Very great massage from munthu wa mkulu, comrades unite please. Do not allow division amongst yourselves. Malawi Ali pamoto uyu, tiomboleni, timakukondani, gwiranani manja,
More fire Mr Kamulepo we need people like you to strengthen Malawi young battalion indeed we're coming from far thanks for your good advise to young ones. Please burn the fire we are tired to this party kuba kuba kuba without thinking about the poor . You're the first politician feeling sorry for the quallel of our activists we salute you Kalua 💪 Thanks God bless you
Malangizo abwino Bwana Koma don't take time to stand up and support them Nthawi ikutha my fellow Malawian alimumavuto We need more people like you koma tikufuna action I wishing MALAWI FIRST kukhala chipani osat gulu kapena bungwe. ViVa Malawi first Viva ViVa The DC President oyamba Wa anthu osauka M'Malawi ViVa!!!
That's a good advise, we trusted them and many of us were behind them, what divided them were just rumours and not genuine stories. We poor Malawians are very worried bcoz of this improper division among them. How can this country go without strong freedom fighters. We trusted freedom fighters a lot bcoz we don't have strong opposition that can fight for poor Malawians.
Comrade kaluwa times its now... come and help us please .u want politicians to destroy this country cause of politics . this its only malawi we hve ...
Time to join the protest is now Mr, remember there's a word saying muvi oyang'anira suchedwa kulowa mmaso, so wat are you waiting for!?. Time to remove the dancers is now!, you wanna eat the meat yokuphaipha kale ndamzanu?, Nonononono
Dad Kamulepo munakomana ndi mikwingwiluma mu one party system timakumvela pa Channel Africa palichani apa . Alankhuleni anyamata athetse kusiyana maganizo
Inunso a dpp simukutithandiza ayi nthawi ya Joice Banda munangotolanso boma Mvuto simukufuna kumapanga campaign mukudikira malawi first inuyo kumangokangana basi
Muli mfundo muganizo lanu, koma mukuphetsa aMalawi ovutika kumudzi, mukamati simungadzuke panopa mukudikira anthu afe angat ndi njala? Kod kalindo akanaphedwa kundende kuja zikanacita bwino, mukudikira campaign Kut muzadzuke? Mulibe cisoni Mene anthu akufera mzipatala? Why can't you rise now to serve poor Malaŵians? Mukati simukufuna kuonekera panopa what do you mean, are you coward? Rise now to rescue poor Malaŵians if not ndibwino kukhalabe cete conco.
Very great massage from munthu wa mkulu, comrades unite please. Do not allow division amongst yourselves. Malawi Ali pamoto uyu, tiomboleni, timakukondani, gwiranani manja,
More fire Mr Kamulepo we need people like you to strengthen Malawi young battalion indeed we're coming from far thanks for your good advise to young ones. Please burn the fire we are tired to this party kuba kuba kuba without thinking about the poor . You're the first politician feeling sorry for the quallel of our activists we salute you Kalua 💪 Thanks God bless you
Zoona abwana kamulepo kaluwa my allah guide and protect all the time l love you chifukwa chauthenga omveka bwino🇲🇼🙏🙏
Thanks mr kamulepo kaluwa we need such people anthuwa nkhani ndiyakut akhale pansi akambilane chifukwa vuto ndilot akufuna wina awayitanise pamene wayamba nkhani ndi munthu wina ndiye ndizovuta kut amene sakuziwapo kanrhu atitanise anthu bila amene akuziwapo kanthuwo plus umboni aitanise olakwawo nkukambilana zikhoza kuchita ubwino kwa amalawi
God might be blessed for your wonderful message to come to the public encouraging and advise our comrades in Malawi first
Powerful massage mr kaluwa wish to you
Malangizo abwino Bwana
Koma don't take time to stand up and support them
Nthawi ikutha my fellow Malawian alimumavuto
We need more people like you koma tikufuna action
I wishing MALAWI FIRST kukhala chipani osat gulu kapena bungwe.
ViVa Malawi first Viva
ViVa The DC President oyamba Wa anthu osauka M'Malawi ViVa!!!
That's a good advise, we trusted them and many of us were behind them, what divided them were just rumours and not genuine stories. We poor Malawians are very worried bcoz of this improper division among them. How can this country go without strong freedom fighters. We trusted freedom fighters a lot bcoz we don't have strong opposition that can fight for poor Malawians.
Powerful message Mr Kamulepo Kaluwa for your encouragement for the Malawi first.
Big up Mr Kamulepo kaluwa
The long awaited President to be......
