So it means such stuff is everywhere. In Zambia too there is much talk about Yo Maps and Chile One, Mr Zambia. The only difference though is that these guyz do not go public word-stoning one other but it's the general public that somewhat promote or proliferate the so called competition, earning themselves a name: "THE DISCIPLINARY COMMITTEE" In the world of sports it's 'Ronaldo or Messi'
Lulu is a Legend......to those who follow Lulu and Namadingo you have to listen nyimbo imene these two anayimba limodzi.....it will prove it all.... Lulu is the Best....and very humble with his talent....Big Up Mr. MATHUMERA
Tikationeso nyimbo zanamadingo ndizongovera basi koma sungati upita ku live show ya namadingo ndikukasangalala njee...king of live show ndi lulu ndinyimbo zake zabwino.... Lulu ndi humble guy Jah bless Lulu
Amwene anthuwa or atadana sikuti apangitsa kt adane ndi amalawi ai koma namadingo ndi amene ali very stupid chifukwa choziva kukoko lulu ndi munthu odekha kmanso kuyimba amatha
I believe they are all musicians and all are Malawians, Why should we waste time with things that wanna not help us?? Let's make them become best friends than before..... tikhale anthu achikondi tisamasonkhezele nkhani ayiiiii....ndi udindo wathu kulanditsa ndeu anthu akamamenyana, ndikuwayanjanitsa... Let us be like Jesus Christ... Philadelphia
🤣🤣🤣🤣🤣🤣Lulu olotaimba guitar ndi Mano 🤣🤣🤣awe ndaseka anyway Lulu he is the best I still love his old songs and I love his dunce tiganize nampula itavuta tikutchola timadunce
Namadingo ndidolo posatengera kt oyambilira kuimba ndindan nama alindiluso even kunja akuziwa pomwe saona hedge lulu mukumuziwa kwa mwenyekondo ndi kubangwe kawamvula basi aaa
Zimangovuta azathu akunja amakonda ma Artist, Mikangano umabwelesa udani.... Thus why Upcoming Artist called Chris Matekenya , He said on his quote “I think music in itself is healing. It's an explosive expression of humanity. It's something we are all touched by. No matter what culture we're from, everyone loves music." #tag ~ Chris Matekenya
Lulu Is a matured guy then he shouldn't allow every Jim and Jack to disturb him We know the way namadingo started his career and how he was supported If anything akanakhala munthu ozichepa .so he can't learn to humble himself he will humiliated Sizofuna zake
The problem of being a judge who's already prejudiced, this TH-camr is like that, Honestly speaking namadingo is a talented artist, so is LULU, both of them are also too pompous, that's the undeniable fact.
Komano tikatengera mmayimbidwe Lulu ndi dolo kwambri. Komaso Namadingo wayamba liti kuyimba ali pa chipasula iyeo amamvera nyimbo dza Lulu nde Lero akukwera mtengo
Dwaa samanena LULU if you follow bible thats a pure bible story there is no any kind of diss in that song and when you talk about zaku BICC Lulu ignited the fire he was the first one to answer and kukhala pafupi ndimunthu its a context of literature sikuti kukhala pafupi in physical appearance anyway LULU ndi dolo
So it means such stuff is everywhere. In Zambia too there is much talk about Yo Maps and Chile One, Mr Zambia.
The only difference though is that these guyz do not go public word-stoning one other but it's the general public that somewhat promote or proliferate the so called competition, earning themselves a name: "THE DISCIPLINARY COMMITTEE"
In the world of sports it's 'Ronaldo or Messi'
Hahahaha .... Am happy to have you brother from Zambia
Lulu is a Legend......to those who follow Lulu and Namadingo you have to listen nyimbo imene these two anayimba limodzi.....it will prove it all....
Lulu is the Best....and very humble with his talent....Big Up Mr. MATHUMERA
Lulu ndidolo kwambiri pamayimbidwe,,,very humble person
Lulu ndi dolo
Namadingo ndidolo
Tikationeso nyimbo zanamadingo ndizongovera basi koma sungati upita ku live show ya namadingo ndikukasangalala njee...king of live show ndi lulu ndinyimbo zake zabwino.... Lulu ndi humble guy Jah bless Lulu
Ngat kwaine Magnificent Matchere.....ondikonda amandtchura kut GINTY....Lulu ndidolo kwambili komaso ozichepesa keep it up Lulu...
