CHAKWERA MACHEDE WAKO CHILIMA KUKUYIKA PA MPANDO IWE NDIKUMUPHA UMAGANIZA BWANJI MBUZI YAMUNTHU PANYO PA MAKO WAVA CHAKWERA NDIPO SITIKUKUFUNASO AI IWE MCP YATHELA KU CHIKANGAWA
Izizi ndimaloto ndithu koma ndakhala ndikukutsata ndipo ndinapeza kuti iwe umakhala mbali ya namadingo koma maganizo amalawi salingati ako let him come out and see what malawi will say nthawi yamavote ikadzakwana, asamale tindalama taketo koma musamupusitse za ndale mudzangomusautsa mwana
Zeze..ndavomera
Ndalama zachepa sangakhale ndi 17 million
All the way we together
My favorite ❤
Very analysed story big up sam
Mpesa ndi number one
Ndinu mpesa?
@@sammalvitha yes filadephia
Chikondi cha pa abale chikhalebe
Mbiri yaketu ndy mwadumpha zambiri eeeee!! Kkk
Always on point bro .... Bravo bravo Mr sam mukubwela nyatwa mn
Exactly do something special
Kodi akulu skeffa chimoto wawina ma award angati chiyambireni kuimba
Inu amabodza khan za Matse Nd kell kay zodanazo nde kusokonezako
Alongo status not awiri
Ma a ward amenewo ndiogura kkkkkkkk kma abale Kelly k mpaka kuwina amaziwanso kuimba
Koma tiyiziwe ntchito yinayo kupatura kuyimba mwafotokoza zonse mulephele job yake
Nde Ma Sister Akewo Ma Ina Ao ATI Ndi Ati
Cuz Cross Ndi Imeneyo Tiwafuxe Ma Pahe Muuu
Sukuyizwa mbili yake
CHAKWERA MACHEDE WAKO CHILIMA KUKUYIKA PA MPANDO IWE NDIKUMUPHA UMAGANIZA BWANJI MBUZI YAMUNTHU PANYO PA MAKO WAVA CHAKWERA NDIPO SITIKUKUFUNASO AI IWE MCP YATHELA KU CHIKANGAWA
Nymbo zake szmandgwra mtima bolanso za Matse
Wawa
Oyimba akumalawi ndiye mwati alindindalama zingati ayi anyway 🤦🤦🤦💐💐
akanali osauka bola akanafikako billion
Kkkkkk
Zilibwino big koma ngati kotheka mutipasireko mbiri ya thomas chibade
Zili bwin ndipo pitilizan kutiberesela zabwn
Ukunena chulungamo.....
😂😂😂zosangalatsa ndithu koma za Ndalamazo ndaletse coz mukhodza kudziwa zomwe zili pa public zokha
Inesoza ndalamazo ndasusa
Cz mutha kuziwa zathumbamonkha
Izizi ndimaloto ndithu koma ndakhala ndikukutsata ndipo ndinapeza kuti iwe umakhala mbali ya namadingo koma maganizo amalawi salingati ako let him come out and see what malawi will say nthawi yamavote ikadzakwana, asamale tindalama taketo koma musamupusitse za ndale mudzangomusautsa mwana
17 million ndizaboza people with 17m they look poor than him try to find out his netwoth
Ndi dolo
Zachepa kwambili ndarama zo ka
Kumalawiko zinthu ndizovutadi eti?
All the way we together ❤