❤❤❤❤more fire mr DK super president and God help us plz we need to be back home when we have good leader yooo but DK we lov you all the way from cape Town pa boma
Great observation. People should read psalms 146 vs 3 going upwards, they will understand that it's only Jehovah the creator of mankind and all the other living organisms and other abiotic factors.
Nkasa ndi Nkasa,akulu kutuluka uko kupita uku sichina kusaka ndalama ,kma khani ndiyakut? Kd unthenga wa nyimbowo ukt chani? Kwa lero nyimboyo ikukamba zodzudzula MCP ndi amene akuyenda ndi zikwanje izi mzosabisanso ,Nkasa more fire ,
Mmmmm koma chaka Chino nyimbo zake za anthu opanda nzeru kumazimamiza kuti kambambe angawine Ku Malawi kuno nde mmmmm nde ine ndizasamuka Ku Malawi coz ine ndizakwela minbius popita kuntchito president ati azidzayenda pansi zizamveka bwanji 😂😂😂😂zina ukamva kambanga mwala
❤❤❤❤more fire mr DK super president and God help us plz we need to be back home when we have good leader yooo but DK we lov you all the way from cape Town pa boma
Nyimbo ndiyomweyi sitikusintha🥳🥳🥳
Chinyimbo chokhacho kuchita kulongosola momvekambwino our next president God help Kabambe to fight this battle ❤❤❤❤🔥🔥🔥🔥🔥💪💪💪💪💪✅✅
Mbande takukonda Dk woyeeeeeee
Davide Dalitso Kabambe❤❤❤❤❤❤❤nyimbo yokoma iyooooo
DANIEL uja akuçhepa
Ambuye tisankhileni ndinu otisogolerera mmene tili mudzikoli Amen
Iyiii ndaikonda kwabwasi
Compose more , iyi ndi one❤❤❤❤❤❤❤❤ DK
Uyu ndye ndamukonda uyu, ndizamuvotera bas ndamupeza
Nyimbo yabwino keep it up
Mpulumutsi wathu, DK
Machine🎉🎉🎉🎉
Kabambe wayambano kundiwaza sakulimbana ndi athu akukamba fundo zake enawa akumagotukwanizana aaa ❤❤
My vote ❤❤❤❤❤
Aaaaa Limbani Chibwana uyu...koma waiswa big up
Musaiponye ku Account yanu pliz
@isaacmidesa never
Waiting for its video
Ndazikonda❤
Limbani Chibwana 🎉❤
So cute song....koma tikaika mma status anthu azitiopseza......tiziimvera konkuno🎉🎉🎉🎉
❤❤❤❤boma ilo
Kabambe better future of Malawi amuna economics my vote
Waimenyatu bho
Kkkkkk DK2025,chopilira ku chiwawu
❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Dk my vote
❤❤❤❤❤❤❤❤ Much love
Limbani chibwana
Dalitso kabambe nd chilima wa relo
My vote kabambe
Ndipo ndizoonadi uyu ndi Davide DK 2025 woyeeeeeee
Nice song for our apure DK 2025 Boma
Kabambe yomweyoo😊
I love the song❤❤❤❤
Kaganizidwe ka ine ngat munthu tsogolo langa poyamba ndimamupempha mulungu osati wandale,ndale ndi bodza.ndipo izizi ndizabodza.
Great observation. People should read psalms 146 vs 3 going upwards, they will understand that it's only Jehovah the creator of mankind and all the other living organisms and other abiotic factors.
Andalewa eeeeeeee!
Mbambande
Nkasa ndi Nkasa,akulu kutuluka uko kupita uku sichina kusaka ndalama ,kma khani ndiyakut? Kd unthenga wa nyimbowo ukt chani? Kwa lero nyimboyo ikukamba zodzudzula MCP ndi amene akuyenda ndi zikwanje izi mzosabisanso ,Nkasa more fire ,
Nice song ❤
Koma a Dan lu akumamvera nyimbo za amzakezi zabwino zi
DK chokucha nsanga
Ndamukonda
Chilima2 I like that
Kabambe my love
Dk much ❤❤❤❤
Mmmmm koma chaka Chino nyimbo zake za anthu opanda nzeru kumazimamiza kuti kambambe angawine Ku Malawi kuno nde mmmmm nde ine ndizasamuka Ku Malawi coz ine ndizakwela minbius popita kuntchito president ati azidzayenda pansi zizamveka bwanji 😂😂😂😂zina ukamva kambanga mwala
Genius
My vote
Limbani Chibwana
Kabambe yemweyo!
Kabambe we will go together and die together
Nyc music but bola apange gwilizano ndi dpp
🔥💥
❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉 Nice and great song
DK my vote
🥳🥳🥳🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥💝💝💝💝💝💝
He deserves leadership
nane waku studio kabambe bas
DK☑️☑️☑️
Vitumbiko Kabambe nizamukuvotera
Dk
Dk my vote❤
❤❤❤❤❤❤🎉❤🎤😍
Nice one
Nice song
I want to register for voter registration where can I register in Blantyre
💥💥💥💖💖💖💖💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥💥🔥🔥🔥
Malawi afunaso chani yapa chipani chosamakidwa NDI chomwechi UTM tayilandila Ma MP atuluka azigulise parliament azaze NDI UTM
❤❤❤❤❤
VIVA AAA
❤️❤️❤️❤️❤️❤️
Komatu Limbani😂😂😂
Vote yanga
Much appreciated
Nice song❤
My vote
❤❤❤❤
My vote
♥️♥️♥️
❤❤❤
My vote
My vote
❤❤❤
❤❤❤❤
Kuganiza mozama ngati mwini wake akumutchula mnyimboyi . Wakwapula chinyimbochi mnyamatayu 💯. Wandifikapo