Dziko la Malawi likuvutika ndi anthu omwe akuti ndiophunzira, to me qualification or education is a big mess for our politics in Malawi. These politicians calling themselves educated are the ones destroying our country
Callister she talks good vision of the future leading of people of God since He is the Loving father non come to live impoverish and others being so special
Akumupangira nsanje Gatrude muntharika ...mwagwa nayo che calister inu mwamuona lero peter kukalambako.....siyani mkazi wake ndi amene anganene zimenezo not you... Musanene zambiri apa muyaluka mayi... Komanso Chilima alibe mtima osokoneza ngati inu... So musiyeni time for him to be a President will come....osamuyipitsira mbiri chilima....ife taziwa kale its family issues kwa chilimako mungobisalilako ...mwalephera basi... Yhoooo!!!
Lero NDI 25 /6/2020 tavotaso Ku Malawi pa 23 June DPP mpungwepungwe pa ndala unayambira apa Ku DPP Pano Boma lapita Ku MCP mai uyu amanena zoona DPP yikanakhala yovera bwezi Pano chipani chilibwinobwino Ichi ine ndimakonda DPP for ever
Iwe callista ndiye nkholokolo ndithu,,,kodi watumidwa eti??ukanangolowa chipani chomwe ukuchifuna basi.wamanidwa banzi,,,,usatibowe.ngati Peter aimire mu 2019,,aimira on his free will,osati akukamizidwa.kufoila basi
Mai calista please if you lost save your mouth by being you. As chief and other members say I understand you mix family and politics. Please you re not normal at all. I am very surprised on you and wish you resign active politics
uyu Callista ndi chisilu kwambili ndichifukwa chake anaphetsa Dr bingu wa Mutharika ndimunthu opanda nzeru mumutu mwake muli nothing to be nothing very poor women
Mama on point...you real care for malawi
I can see alot of sense in her speech... congrats
Calling a spade by its name. I love the courage
She was spot on👌🏾
And her words came to pass. Look what is happening today?
this is fire baba
True madam calista mukunenazo Zoona nkhani ndiyoti Munthalika wakulisa now 85 mpaka pa mpando???? Hiyaaa azikapuma uku a kumwa thobwa
Good move mama
big up mama
Very true Malawi should wake up please
congratulations
Joab i want this mama in cruiser ✋
kkk koma kudziko lathuro kuli zinthu, big up
Dj play Mama by christopher martin
APA yinali 2018 Mai Callister akunena izi lero Boma lapita DPP kusavela eish
good idear
Good signal Mama
Mama athileni show anthuwooooo
I love her
Congrats mama
Timadziwa ndi kale kut Callista ndi wa UTM asatinamize
Musamanenere ndale mufuna anyamata anuwo azionongabe dziko osamukhomelera peter mutharika
Dziko la Malawi likuvutika ndi anthu omwe akuti ndiophunzira, to me qualification or education is a big mess for our politics in Malawi. These politicians calling themselves educated are the ones destroying our country
Mmmmmm lekan ndale mayi muzingopephela katolokayo
Ndinu abodza amayi simukalowa kumwamba(1)munasiya banja Alan( 2)Bingu anapha anthu kumpoto munalikuti mulindivuto malawi ali ndisoka
Koma mai uyo aliso ndi nzeru kaya a tonse amuganizila bwanji?
Yes sure osamangolubwalubwa apa hahahahah... Ulemu wanu mama
Zoona mama umbamvadi wakulu shaaaaa Malawi wanga
Xoonad ndipo am agree with her
Kkkkk...Mai wafuko lathu pitilizani kutimenyela ufulu wachinyamata
Zoona mai wanga.
The truth hurts.
Mayi wanga kuyankhula mopanda mantha akuti alamu awo awazulilira akuba ndi amene akwazokoneza maganizo
Mai mwalankhula chilungamo pitilizani
Go deeper mama…zandisangalasa coz amalawi tayamba kuwona
Chimwemwe Chimwaza kkkkkk family party
Callister she talks good vision of the future leading of people of God since He is the Loving father non come to live impoverish and others being so special
Malawi need the leader who is a man of God...a man who is inspired by God..aman who is guided by God..
Washington Dulla, you can say that again brother!
