According to my decision, I SALUTE Lulu he is the best humble intertainer in music industry, he is a man who accepts the defeat without talking too much, but he also receives FAVOURS from God depending on his behavior. You are really a legend.
How can you copare Subaru and BMW.... Team Lulu, as far as I understand panopa I like Namadingo, koma Lulu it's a greatest of all time. Lulu ndi bwana pamene Namadingo ndi mwana
They are both legends but not historical or generational legends yet. I agree with Namadingo on this. These are two very talented musicians but you have to be real when you come to the definition of legend. Legend transcends and encompasses decades of preeminent work and name recognition in music industry! It’s stupid for them to even argue over this. They don’t even begin to be considered “living or generational legends” at this moment!
Lulu musiyeni pa mbali iye ndiozindikila salankhula mwa chibwana pomwe Namadingo ndi mbuzi ya munthu yotamika yoyerekedwa koma zoti zafika pa LULU aiwale
Legend suzimveka wekha, amaona okha mmene udayigwirira ntchito anthu, ndiye lulu ndi legend musamumvere Dr Namadingo, kumene akupangako ndikupereka ulemu kwa lulu chifukwa akudziwa kuti ndi dolo koma Ali pa denial chabe 😃😃😃😃
Ine sindikonda nyimbo za namadingo ai km lulu munthu wamkulu komaso ndimafuna nditawonera interview yake zikomo kwambili sam mavintha ndimakunyadila potiziwutsa Khan za malawi
Thank you so much Hawah Tomorrow morning ndiponya another video imene mukhale ma interview a anthu awiri onsewa .. and i will give a shout out to you .... . 🤗🤗💕
Kunena kuti wina satha kuyimba pakati pa Lulu ndi petience nkuzi namiza, ose amath kwambiri. Inde ndi zowona kuti petience ali ndi advantage yotha marketing kuposa mzake koma limenelo so vuto lomwe anthu kuno ku Malawi alinalo. Chikusiyana kwambir pa awiriwa ndi personality, Namadingo ali ndi kuzimva, anthu amudziwa lero pamene watchuka ndi secular koma ndi mene aliri sikuti anasintha, pamene Lulu naye ndi wo dekha kuyambira ndi kale. Kuzipopa kwa Namadingo Kuma tulutsa nsanje mwa anthu ndipo olo atapereka professional advice kwa artists wina imawoneka ngati mwano maso mwa ma fans.
Mu nkhani yoseyi kuyambila pa chiyambi mpakana pamathero olakwa ndi namadingoyu komaso mukafunsa za dolo PA awiliwa dolo ndi Lulu kusiyana kwa udolo wawo tsopano Lulu anadziwika chifukwa chopeka nyimbo zake pomwe namadingoyu wadziwika chifukwa choyimba nyimbo za anthu ena ine ndiye olo nyimbo imodzi yomwe ya namadingoyu sindimayidziwa nsaname koma pomunyoza Lulu sitingadabwe naye Tiana ta satanic ti ndichoncho timakhala tokula ntima ndiye usataniciwo
Akulu akulu zomapanga compair zi muzipereka maudani kwa anthu aliense Ali ndi okonda wake. bwezi simunafuse fuso lakuti opambana ndindani maudani kunalibe
To be honest Lulu ndikutali sitinganutse ndi Nama! Please tiyeni tizizichepetsa kuti tithandizane ,koma utm isanyasisepo nyimbo ya Lulu chifukwa chotathauza chake nyumbo ija was not thi satanic utm!!!!
Doc anavaya!!! lets give credit were its due at the same time Lulu is also a good artist
Both have a smooth voice and with me here in Zambia, l salute both of them.
26 not.. B MNn m❤
Kid oioiu
According to my decision, I SALUTE Lulu he is the best humble intertainer in music industry, he is a man who accepts the defeat without talking too much, but he also receives FAVOURS from God depending on his behavior. You are really a legend.
