Choyamba inu mtumiki munthuyi iyi sinkhope yake yeniyeni nde musamakambe mofuna kuntchuka pot mwabwera ndicholinga chofuna kukamba chilungamo nde musamasokoneze chonde
China Yesu timaziwa navomeleza kt ndimwana wa Mulungu wamoyo koma kut ambiri aziti ndi Mulungu, ndi apa Chivumbulutso 1vs 17 akut mwachidule ine ndine Alefa ndi Omega. Ndiponso wamoyo ndinali wakufa koma taona ndili ndi moyo kwamuyaya ndipo ndili ndi makiyi a imfa ndi Amanda. Komabe zonsezi sizisintha kanthu tikamapemphera timazera mwa Yesu monga mwana.
Chapter chimenechi mwalembedwa zoti Yesu ndi Ambuye komanso mwalembedwaso kt Yesu ndi mwana wa Mulungu zomwe inu mumazikana mumati Yesu simwana wa Mulungu komaso Yesu si Ambuye, koma zili m,buku lomwe mukuwerengalo. Brother ndinu achiphamaso ongotsata zomwe zikupanga suit mchiphunzitso chanu
Agnes Katwela ndipezeni panambala iyi +27715528411 (Whatsapp) kapena muyimbe pa +27786868209 or ndilembereni pa facebook mungopanga search Elias M.Pemba,kapena email pa epemba3@gmail.com
Anakuuzani kuti yesu ndi mulungu ndani ????? Ife a Christu we don't say Jesus is God ..but he is the only loved son by God sent ...the Messiah ....the rest are just bogus
Well done my brother Allah guide you all the time
Tiziphunzisana mwachilungamo osati mopotoza mofuna kukondera mbali yomwe tikhulupilira
Uthenga wabwino wakuva wava osava sanave
ManshaaAllah
Shukran wa jazaakallah khairan brother Moosa Nowa
Baraka Allah fiki
Ndizoona
Balaka llah fiki
Choyamba inu mtumiki munthuyi iyi sinkhope yake yeniyeni nde musamakambe mofuna kuntchuka pot mwabwera ndicholinga chofuna kukamba chilungamo nde musamasokoneze chonde
China Yesu timaziwa navomeleza kt ndimwana wa Mulungu wamoyo koma kut ambiri aziti ndi Mulungu, ndi apa Chivumbulutso 1vs 17 akut mwachidule ine ndine Alefa ndi Omega. Ndiponso wamoyo ndinali wakufa koma taona ndili ndi moyo kwamuyaya ndipo ndili ndi makiyi a imfa ndi Amanda. Komabe zonsezi sizisintha kanthu tikamapemphera timazera mwa Yesu monga mwana.
❤
Like
Allah akbar! Uthenga omveka bwino
Chapter chimenechi mwalembedwa zoti Yesu ndi Ambuye komanso mwalembedwaso kt Yesu ndi mwana wa Mulungu zomwe inu mumazikana mumati Yesu simwana wa Mulungu komaso Yesu si Ambuye, koma zili m,buku lomwe mukuwerengalo. Brother ndinu achiphamaso ongotsata zomwe zikupanga suit mchiphunzitso chanu
Zikomo
Achristu timaziwa kuti yesu si mulungu koma inu asilamu mumalimbana ndi mafunso amene sangakupindulireni
Brother, moti simunamvepo akristu ena akunena kuti Yesu ndi Mulungu?
@@ChePemba .....tsekulani maso anu, palibe munthu adaona Mulungu, Mulungu yemweyo adatsika kudzera mthupi la munthu mkukhala pakati pathu, mchifukwa chake timati Mulungu wamphamvu zonse amene amachita chilichonse ndipo kwa iye mzotheka. Brother mukusowekera nzeru zauzimu, maphunziro a chisilamu simungamudziwe Mulungu olo mutaphunzila bwanji, funsani anthu omwe akusunga malemba (akhristu). Koran ndi buku lomwe siliphunzitsa zomveka bwino ngakhale nkhani zake sizilumikizana bwinoyi, brother landilani Yesu lero simudzakhumudwa pakuti iye ndiye njira ndi choonadi. Stop deceiving people
@@christophermanyamba5552 here is my WhatsApp number, please feel free to contact me brother. We can discuss any topic
Asallam tiku limbana nanu ndicholinga choti mukapulumuke
Sikuti akulimbana ndi anthu koma kuphunzitsana anthu aziwe choonadi
Nde funso langa ndi ili nokha mumati baibolo simau a Mulungu, koma mukugwiritsanso ntchito yomweyi ndiye tiziti bwanji pamenepa, chifukwa nkosatheka kukhulupilila mabuku awili ndiye kt ulibe posamila
Murungu ndimurungu yesu ndiyesu
Ngati yesu ali mulungu iye adamulenga ndani nanga mulungu amabelekedwa
Nanga disc ya malemba akutinji ndingayipe kuti ?
Agnes Katwela ndipezeni panambala iyi +27715528411 (Whatsapp) kapena muyimbe pa +27786868209 or ndilembereni pa facebook mungopanga search Elias M.Pemba,kapena email pa epemba3@gmail.com
😂 ASILAM athu opanda MZIMU wa MULUNGU mungaziew bwanji za ambuye?
😂😂😂 Akulu mwadyachani mpaka kumawanamiza anthu chocho anthu a opanda bvumbulutso😢😢
Ngati mukulupilila kuti yesu ndi mulungu tiyeni tipembe mulungu pakati paife asallam ndi akilisitu ationese chisindikilo choti osochela ndiuti oloñdola ndiuti😅😅😅😅 andu osochela yinu
masha allah .. bt y we can nt download ??
You can download it using snaptube or vidmate.
Balaka Allah Fiki
Allah Akbar
Allah Akbar
Alhamdulillah
Asilamu amapembeza chgawenga Muhammad,Sono ife sitilimbana ndzazigawenga,sitisatila kamasikin Muhammad,timasatila yesu wamoyo
Zukani chonde tsekulani maso musamapusisike ndichopeleka cha Sunday
Anthu osochela yinu simusalungamaso asallam akukuusani kuti mukapulumuke koma yinu mukukani kkkkkkkkkk simusalungamaso
Zosekesa kuzimvatu zimenezo 😂😂😂😂
Talk to Christian Prince on TH-cam
Anakuuzani kuti yesu ndi mulungu ndani ????? Ife a Christu we don't say Jesus is God ..but he is the only loved son by God sent ...the Messiah ....the rest are just bogus
Shelk mukunama ngat mukufuna kudziwa za yesu tiyitaneni for a debate plsss don't cheat people
Here is my contact details brother Nazombe: 265997614263, email: epemba3@gmail.com
inuyo perekani ma verse anu, apa sipongoyankha za mmutu