KEEP IT UP BROTHER ALEXIOUS KÀMANGILA .WALKING IN THE FOOT STEPS OF OUR LORD JESUS CHRIST TO ƁÈING LÌGHT OF THE WORLD AND BEING SALT OF THE WORLD.WHERE THE SALT HAS LOST ITS TASTE .THEN THROW THÄT BAD SALT AND PUT NEW GOOD SALT.REFER MATHEW 5 VS 1 TO END AMEN.ZÌKOMO.KWAMBIRI ABWANA ATHU.AMEN
Yes you are young, but in your mindset is big, keep it up bro, freedom sikhala mu anthu 100 koma awiri atatu up to 5 persons, then kenako odyelera ndi ambiri, GOD BLESS YOU
I think you don't know what you are talking about kumbali ya police aise stick to what you know police officer are being killed what do you say about that??
The day he talk about Chilima mnachoka naye chidwi, why talking about the dead while we have corrupted president, ngati ndi dolo athane ndi nduna zakubazi osati the late SKC
Alex and Denis is the young men generation we need as a country
Muthu wazelu kwambili big up mupitilize ku yakhula chilungamo❤❤❤
KEEP IT UP BROTHER ALEXIOUS KÀMANGILA .WALKING IN THE FOOT STEPS OF OUR LORD JESUS CHRIST TO ƁÈING LÌGHT OF THE WORLD AND BEING SALT OF THE WORLD.WHERE THE SALT HAS LOST ITS TASTE .THEN THROW THÄT BAD SALT AND PUT NEW GOOD SALT.REFER MATHEW 5 VS 1 TO END AMEN.ZÌKOMO.KWAMBIRI ABWANA ATHU.AMEN
God shud continue protect U🙏🙏🙏🙏🙏
Good stuff son of Malawi. Keep it up.
❤❤❤❤more fire Alexious
Osachedwa kutsegula u tube chanel ,big up comrade.
Yes you are young, but in your mindset is big, keep it up bro, freedom sikhala mu anthu 100 koma awiri atatu up to 5 persons, then kenako odyelera ndi ambiri, GOD BLESS YOU
😮 Well spoken we've lent a lot. For sure Zikhale is gone to mining to steel.
Men of my future kamangila and Denis nkhandwe ambuye tiveni kulira kwathu
Lawyer wagulu wang'amba mosaphethira kuno bravo comrade ❤❤
Alexious you're not alone i know God have purposes to you and malawians, osaopa,osatopa this is Democratic country
Ndpo anaaikaso apolisi anzawowo pa chiopsyezo 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
That's why the commissioner of Southern Malawi police has denied the Older from above, amadziwa malamulo
Whistle blower Number 1,
One Malawi one nation!
🎉🎉🎉🎈
Salute. Genius bravo ❤❤❤
You are great, man
Brother I need your help anthu akufuna kulanda property yanga I don’t know how can I get cominicate with you
Zikomo kwambiri kamangila I want you to become a president of Malawi you and Denis my hope is
Timakukondani akamangila koma musilangula chichewa chifukwa siose adapita kusukulu ❤❤
Big up Kamangira,
Amen brooh
nanga khani ya ku congo ija mukunva bwanji kumbali yanu bwana ana anga mulidwa zoti ampedwe
Chichewà please
Atambwari sametana, that's why those top politicians can't speak against a system that benefits them most.
Your stronger person
Bwana waine ndevuzo kapunguleni kkkk
Ulemu wanu boss man
Guys mwampanga divert munthu bwanjiso? Kamangira tazisiya za mpira zitae
Auzen anthuwa akupanga chibwana akuwona ngat abwana awo kudzachoka adzawaonanso ...akuputa fire kwa anthu ,avulazitsa azibale awo
Kodi pano mukuimilabe anthu ku court?
Mumakwana
Kodi milandu ya Bushiri munganenepo chani chilungamo chilipo
Kunalibe ku malawi ngati izi munthu olimba mtima kunena molimba mtima ma court mosaopa, Ambuye APITILIZE izi, mcp chipani choipa
Dziko lowola ili ndipo losasililitsa olo pang'ono.
Chakwera ndiwakupha waombera nzimayi nkono
Koma ndalama zamisonkho zikatoleleldwa ndi MRA zimapita ku account 1 ndalama zomwe boma likulephela kugula mankhwala mzipatala kulephela kugula feterizer fuel chilichonse palibe chikuyenda mboma lomangoyenda ngati mphepoi kulikose kumangopita zikungotapidwa chithumba chaphweka usogoleri kulibe
Anyways but mcp is more corrupt ever