CORRECT
To be honest Namadingo ndi moto wamalasha olo mutatani sizikutigwedeza Namadingo umakwana
Zodekha zawozo kwawo konko
pankhani yozichepetsa Lulu ndi number one, koma tikanena za nyimbo Namadingo ndi international artist 💪💪🎶
Anzathu maiko ena oyimba amakondana ndicholinga chopititsa patsogolo luso loimba , amalawi tigwire manja, lulu ndi namadingo onse ndi superstar, ndi ofunika kumapanga colalation ndi anthu amaiko akunja otshuka osati kumalimba.
Namadingo has the best smooth/silk voice, no doubt about it. The guy has the confidence too
Lulu is the best.... He is humble in everything just like Sam smacks....... Keep it up Lulu
How can you copare Subaru and BMW.... Team Lulu, as far as I understand panopa I like Namadingo, koma Lulu it's a greatest of all time. Lulu ndi bwana pamene Namadingo ndi mwana
Mau amzeru
They are both legends but not historical or generational legends yet. I agree with Namadingo on this. These are two very talented musicians but you have to be real when you come to the definition of legend. Legend transcends and encompasses decades of preeminent work and name recognition in music industry! It’s stupid for them to even argue over this. They don’t even begin to be considered “living or generational legends” at this moment!
Mmmm NAMADINGO
Mukudziwa kuti lulu adayamba kuimba liti? If u say skeffa ndi legend why not lulu? Lulu anayamba kuimba kalekale ngati achina skeffa
iweyo ukukamba zoona, this was wat doc meant not what the fanz were insinuating
My favorite musician Lulu very humble man
Lulu is the best artist namadingo he is still young in music industry
Lulu musiyeni pa mbali iye ndiozindikila salankhula mwa chibwana pomwe Namadingo ndi mbuzi ya munthu yotamika yoyerekedwa koma zoti zafika pa LULU aiwale
aaaaaaaaaaa Namadingo amanama ngati. infact amanena zoona , Lulu si legend is in making, kukhala legend sichifukwa choti amaziwika nde ndi legend
Lulu he's legend ever we can't compare him and namadingo
My Brother Namadingo be Humble please,I'm one of your fans so please don't disappoint us
Lulu ndi akatundu pamaimbidwe sitingafanizire ndi mthumbidwa multi Namadingoyo💪💪💪💪
🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Namadingo he's legend ever we can't comparer him and lulu🎉🎉😂
Your presentation is partial, you're leading us to judge that Lulu is best
Lulu ndi legend, Anamadingo olo mau ochita kubera kwa Lulu nchifukwa amanena kuti aphunzira zambiri kwa Lulu
Lulu ndi machine
Paziko lapasi parib dolo
Team Lulu since day munthu ozichepetsa team Capetown 🎉
Lulu ndi dolo mbali zose mwachidure ndiodekha Lulu thanks for that
Of course Lulu ndi legend koma Namadingo ndi International Artist.
International ya Zambia?
International wakuti inu u think ku south africa amavela nyimbo za namadingo?
Onse ndi madolo, Patience amatha Lulu nso amatha, ndipo palibepo udani, koma anthu mumakokomeza nkhani.
Legend suzimveka wekha, amaona okha mmene udayigwirira ntchito anthu, ndiye lulu ndi legend musamumvere Dr Namadingo, kumene akupangako ndikupereka ulemu kwa lulu chifukwa akudziwa kuti ndi dolo koma Ali pa denial chabe 😃😃😃😃
Ku mbali ya mayimbidwe Dr Namadingo ali kutali kwambiri kwakuti tingadzayambe kumuyerekeze ndi Lulu chifukwa Lulu ndi machine
Ine sindikonda nyimbo za namadingo ai km lulu munthu wamkulu komaso ndimafuna nditawonera interview yake zikomo kwambili sam mavintha ndimakunyadila potiziwutsa Khan za malawi
Thank you so much Hawah
Tomorrow morning ndiponya another video imene mukhale ma interview a anthu awiri onsewa .. and i will give a shout out to you .... . 🤗🤗💕
@@sammalvitha Thacks so much Sam malvitha TV ndikhala ndikudikila zikomo
Team Doc Namadingo even in my computer/phone you can't find music ya Lulu
Lulu ndi number one pa zonse pa ine amakwana
pa Lulu timacedwapo ife MACHINE
Kwaine lulu namuziwa ndili mfana nyimbo zake ndiye doc eeee basi zaziko izi
I love both of them, Doc anavaya
Kunena kuti wina satha kuyimba pakati pa Lulu ndi petience nkuzi namiza, ose amath kwambiri. Inde ndi zowona kuti petience ali ndi advantage yotha marketing kuposa mzake koma limenelo so vuto lomwe anthu kuno ku Malawi alinalo.