I like the way lulu answered namadingo
Wosendi Malawi komaso wose ndimadolo sitikufuna athuwu adane Ayi Amen🙏🙏🙏🙏
Amwene anthuwa or atadana sikuti apangitsa kt adane ndi amalawi ai koma namadingo ndi amene ali very stupid chifukwa choziva kukoko lulu ndi munthu odekha kmanso kuyimba amatha
I just like how this guy called lulu xpress himself to the entire Malawian nationa. Lulu v machine!!! Music that fit everyone-any age! 8:49
Kkkķkk inu namadingo sangafike pa Lulu .
Imeney nd mbuzi ya munthu
Bwana Sam luso lotambasula nkhani. ! muli nalo km vuto lanu ndikut pena mumaonesa mbali , ngat apa zikuonesa kut mwakwera Lulu .
I believe they are all musicians and all are Malawians, Why should we waste time with things that wanna not help us?? Let's make them become best friends than before..... tikhale anthu achikondi tisamasonkhezele nkhani ayiiiii....ndi udindo wathu kulanditsa ndeu anthu akamamenyana, ndikuwayanjanitsa... Let us be like Jesus Christ... Philadelphia
🤣🤣🤣🤣🤣🤣Lulu olotaimba guitar ndi Mano 🤣🤣🤣awe ndaseka anyway Lulu he is the best I still love his old songs and I love his dunce tiganize nampula itavuta tikutchola timadunce
Ganiza bwino tinyamuke 🤗
Uli ndi Mbali AISE.... NAMAFAN TEAM Doc Ovaya palibeso..... NAMADINGO ND G.O.A.T.
Namadingu ndidolo ine lulu olo nyimbo zake sindingavele
The guy is taking side Indeed in his analysis. Chibwana🚮
Lulu ndi machine, Namadingo kwake ndikulubwalubwa
lulu is very humble and amatha kuimba siwalero komaso
Lulu ndi muthu wamkulu and he is a humble man music anaiyamba kale enawa Ali ku primary std2 so ulemu umafunika
Komabe Lulu ndi faddah🔥
Uli ndi Mbali AISE.... NAMAFAN TEAM Doc O
Umatha
Anthuwa chilipo akulimbana si nyimbo zokha ayi
Lulu ndiwakuluzedi,ndimunthu amene SAdakhaleko ndinthawi yolimbana ndimunthu,ndiye uyu mukunuti namadingo wangokula ndi unyopoli basi ,ife nganganga pambuyo pa Lawrence khwisa LULU
I like the way he answered Namadingo
Muthu sakana kale Lake zikakhala6 zayenda.
Namadingo ndi mwana mu music industry. Lulu ndi dolo.
Anamadingo mwatani kod Inuo mungafike pa legend Lulu
Kuyimba kulingati politics ife timangomvela zalunja basi amalawi akatchuka always matama basi
Lulu ndi dolo👏👏👏eeeee straight up 🤟😅
Every one should respect legend Lulu nd lagend
Lulu is the best ever❤
Namadingo ndidolo posatengera kt oyambilira kuimba ndindan nama alindiluso even kunja akuziwa pomwe saona hedge lulu mukumuziwa kwa mwenyekondo ndi kubangwe kawamvula basi aaa
Sudziwa sakha kukhara chete lulu amatha kuimba ndipo ndioimba wamkulu mangalande imadziwa zalulu lulu ali pa map
Ineyo ndingofuna ndiyamike Lulu poyika post imeneyo cz wafuna chilunga mabodza ayi wachitabho am Eric from BT ndix
Zimangovuta azathu akunja amakonda ma Artist, Mikangano umabwelesa udani....
Thus why Upcoming Artist called Chris Matekenya ,
He said on his quote “I think music in itself is healing. It's an explosive expression of humanity. It's something we are all touched by. No matter what culture we're from, everyone loves music."
#tag ~ Chris Matekenya
Inu nkhani idzitha. Mufuna anthu atani?
Koma adah awaa amafusa timafuso tawo, tachibwana🤣🤣🤣
Lulu Is a matured guy then he shouldn't allow every Jim and Jack to disturb him
We know the way namadingo started his career and how he was supported
If anything akanakhala munthu ozichepa .so he can't learn to humble himself he will humiliated
Sizofuna zake
Lulu ndi founder i support him so much
Namadingo ndi kape kombili palibe chomwe akudziwa chitsilu
Ndakuomani muli ndi mbali😂😂😂
Lulu ndi legend basi olo Ena afune olo asafunei
The problem of being a judge who's already prejudiced, this TH-camr is like that,
Honestly speaking namadingo is a talented artist, so is LULU, both of them are also too pompous, that's the undeniable fact.
