Chakwera muthu oyipa iwe mbusa wantundu wanji wakupha iwe kodi mazibusa amakuphuzisani kuti uzipha chorengedwa ndi mulungu zimenezo amakuphuzisani ndani kuti muzipha athu chorengedwa ndi mulungu iwe crocodile mau amene unaphuzira kapena mau ati ambayibulu amene akunena kuti muzipha athu time is coming soon
Ndiye zaka 31 zo moyo wake umenewu.A Richard chimwendo Banda anthu apatchito tili pamavuto Zedi ndalama imene anthu tikulandila ikutha tsiku limodzi ndipo achibale Tikulephela kuwathandizako.Njala yakulatu m, Dziko muno
Those people are not forget good song continue brother
Lembani chichewa timve nawo, chingerezi chani chiri very deep olo Dausi sangamake.
Ilibwino kwambili 100/%
Good song ❤❤❤
Anthu a MCP including Gotani Hara amayenera kumangidwa kumwalira Kwa Chilima Koma days are coming next year they will be jailed
Bwana nyimbo munaswa iyi ulemu wanu bwana
@@MustafRajab zikomo kwambiri bwana wanga. Ndikulupilira mnapanga subscribe channel yangayi🙏
Chakwera muthu oyipa iwe mbusa wantundu wanji wakupha iwe kodi mazibusa amakuphuzisani kuti uzipha chorengedwa ndi mulungu zimenezo amakuphuzisani ndani kuti muzipha athu chorengedwa ndi mulungu iwe crocodile mau amene unaphuzira kapena mau ati ambayibulu amene akunena kuti muzipha athu time is coming soon
Powerful massage
@@BreciousMbalureMangeni thank you
Misozi yamunthu osauka imabweresa minyama padzikol tiyeni tikhal ngt ndfe alendo palib amadziwa zamawa guys thank u God almighty
sounds good brother
Nice song
Good song
Song nice😭😭😭😭😭😭
@@Hawa-k5q 😭
Nduna zasatanic presidentso
😭😭😭😭
Ndipoooo live kulibedi wamuyaya
Nsipo mulungu alange onse anatenga gawo pa imfa ya SkC ndi ena onse
❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉
Ett wapindulanji suzakhala muyaya president oipa moyo.
Dyera ndi ndalama zathu komatu kumwamba kuli Mulungu, Chikumbumtima chimapha
Mizimu ya anthu 9 kumwamba kulankhura pompano
Nice
@@JACKSONHULUWA-j2n thank you 🙏
Ndipo mpaka pano ine sindivetsetsabe
@@ElizabethMulinde Nzobvuta kumvetsa kwake 💔
Fire mabomba
Ndiye zaka 31 zo moyo wake umenewu.A Richard chimwendo Banda anthu apatchito tili pamavuto Zedi ndalama imene anthu tikulandila ikutha tsiku limodzi ndipo achibale Tikulephela kuwathandizako.Njala yakulatu m, Dziko muno
@@LilianKachala-yz2xfTingopempha Ambuye alowelelepo zinthu sizili bwino ayi.
MCP ndiyakuphakuyambila kalekale sichipanichochipanga sapoti iyi
Ifesositilola ayimpandotikutenga basi uonachakwela chakachino cha 2025
Koma pa imfa zonse mu malawi i.fa ya chilima nyimbo anyamata ayimba sabata lili lonse nyimbo zikutuluka
@@TakalaniGlenda Yekhayo tinkadali
M H S R I E P ✝️✝️✝️✝️ S K C.
CHAKWERA YOU ARE EVIL YOU WILL NEVER HAVE PEACE. MUNAPHERA NJIRU.
MCP NG'ONA NDI NG'ONA 🐊🐊
WELDONE NICE SONG ❤❤❤
Dpp mukuyesetsa
Nice song
Good song
@@0wenNkhambule 🙏