Chikusiyana kwambir pa awiriwa ndi personality, Namadingo ali ndi kuzimva, anthu amudziwa lero pamene watchuka ndi secular koma ndi mene aliri sikuti anasintha, pamene Lulu naye ndi wo dekha kuyambira ndi kale.
Kuzipopa kwa Namadingo Kuma tulutsa nsanje mwa anthu ndipo olo atapereka professional advice kwa artists wina imawoneka ngati mwano maso mwa ma fans.
Lulu is the legend ✨
Lulu he's the best regards singer namadingo his nothing in industry
Namadingo ukaoneka Ngati Muthu wabwino Koma ndiwe chisiru ndipo ulibe nzeru iwe ungamupose lulu maimbidwe Mutu wako suyenda bwino eti ungamuphunzitse lulu umadziwa chani ulemu ndiofunika wamva umakhala ukunyoza anthu ena iwe ndindani mbuzi yamunthu iwe eti auncle lulu timakukondani mumatha kuimba musakhumudwe ndi namadingo alibe nzeru kucokera Kuno kuthyolo thekerani fifity miles lulu ndi otchuka zedi tsogolo jdiliona ndilowala ND lotheka
Doc & Lulu they are not enemies but we try to create it. Doc & Lulu onsewa ndi ma dolo basi
Bodza Lulu ndi fire 🔥🔥🔥 🚒
@@lameckkanga4090 that’s your opinion boss. Unfortunately I don’t listen to their music 🎶 at all.
Doc anavayaa!!!
Doc tsimngayerekedze ndi Lulu Doc anavaya
dolo ndi lulu palibe anagayime kunena za lulu ndiozichepesa odekha sindinamumvelepo akukangana ndi ndi anzake .thats a legend
Lulu anakhoza ndi machine omanga ndi mawaya
Lulu Nde Dolo man,enawo angochulutsa zo lubwa lubwa
Ndi munthu oipa amazitgenga ngati ndi ozindikira koma palibe ,lulu ndi munthu wofasa, end mulungu azmudalitsa Lulu
Lulu is the best❤❤❤
Lulu number 1 than namadingo
Komatu ndayiwona mochedwa iyi kodi mukankhilanji galimoto yosayenda Namadingo kusiya ya 1 kick Lulu?
Aaaaaah inu ndiolephera inu basi mngokharira against aaaaaah zaziii Namandingo si level yanu,,, Lulu nayeso nd doro
Namadingo akuyenera kulemba mawu woti leka Kwa Lulu chifukwa chifukwa ndipame alipo iye
Munthu kuimba nyimbo za anthu ena ndiye kuti kuziwa kapena kumakhala kusowa mfundo zopekera nyimbo?. Lulu ndi legend
Lulu Alaways Is Humble Guy And I Never seen Guy Ĺike Lulu Iwe Namadingo Stop Insulting Lulu For Nothing Utaya Thawi Yako Pachabe
Lulu on point,💪🏽💪🏽🔥🔥
Lulu number one
Udolo amakuwona ndi anthu osati wekha kunena monveka bwino dolo ndi Lulu
Lulu ndi star mapeto adolo
Dzikomo poonera video iyi 👏👏❤️❤️
Chonde pangani subscribe 💕💕💕
Chitani like vide iyi💖💖💞
Ok
U legend suudziveka wekha koma anthu , APA wina akudziveka u legend
Lulu it's my artistic
Dolo ndi lulu osati amenewo amangotithera data za ziii pano ndipo mnaleka ndiku danloder kumene 😂😂
Mu nkhani yoseyi kuyambila pa chiyambi mpakana pamathero olakwa ndi namadingoyu komaso mukafunsa za dolo PA awiliwa dolo ndi Lulu kusiyana kwa udolo wawo tsopano Lulu anadziwika chifukwa chopeka nyimbo zake pomwe namadingoyu wadziwika chifukwa choyimba nyimbo za anthu ena ine ndiye olo nyimbo imodzi yomwe ya namadingoyu sindimayidziwa nsaname koma pomunyoza Lulu sitingadabwe naye Tiana ta satanic ti ndichoncho timakhala tokula ntima ndiye usataniciwo
Lulu ndi machine ❤❤
We love lulu
Doc international artist 🔥🔥
Namandingo ndi wakwaya zoimbaz
Tasiilen achinalulu omweo chifukwandiye namadingo wayesesatu kuti ankhale ngati koma😝😝😝😝☹
Lulu ndi ngwazi
Lulu mulungu anamudalitsa Ali wangono zoyimbazi amatha
Clearly eni channel awa ndi a Lulu.