Chilungamo ndimwano
Zilombo etiii kkkkkkkk
Ine pazomwe zayankhulidwa apa sindikuonapo cholakwika chifukwa sananyoze mayiwa akungounikira zofunikira kuchita
Maiwa ndiokongola koma akungofunika kudzichepetsa kukayanjana ndi alamwawo
Amayi pelekani ulemu Kwa aramu anu chonde kumbukirani dzana munali kuti????
mukunveka masteni
Amayiwa akunena zoona muthalika walephela kuyendesa boma tili mumavuto akulu
Kkkkkk anthu akungolubwalubwadi basi...auzeni masten amve basi
Udani wanu ndi alamwanu usatikhudze
Patakhala anthu ochuluka otsata chilungamo ngati mayi uyu theradi Malawi asintha
that is malawi kkk
Akumupangira nsanje Gatrude muntharika ...mwagwa nayo che calister inu mwamuona lero peter kukalambako.....siyani mkazi wake ndi amene anganene zimenezo not you... Musanene zambiri apa muyaluka mayi... Komanso Chilima alibe mtima osokoneza ngati inu... So musiyeni time for him to be a President will come....osamuyipitsira mbiri chilima....ife taziwa kale its family issues kwa chilimako mungobisalilako ...mwalephera basi... Yhoooo!!!
Callista ali bwino zedi uyu uyu ine ndimafuna anthu otere mama simukulakwitsa
Gamers Republic ulemu wa mama ndizoona amalawi tikuyenera kudzuka.kutulo kodingati ifetikuvutikachonchi ana athu azvutikabwanji?
Vutonso kwathukuno chinyengo kwaoyendetsa chisankho
Anthu omwe anayambisa ulendo oika amalawi pamotp omwe uklephereka kuthimau
Ndale sungazimvetse
Apitala akapume amadala
Mai uyu anakamba zoona DPP lost an opportunity of holding on to power, only if they allowed Chilima to take over in 2019
I thing nkholo ndilimene limamulangiza mwana zoona
Lero NDI 25 /6/2020 tavotaso Ku Malawi pa 23 June DPP mpungwepungwe pa ndala unayambira apa Ku DPP Pano Boma lapita Ku MCP mai uyu amanena zoona DPP yikanakhala yovera bwezi Pano chipani chilibwinobwino Ichi ine ndimakonda DPP for ever
Now she has been vindicated the legacy of APM is in tatters now.
Zonama chipani chinazusa Malawi pasi ndi ndi MCP not DPP ndiye founder yanu ndiyiti
Mai uyu malo okomera ku gehena.
Mai adalankhula uyu
Kuno ku Afrika ngati kuli ma president wolephela mthalika ali pa no one
Amai muwanamiza amalawi chiyambi kuti athu asokonekele mitu munali inu munayankhula kuti apita akalamba komazoti munatilakwila amalawi mumadzi kodi saulosi chilima ndindaniso angakhulupilile zadziwika kuti ndinu zithumwa zotumidwa ndisatana munatizi apamwabwelaso komatchito yasatana muigwila muli ndimawonekedwe achipembedzo mphamvu yake mutaikana chilima akalamulila nyumbayanu osati malawi wakuba watipweteketsa kuti mcp ilamulile ndiinunomwe ufumu okakamila owooooo
Iwe callista ndiye nkholokolo ndithu,,,kodi watumidwa eti??ukanangolowa chipani chomwe ukuchifuna basi.wamanidwa banzi,,,,usatibowe.ngati Peter aimire mu 2019,,aimira on his free will,osati akukamizidwa.kufoila basi
Inu amayi chifukwa anakuthamangitsani ku Ndata farm.
Kod malemu munthalika anamwalura ndi matenda anji?anali munthu wabwino
Bp
Mai calista please if you lost save your mouth by being you. As chief and other members say I understand you mix family and politics. Please you re not normal at all. I am very surprised on you and wish you resign active politics
Iweyo, amunaako a Bingu anali asanakalambe, wayamba chibwenzi ndi saulosi kapena?
ZILIBWINO AMAYI AMAIAWI KUOPA KUFA ATHU AKUBA NDAIAMA KOMA SAKUMA NGIDWA
Auzeni mayi monga mayi obereka.Amadziwa Bambo a mwana ndi mayi .Mukunena zoona. Tilankhulireni mayi.
Told them truth
Muerte mukawafunse amuthalika muzanena mulamuwanu bodza
uyu Callista ndi chisilu kwambili ndichifukwa chake anaphetsa Dr bingu wa Mutharika
ndimunthu opanda nzeru mumutu mwake muli nothing to be nothing
very poor women
Chosamva chinava nkhwangwa ili mu mutu a dpp anapumunthidwa
😂
Chilima wake uyuyu wakuba, wabodza,wamatama, wankhanza kwa a zimayi yu.
Waboza iweee pitala mbava yohipaa chilima bomaa
Kkkkk zilombo zimenezo zatikwana zotibela ndalama ife a malawi didapenya pano
Mai mukapeza mpata mutiuze chinapha Bingu. Mai ngati Nkotheka mutiuze chifukwa cgani mukukakamira dzina la Munthalika?
Mayi wakuba katundu wa Malemu ku state house nthawi yomwe bingu anamwalira
Zaziiiii kuba kapena kutenga mesa ndizake zomwe
Mesa linali Banja, Nde umafuna asiye?
😂
😂