Chimwendo anka nyoza Late VP Chilima pagulu,kumusonkhano, ndiye anakonza zokumpha Chilima. Namalomba, wafunsa zowona, ambuye akutetetezenu nonse ndi Suleman.Rest with the Lord VP Chilima ✝️🙏🏾
Chi Sulemam ngati chilowelere a mwene, but one day in this cbember, ohooo😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮😲😲😲😲😲😲😲😲😲😲😲😳😳😳😳😳😳😳😳😳😯😯😯😯😯😯😯😯😯🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄Kasongo ye yeeeee😅😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂😂😂
Yes tikufuna anthu olimba mitima ngati inu mo fire tie naeni wado wado akudziwapodi kanthu asatipusise imenei ya cilimayi tili nayo nayo mpaka 2025 woo! Mcp ikutiona kupusa.
Violation of civil rights in the house of Parliament in Malawi is a joke, miss speaker defending the right for people not allowed to freedom express and freedom of speech is important for any minister don't violate their rights.
Namalomba ndi Sameer sulemani mumaimililadi amalawi osauka.🎉🎉🎉
Namalomba and suleman are the real honourable
That's for sure they are the Lion 🦁of Malawians
Anthuo ndima dolo hvy
Chi sameer ngat chilowerere amwene I love these bravo opposition guys mwabwera inuyo kkkkkk❤❤❤
Yomweyo galu iwe ❤❤❤❤❤❤
Very good Namalomba and Suleiman ,ndege ya kuchingawa.
This is a way to go Namalomba & Suleiman I really appreciate for the good job u are doing in Parliament 😂😂😂😂
Chimwendo anka nyoza Late VP Chilima pagulu,kumusonkhano, ndiye anakonza zokumpha Chilima. Namalomba, wafunsa zowona, ambuye akutetetezenu nonse ndi Suleman.Rest with the Lord VP Chilima ✝️🙏🏾
Ndipo zoona
Bravo zikubeba
Namalomba and Suleman ndima big boys a Dad
Namalomba and sulemana 🙏🙏🙏🙏🙏🙏 God bless you guys
Suleman ngat aduphe 😂😂😂😂
Kkkkkkk mtima umadumphatu ngat watch
More fire 🔥 big man we all love you namalomba ,
Ilike your channel bro umakwana kufotokoza momveka bwino 🙏🙏🙏
Anthu osaopa inuyo mumakwanila osawaopa ayi ❤️♥️❤️♥️❤️♥️❤️❤️♥️❤️
Very good a Bambo Nalomba that's a fact and a true thing.
Wado wado pakana wapuma mwabakha bakha yomweyo namalomba iponde fada!!😂😂
😂😂😂😂
Wonder Msiska akonzeke...
True leader namalomba
We lovie namalomba and i wish he have been the state President of malawi
God Bless Malawi 🇲🇼 Amen 🙏
Fadagadi .iponde fada .sitili tonkha amalawi koma alipo lije samiear ndi namalomba .dpp❤
Namalomba fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Namalomba keep the fire burning osaopa
Chi Sulemam ngati chilowelere a mwene, but one day in this cbember, ohooo😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮😲😲😲😲😲😲😲😲😲😲😲😳😳😳😳😳😳😳😳😳😯😯😯😯😯😯😯😯😯🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄Kasongo ye yeeeee😅😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂😂😂
Alikuti wonder😂😂😂😂😂 msiska akambepo mbali yake kma namalomba respect ndiye suleman yoo ngati ailowereretu wamuwawat😂😂😂😂
Mr namalomba and sameer sulemani tikupemphelerani kuti pamene mwaima pa chilungamo pasapezeke ng'ona iliyonse yofuna kukusokonezani chifukwa mukuimila amalawi ambili mulungu akuthandizeni pa nkhondo imeneyi akupatseni kuthekela kuti choonadi tichidziwe zikomo,
Achimwendo mwakumana nazo kuipa nkhope ND mtima omwe unatichosela chiembekezo Cha amalawi zopusa basi
Suleman anasala pang'ono kuigula ndewu imeneyi
Sameer sulemani namalomba osaopa osatopa osafooka tiziwe chilungamo basi god bless all
Bravo Namalomba ,Suleman
Namalomba wanena bwno osamabisa zikhalakwika anachita kuigweza dege
Kkkkkk km ukuku kkkkk simungatiitaneko km 😎
Mary Navicha .Sameer suleman .Namalomba..anthu awa akuwapatsa pain mu parliament
One more Jolobala I like this lady too
😂😂😂😂😂😂 DPP woyeeeeeee
Kwachemaaa, anyway,chilungamo chizadziwika pompano ndithu
Kungopwisira zindalama zonse akhala akupeleka kumisonkhano ya chimwendo kuti chubwi😂no more kampeni ife akupha ayi musavere ndiwauve ameneyo
😂😂Wonder msiska, khweeee.
Ndakhala ndikunena kuti Chimwendo Banda ndiwodelera, ayenela ayankhe.
Namalomba ndi 1 kkkkkkkk
Umakwana chimwendo ayakhedi agwesa bwanji ndege
Why is suleman laughing 😂😂😂😂😂😂😂
Akukanawo chilungamo akuchidzawa
😂😂😂😂Eeeee mizimu yakwiya
😂😂😂😂kuma kumabeba bwanji 🤣🤣........
