"Kudziwa choonadi" Malemba Akutinji?vol.1 By:Elias M Pemba

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 6 ม.ค. 2025
  • Kuyambira pamene Mulungu analenga munthu ndi kumusiya padziko lapansi,Mulungu wakhala akutumiza aneneri ochuluka ndi cholinga choti aunikire munthu ndi kumuonetsa njira yoongoka,ndinso njira imene ingamutengere munthu kuchionongeko.Ndipo ife a lero kuti tidziwe choonadi chimenechi,ndikoyenera kusanthula malemba mokwanira.Pachifukwa chimenechi,brother Elias M.Pemba akufukula malemba mwakuya mu ulaliki uwu.Tengani nthawi yanu mumvere ulaliki umenewu.

ความคิดเห็น •

  • @yahyaabbie9795
    @yahyaabbie9795 5 ปีที่แล้ว +2

    Nice work brother😊

    • @ChePemba
      @ChePemba  5 ปีที่แล้ว +1

      Jazaakallah brother

    • @JeemisHassan
      @JeemisHassan ปีที่แล้ว

      ​@@ChePemba
      11:18

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 5 ปีที่แล้ว +2

    Ndiye choonadi ndi chiti pamenepa popeza akuyankhula zopanda sense, Acts 9:10-16, 1 Cor 16:22, Rev 22:20, 2 Cor 12:8. Komanso mu Bible mulibe mawu oti allah, tikapita ku egyptian civilization tikupeza kuti allah ndi kamodzi ka timilungu tokufa (the goddess of the moon). Mulungu ndi mmodzi dzina lake ndi Yehova koma ali ndi ma title, Yahweh, Lord etc but not allah, ndipo Mulungu ngati Ali mmodzi sangakhale ndi ma book awiri, (quran ndi Bible), mu nthawi ya Noah, chombo chinali chimodzi, mu nthawi ya Yesu Moulumutsi ndi mmodzi yemweyo, Muhamad Bible silinamukambe.

    • @sharifsaidi6706
      @sharifsaidi6706 5 ปีที่แล้ว

      Try to learn more about meaning of Allah in Arabic. And utanthawuzire mu English or chichewaa. You will found the meaning

    • @christophermanyamba5552
      @christophermanyamba5552 3 ปีที่แล้ว

      @@sharifsaidi6706 ........allah mu English ndi God, ndiye the question can come kt which God? In Christian God has a name Yahweh or Jehovah. Ndipo iye ndi Mzimu, palibe angamuwone ndi maso mkukhala ndi moyo, inu asilamu mulungu wanu alibe dzina komaso si Mzimu ayi ndipo ndipo ngakhale Muhammad sadalankhule naye