ZA MAFUTA
SADYEKA WADYEKA LERO, ANTHU ATAFIKA POTOPA OSACHITIRA MWINA KOMA KUDYA FISI
มุมมอง 2Kปีที่แล้ว
SADYEKA WADYEKA LERO, ANTHU ATAFIKA POTOPA OSACHITIRA MWINA KOMA KUDYA FISI
NKHANGA ZAONA KULINDERA(RSA) KUNALI CHIPWIRIKITI POMWE AMALAWI AMAMENYANA NDI MZIKA ZA KU MOZAMBIQUE
มุมมอง 15Kปีที่แล้ว
NKHANGA ZAONA KULINDERA(RSA) KUNALI CHIPWIRIKITI POMWE AMALAWI AMAMENYANA NDI MZIKA ZA KU MOZAMBIQUE
MA ACTIVIST ANU ALIPO ONSE TISADERE NKHAWA BY RC MPHEPO
มุมมอง 6Kปีที่แล้ว
MA ACTIVIST ANU ALIPO ONSE TISADERE NKHAWA BY RC MPHEPO
MALO ABOMA AYAMBA KUTENGEDWA KUMAGWIRITSIDWA NTCHITO NDI CHIPANI
มุมมอง 9Kปีที่แล้ว
MALO ABOMA AYAMBA KUTENGEDWA KUMAGWIRITSIDWA NTCHITO NDI CHIPANI
I like the song
Live from mocambique🎉🎉😂😂❤
Osaoopa osafooka, nenani basi
Opadi chimunthu chosanva chisoni kuti anthu a kubvutika ndi njala fetereza odula bzoti kuli apele opan da chisoni
Boma lachakwela boma la chigololo boma lachimangawa boma lakupha
Panga zako ndi banja lako, zimenezo sizikupindulira ntanyiwa aaaaaaa za ziiiiii,nde ife zitipindulira chani?
❤❤❤❤
Ibwegede ndithu
Zaziiii
Vuto amalawi ngati munthu mwamukonda simuona vuto lake mwaona abon kalindo aja agwa kundarama apapa sangavomere kuti ndarandiradi dola koma mulungu afuna muone zakuseli
Wamisala anaona nkhondo muziti akunama pomwe munthu akunena zoona kuti amalawi muziwe zakuseli anthuawa ndifuna ndarama
Ndimwamuna Bon kalindo komanso mulungu amamufuna kwambili chifukwa amayankhula chilungamo
Ndiye kuti chakwela amkanamizila kudwala ndicholinga chakuti akakambilane zakupha kalindo eeeee koma chakwela
Timadziwa kale kuti chakwela ndichilombo
Ine manyazi amuluzi 😅😅😅😅😅😅 mutu opanda chisoni anali kut aaaaaaaa dziko lamalawi laipadi
Malawi is adecratic country
Kodi bwanji mukulimbana ndi UDF yaanthu mesa mukuti DPP ndichipani chachikulu bwanji osapanga zanu
Iweyo ndineyo timavana izsi ndisakare bwanji alephere chakwera kumuyendere bakili mulusi alakwachani kapena akuusani kut UDF ililimosi ndi mcp bwanji kod athu inu dikilani aliyese apanga ndare zake
Mcp zitikuimvuna kom usapangire kapeni atupere akusiwa chomwe akupanga
UDF sitilola kukhala munkhwapa mwa MCP or DPP sitikuifuna tipita tokha kumasakho win or lose period
Umbawi
😂😂😂😂😂😂😂😂 ine manyazi inu okay amuluzi
@@UseniMailosihahaha umbawi😂 wabwanj? 😂
Amuluzi dyera zoona mpaka akugulitsa chipani?
Nthanyiwa ndikuchita kukusalila kudya
Adani asakuone
Adaniasakuone❤
Mumatilankhulira mukukhonza ndithu Limpopo
Timayikonda wayiresi imeneyi.
Mtanyiwa ndiwe mbuzi kwambiri, bwerani poyerapa tikuoneni, agalu inu
Nde za Ku state house dzikukudzani bwanji agalu inu. Kalindo pamsana pako, mtanyiwa ndi galu, mtanyula mbuzi
Dzitsiru dzokha dzokha inu. Mbuzi za chabe chabe inu. Ana Annika inu. Zikamwa dzanu dzonukhadzo. Inuyo ndinu dzitsiru komanso dzabodza
bg up sir osaopa akupezani kt
Mumati sasewere golf lero ali mu ground ndiye time ziti munati akhala pansi sasewera
Ngati ma sms mukulandilawo ndiwokuopysezani,kulibwino mupite kunja bola Limpopo timakudalirani
Zoona koma lipopo mbambande
Tiwuze kkkkk tive
Atukwana asanave
Kkkkk
Anthu woipa
More 🔥 a malawi chakwera watikwana kwambiri azipita basi enough is enough a malawi pangani chocho ndithu
Mwasowatu bg boss
MULUNGU ali naanu Alimpopoooo akutetezelani nthawi zonse Osatopaaa osafookaaa osawopaaa💪
Kkkkk koma kwachematu 😂😂😂✊✊🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼Winaathawa
😂😂😂😂
Chikakhala chisembwerecho mdiye Mcp nkudya kwake ..koz akuti even mbumba za Kamuzu zinkadyengedwa nda youth myp kalero kumisonkhano yogonera konko mhuuu
Koma ase iwe ndi katundu kwambili
More fire comrade
Siku limene boni karindo akazapwedwa nkhondo izayamba popopopo Inu asilikali zigonani m cpathubwa kwambir
Tiuxen zowona
osaooooooooooopa
Ndipo sizitheka
I love nkhanga zaona more fire mthanyuwa!!
More 🔥🔥🔥🔥 keep the fire burning
Mumakwana itoseni itoseni acomsy
Kodi lero timva zotani za aerio chair man anali kuchinawa
Sikuti nkuopa bill ya mkadzi ati nkukhwimila anamunamidza Kwa sing'anga akabiba mu toilet apenga a Vaya 😇🤣🤣🤣