ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
WE HERE🥳🥳
He is going to win straight no minus
Our president Good work
My vote❤
Ndipo ndika votera chikuwawe, tichotse izi zilipozi, viva UTM
Uyutu adekhe nkhani yothana ndi chikangawa ,zozikonda apa ai ,,,,akuona ngat wafika pa chilima kale
Amalawi musanamizidwe izi ndiomwewo amene anauuza anthu kuti khulupilirani alayasi lero atinamizenso kuti chani kabambe wachepa ife tifuna kulima kudya
My vote
Gud idea
I don't think akukana mgwirizano, Koma akukana kudzakhala kumbuyo kwachipani.
Apa mungopanga alayasi not zoima panokha simungawine simunafike pa legase ya chilima a kabambe musamupase mpata chikangawa kuwinaso don't do that.
Mkulu uyu ngwa fundo zabwino nchifukwa akuwina
zochita koma iziii
A utm akulisa chipani kabambe sangayende ndi ndizipani zinandipo sizingatheke kuyenda ndi DPP chifukwa amafuna pando ndiye kuzichepesa kumvuta
Zoona zake❤❤
❤❤❤❤❤❤❤❤❤
For the love of UTM ❤❤, my vote is ready and being kept safely
Izitu tingovomeleza kuti mcp mpaka 2030 woo ,,, chifukwa utm,dpp,aford, udf sangawine paokha ngati sangapange gwilizano.
Vuto ife anthu timayiwala mwasanga UTM yinapanga mugwirizano ndi MCP anagwirizana zaka 5 winaso 5 kodi MCP yinavomereza kuti SKC adzayimire 2025 panopa SKC alikuti zogwirizana zimenezo munthu akatenga boma amasitha tiyeni a Malawi tizikumbukira fast zithu .
Davide anagonjesa Goliat paiye yokha kuzela phamvu za Mulungu tiyeni tisithe Malawi wathu .
Amen 🙏