Lulu ndi more and it's ulemu ndiofunikadi mu industry imeneyi l love that point 👉
Dakter anavaya aixeee ,,, lulu ndi iweyo nonse ndinu ana ,,, pitani mkavine kwasakwasa uko
Lulu ndi machine kukhan yoyimba . Olo namadingo akulubwa lubwa pot anat munthu sayamika
I like it
That's why I like you Lulu
Kma bolani osadanitsa anthu
Lulu ndi amuna namadingo anagwa mu mpingo afuna agwetse lulu wachepatu size yake ndi faith mussah dadawa asiyeni ndi mtendele wao
Komatu zimangovuta...I wish they could work together
Doc anavia athu mungochedwa aaaaaaa za ziiiii
Lulu is the best than namadingo 💯
Lulu amaisata music
Lulu ndi Dolo💥💥
Namadingo mashin
Komano tikatengera mmayimbidwe Lulu ndi dolo kwambri. Komaso Namadingo wayamba liti kuyimba ali pa chipasula iyeo amamvera nyimbo dza Lulu nde Lero akukwera mtengo
A Namadingo aja 🤣🤣
Inu a Sam mavithaso ndinu amtopola mukukolezera zoyankhula za anthuwa kuti tizidanisa anthuwa Inu ndiausilu ndakuonani.
Big up Lulu
Lulu number one iwe mbambande
Namadingo ndiwamatama opusa nawo. Lulu ndi machine
Bg🎉🎉🎉🎉🎉
Namadingo Legend
Zikomo kwambili broh
Lulu is a legend than the so called Namadingo
Lulu ❤
Lulu amatha and dolo ine namadingo kuyimba kwake sindimakuona anatchukila ma mash uyu
Lulu ndi Biggy mwanayo muuzeni apeze size yake. Osamayamba zoti sangamalize kkkkkkkkkkkkkkk
Ndingokamba za chithuzicho tinayenela kudziwa kuti sikuti poti anali asanasukusule ndiye kuti amakapeza luso ayi
Anthu ambili amafuna kugwilitsa ntchito luso laanzawo omwe sanatchuke mwina mkutheka apa Lulu amafuna kupindulira lunso lanamdingo popeza anali asanatchuke
Lulu ndi mphuzitsi Namadingo angovomeleza basi coz choonadi akuchidziwa muntima mwakemo
namadingo ndi fana simwaona nokha wapusatu apa
Onse ndi madolo🎉
Lulu ndi mbambande awowo afuna akwiye anyanyale azipitaso Ku Zambia kkkkk
You need to refrain from being biased and a fan boy of one artist of another. Keep things balanced.
Thanks bro
Eya ndizabwino coz iyeyo Amanama kut sanakhalepo pafupifupi ndi Lulu yet waphunzira zambir kuchokera Kwa Lulu
Lulu💥
Lulu much love you kudzichepetsa kuli mwa iwe
Dolo ndi DAN LUU apa onse awa ma mafana
namadingo dzichepetse lulu ndi madala nzakoyo amajambula yekha nyimbo pamene namadingo amachita kujambulidwa ma audio
Uli mbali ya lulu iwe,,, akupasa zingati?
Sizabwino zimene anapanga apopo namadingo
Ulemu kwa lulu more 🔥🔥🔥🔥
Lulu ndiodekha sazipopa koma ada a Namadingo mmm kuzifila kumachuluka
Lulu ndi star
Lulu ndidolo
Lulu ⭐⭐⭐
Dolo ndi Lulu
Nyatwa, respect
Iwe ndikape ndakuona page apa umakamba zopusa ndikutulukaposo
Eya ndizabwino chifukwa Lulu nayenso ndi munthu amamva kuwawa
Ndizabwino ngati namadingo akuchita mwano
Ungatchuke bwanji omwe anayamba kale tiwapatse ma ulemu tiwayamikir
e
Lulu NDI dolo ...namadingo amangochita matama chabe ... empty tin make alot of noise
Zomwe ukunenazo ndizoona koma vuto ukuonesela mbali, nde sizikubeba
Aliyese amatopa ,but I have namadingo more than devil,but lulu umatha kuimba isanama
I hate namadingo ,sanayakhule bwino
Zaziii ukukamba iwezo akutuma kuti unyoze namadingo et
Lulu ndi one
Sizabwino zomwe anapanga Namadingo
wina asafepo apa
Lulu sanalakwe coz anamutopera
Dwaa samanena LULU if you follow bible thats a pure bible story there is no any kind of diss in that song and when you talk about zaku BICC Lulu ignited the fire he was the first one to answer and kukhala pafupi ndimunthu its a context of literature sikuti kukhala pafupi in physical appearance anyway LULU ndi dolo
Lulu is good
Namadingo ndi fana sangamake pa Lulu aja kwawo kulubwa lubwa basi atha ngati pat lekeni
Lulu ndi dolo kuposa namadingo
Namadingo ndi dolo