That's nice massage to you Guys on Malawi first keep it up Respect
Thank you bwana kamulepo for encouraging these boys ....iam also behind them
😂😂😂 Munthuwamkulu kuyankhula, more fire Kamulepo
Powerful message very very powerful Mr kamulepo
We need people like you Comrade Kamulepo Kaluwa❤❤💪🏽
Good Message ❤ Zoona big man
Imtianz from mangochi keep it up
Yaa olo atakambilana Ife uyu wowola pakanwayi sitikumufuna Ben
Thanks sir for ur advice
Niwewakwe turimomo anangolo amene munavera zikoli bwererani please chifukwa dictatorship is back tikuchokera kutari malawi josopee💪💪💪💪ndipo liyake pozachedwa chadula mbalaa kwambiri ngani ili spa ndiyopulumuza dziko Latu ma dictated nose tithana nau
Ma comrades imvani uthenga wa munthu wamkulu
You are hundred percent right Mr kamulepo
Redson Munlo ndi munthu wabwino komano akumvera maboza a chisiru Ben Longwe
Kuyankhuratu kumeneko❤❤❤
Nkhufi ya munthu iyiiii
Takuthokozani bwana Kaluwa powathandiza/komanso powapempha kuti ayanjane,ndithudi anyamata amenewa tikuwadalira
Amenewo ndiye mawu bwana anthuwa asadane akambirane asaumirane ntima dziko siliri bwino
Zoona kambiranani koma Ben Longwe achoke ndimunthu wa miseche osokoneza
Powerful message
Big up
Comrade kaluwa times its now... come and help us please .u want politicians to destroy this country cause of politics . this its only malawi we hve ...
Tiyamike ndithu
Thanks Mr chwe mwana chwe
Tabwerani mu joine mademo
Good msg big
Big man vuto langon apa ndindyel
Nthawi ndiiyiyi mkudikila chani 😢
Kamulepo mbuzi yamunthu imeneyi
Takunyadilani munthu wa nkuru polankhulapo mwasowa ndithu zikomo kwa mbiri
Greater
Mukakomana anthu adyela zimakhala choncho ,
Zikomo kwambiri bambo anga mulungu yekha akudaliseni uku ndiko kuyakhula zoona dii
Tayasan moto bwana tatopa ife
That is true mr kaluwa
Zauchisilu Pali zeru apa mbwelera zokhazokha
Kuwaudza mwamadyo
Komatu nkhanga zaona yasowa , a mtanyiwa zikutibwanji kumeneko
Koma mukuyang,anila anthu akufatu mdzikomu
Voice of the veteran..
Kulakhura kwabwino kambilanani anthu amakukhulupilani zedi
Perfect speech
Time to join the protest is now Mr, remember there's a word saying muvi oyang'anira suchedwa kulowa mmaso, so wat are you waiting for!?.
Time to remove the dancers is now!, you wanna eat the meat yokuphaipha kale ndamzanu?, Nonononono
Mawu amphamvu kwambiri
Zoona zake mau abwino zedi achilimbikitso kambilanani guyz
Kuyankhula komanga mudzi ,kwa munthu wankulu
Zoona bwana
For sure💪💪
Dad Kamulepo munakomana ndi mikwingwiluma mu one party system timakumvela pa Channel Africa palichani apa .
Alankhuleni anyamata athetse kusiyana maganizo
Zoonadi kupezeka pa Kwacha roundabout mmamawa sizocheza waziona mkuluyi nde imvani pempho lake guyz 😅😅😅
Nkhanga zaona suzowonaso pano zinapanga khungu
Inunso a dpp simukutithandiza ayi nthawi ya Joice Banda munangotolanso boma Mvuto simukufuna kumapanga campaign mukudikira malawi first inuyo kumangokangana basi
💪💪💪💪💪
👍
Muli mfundo muganizo lanu, koma mukuphetsa aMalawi ovutika kumudzi, mukamati simungadzuke panopa mukudikira anthu afe angat ndi njala?
Kod kalindo akanaphedwa kundende kuja zikanacita bwino, mukudikira campaign Kut muzadzuke? Mulibe cisoni Mene anthu akufera mzipatala?
Why can't you rise now to serve poor Malaŵians? Mukati simukufuna kuonekera panopa what do you mean, are you coward?
Rise now to rescue poor Malaŵians if not ndibwino kukhalabe cete conco.
Palibet mavuto odetsa nkhawa apa, ndipo mavuto akadza ndiku khala pansi kukambilana nde umodzio umeneo?
Its true
Kukulirana ntima kwachuluka sakufuna kugonjerana.
Don't be deceived Mr kamlepo kaluwa he is a deceiver! has ever he attended the demos ever since started them