Tinaigula kale,,koma poti mwatibweleselaso tagulaso kachiwili,,koma padziko lapasi chinsisi palibe
Anatsikiranji ndege ya chilima
Kuloza mfiti direct
Yomweyoooooo iponde fadaa
Hahaha anenedi chilungamo anakanilanji kukwera ndege hahaha kuyaluka kulipo
Atiuze chifukwa chani sanakwele ndege iyeyo anali paulendo wopita ku maliro akudziwapo kanthu chifukwa sanakwelenawo
Chimwendo ndamene anapanga zimenezo kuphatikizana ndi chikangawa wakeyo 😂😂😂😂😂 anapha amenewo asakaneso bwanji ndege imene inagwa komweko uja anapulumuka zungu uja ndie iyi iphe anthu 9 popanda wopulumuka siboza limenelo 😂😂😂😂😂
Namalomba ndi Suleman mumayimilia amalawi osaopa afit amenewa
Anamalimba ndikupempheni,chonde musamalinbane ndi chimwendo chonde,akusoweseni pajatu MCP kupha munthu sinkhani,ndiye kananji chimwendo eeee akuwopyatu
Yomweyoooooooooooooooooo galu iye
Very good Namalomba.Kenako ndi kakape
Tonse tidzafa ufa yathu akudziwa ndi Mulungu
Wakupha ndilupanga lupanga lomwero ndilomwe lizamuphe muzonse timusiile mulungu mwiniwake🙏
Kumumvesa sabola chimwendoyo iya😂😂😂
Kkkkkk ayi zikafika apa timati tsobola kkkk
Good job namalomba inuyo ndi sulaiman mukuyigwila tchito
Only truth we need
Namalomba tsopano 🎉😂
Chimwendo anangokula chimutu alibe nzelu
Umakwana fada"
Mr namalonda osamusekelela ameneyo akudziwapo kanhu ngat kunali kufa amayenela kufela limodzi ndithu kunena mosabisa akudziwapo kanthu achimwendowo
Ndaona sureman anavuka pachematu apa
Suleman ngat ailowelere nawo 😂😂😂
Samakhazikikatu suleiman ngat aloweleredi
😂😂😂😂😂@@ellenMakoloma
Samaugwira bwana suleeee
Ndipoditu ayankhule chomwe chinamupangisa kuti asakakwele ndege pomwe ndegeyo sinaliyozaza
Chilungamo sichibisika
Yes tikufuna anthu olimba mitima ngati inu mo fire tie naeni wado wado akudziwapodi kanthu asatipusise imenei ya cilimayi tili nayo nayo mpaka 2025 woo! Mcp ikutiona kupusa.
Din or decoram in august house? Honourables or decipicables????Freedom of speech or invective/censure???
A Malawi panopa tili ndi aphungu a maso pasogolo sakuopa alibe manta zantchito bas
Awuzenii chilungamo amveee
More fire Namalomba
Kkkkkkk mzimu wa chilima musafananitse ndi mizimu ya anthu ena uwuwu ukusautsani guys,,,
Koma nde tiwona zithu😀
Sameer suleman naye kuzangoilowelera ai mumatha ma bigy namalomba umatha
Olemekezeka ku nyumba kwawo
That's what we call blue stand team
Iweso chanilo chako chopoyi adpp aledzela ntonjani adpp iweso opoyila nkama mopanda manumo
Eya ulipo akafunse andevu
MCP yathaaaaaaa 😅😅😅😅 tiyeni nawoooo atiuzeeeeee 😅😅😅😅😅😅
Kkkkkk kma kumeneko wayamba chifuwa chimwendo banda game over, Suleman nkuzayipasa moto pamenepaja....
Aziona
Anaphadi iya akukana chan
Ameneyutu afune asafune funso limeneli adzayankha nthawi ikubwera ase
Mwachoma bwanji
Yaaa 🎉
😂😂 kwachema
Inenso Ngati M Malawi zika la dziko lino. Mtima Wang's udzakhala bwino Chimwendo ataliudza dziko çhifukwa sanakwere nawo ndenge. Yonsei tinamva pa Times akunena ndipo even tsiku limodzi sanakanepo Kuti ndi bodza. Chilungamo tichidziwa. Palibe chinsisi pa dziko lapansi pano
Oloasaseke ndichigawenga basi ndipondizoona akuziwapokanthu zainfa yaku chikangawa
Violation of civil rights in the house of Parliament in Malawi is a joke, miss speaker defending the right for people not allowed to freedom express and freedom of speech is important for any minister don't violate their rights.
Amufinye pali yonse azikumanapo amene chilungamo chomwe sanakwelele ndege ija akuziwapo kanthu
Ndazikonda zimenezi cifukwa ndikuonapo cirungamo cokhacokha or abisare motani cirungamo ciri ngati goride aziona pasogoropa. Ndakunyadirani wankulu murungu akusamarani
Mumufinye chimwendoyo mpaka afotokoze chifukwa chomwe sadakwelele ndege yomwe inatenga Chilima pomwe iyeyo anali pamndandanda okweranso.Suthawa uona tikufinya pangatalike bwanji utiuza zomwe ukudziwapo.
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Ndizoona afotokoze bho bho analemphera bwanji kukwera ndengeyo
Inuso ndiopusa kwambili ndakutulila kapolo iwe mukhaula simuwona anta mukuona ngati ampeni yonhudza chilimayo muwina mwapoyila mulila simunati
Chimwendo chimwendo zinalengezedwa pa wailesi Kut munabwezedwa
Iyi ndye opposition yomwe timayembekezera. Commission of ikwayale yake iti? Yazitsiru ngati imeneyo asiyako kale ndalama ndye anganene chani chanzeru
Musamuletse muntuyu akunena zoona chimwenndoyo akuyenera kiyankha zimenezo