Lulu ndi fire 🔥🔥🔥
Akulu akulu zomapanga compair zi muzipereka maudani kwa anthu aliense Ali ndi okonda wake. bwezi simunafuse fuso lakuti opambana ndindani maudani kunalibe
Lulu ndi best all time
Namadingo ni best pa Africa
Lulu is the best than namadingo
Onsewo ndima legend palibe zot winayo alibe khalidwe
Iii kaya koma ine nyimbo za onsewo ndimanvera koma za lulu zowerngeka zomwe ndimanvera
Mthawi yambiri mdimanvera za namadingo
Lulu amatha doco azichepetse basi
Lulu ndi wa one Malawi music 🎵
Mayimbidwe lulu hi Is the legend
Lulu ❤️
Lulu is the legend
What I know is Doc anapita ma levels atali atali...koma kuzoyimba onse amatha
Ndamaliza kuwenga may comment onse zaonesa kuti lulu nd akayundu omanga ndimawaya 98%😅
Doc Anavaya,
Lulu ndioyimba wa luso namadingo kutali tali nd Lulu
Namadingo sioyimba or ND driemo sangamache
LULU ,
He is LEGEND!!!!
lulu 🥰
Lulu ndi legend 🔥🐐🐐🙏
Lulu ndi one
lulu ndi legends
Lulu ngozichepetsa pitiliza kutero
Iwenso ukulakhulawe ndie wamabodza
Lulu ndiye oimba osati Namadingo .iyi si mbali yanu Anamadingo pangani zamalonda
Dolo ndi lulu man
Mwafotokoza bwino koma vuto mwaonetsa mbali kuti muli mbali ya lulu
Lulu is the best.
LULU ndi machine opangira machine anzake. Anamadingo mwaimbira kt? Nyimbo zake zomwe zija zobweleza za anthu zija? Iwe namadingo pita ku xool ukaphunzire kuimba sumatha iwe.musiye lulu apite chisogolo usamufookese iya
Thanks
Lulu ndi legend not docs Kodi namadingo umaimba chani
Lulu ndi dolo chimodzimodzi namadingo, koma mumawadanitsa ndiinu atolankhani ama tv opanda chiphaso
😂😂😂😂 Koma guys
Lulu ndi dolo, Tsogolo, kumalembe eeee
Lulu ndiwa studio...pa stage ndiwa ma off code....
I guess sound simuitsata. Tisakanganenanu
Lulu ndi Dolo!
❤
Lulu amatha
Mayaz namadingo ndi dolo
kodi namadingoyo ndindani? uja amayimba nyimbo za anthu uja, ndi amene mukumupanga compare ndi lulu yo, kkkkkkk namadingo aziombela m,manja lulu akamuona
🤣
Namadingo ndiwamatama amakhala ngt sazafa ndalama is nothing mn kumwalira lelo zimenezo zilibe ntchito MN anamadingo muphunzile kulemekeza anthu
Ndipo ali nkuyankhula mong'anduka