ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
The way Hyphen kept his cool tho 🤜🤛🙌🙌👋👋
Piksy and Sangie are a good combination 🔥🔥🔥
🔥🔥🔥🔥
Koma ka nthawiko kakutichepera khwambir please should be long if possible guys ❤❤😊😅😅
Extend the time plz atlist 30 mts
Ndipo inu aaaaa
Hyphen 😫🔥 mwabwera guys 🥳Nice one, keep the fire burning from all angles🎉 loved every minute of this episode🔥
😂😂😂magulitsa mandimu lne🙌🙌Ati Mwano wake wakupitirira lweyo eti😅😅😅mumakwana guys 🔥🔥🔥
I just feel that Connie ndi chibwezi cha ngozo tsiku linga ngozo zizamudera 😅🙌
"Ayi si baby girl don't receive it, i can see twins" you have finished me munthu wamulungu😂😂😂
😃😃😃tcheni pa kalanka amwene. Avula bwanji ma socks chonde😃😃😃🙌mapemphero Anji awa eeeh.
Ndiwo zuveka chwe😂😂🔥🔥
Kikikikikikikikiki koma ngozo ulindi kachipongwe eishiiii
kubwera nyumba kuvula nsapato kuti apemphere bwino bwino kkkkk
Nice video koma mumatenga mthawi yaitali
Sangie is my gee for life yoooooo😂❤
Guys you are great!!!
Mwafka guys 🎉🥳🎉🎉 mukachedwaso tigenda
Akumachedwa kma si bho
Mtebe la 41 lakwana
Watching from eastain Cape port Elizabeth South Africa 🇿🇦
Mwatisiya mmalele kkkkk.
u gyz come on mukumatenga nthawi musanabwere plz kanthawikonso taonjezerani we are following u sangie + piksy = a very good combination
Mukumachedwesatu koma mpaka mwezi kutha 😂😂😂
Km a ntebe kkkkk mapemphero mpaka socks out
Ati ndiwo zikuveka tchweeee tu uku😁😁😁
I missed Mayi Ngozo finally she is back
Koma Kwa Albert ndi Dorica kuchema😂😂🙌🏿
Piksy and sangie it's a best for drama ❤ l love them all
Dessa vez demoraram publicar, mas obrigado 🇲🇿
Akyt zonse ndi ambuye kkk🤣🤣🙌
Nyimbo yikhale ya piksy....Limakwana la 40😂😂 Dorica zimuvuta
Iiih koma kupemphera mpaka kuvula ma socks😂😂😂
Iweyo sudya umutsatire mzakoyo
team usauver your the best but nthawi mukumangonyonola , plz plz tiganizireni kumeneko
Nice guys keep the fire burning🔥🔥🔥🔥
Kamdala kaja kamuthira batile mkazi wa Young Kay. Sikamaseweradi .
Komatu kam'busa akanakaonetsa aaah kungokasiyasiya zoona😂😂😂😂 sangie ujayo ndi makina❤❤❤
Mpaka ma Conve. Sakuveka boboo cuz of HangOver Piksy ukanayipola mowotoo
Komati guy naneso I receive it
Koma mkaz ngozo wakuna naye nzake wogala Gaza. Mowa
Koma Kwa Hyphen ma guy aphanako🤣🤣🤣🤣🤣
Kkkk abusa kupemphera mpaka kumvula sapato hahaha kma yaaa.. nice one kma Musamasowe kwambiri
😅
🤣🤣🤣🤣🤣Piksy iweyo wachipongwe kwambir walakwa Chan ganizani
Ulemu wanu adona mumatha❤❤❤
The combination of piksy and sangie is something else.,....10 pa 10
Koma mulendoyu ati ndikukawupitiliza kayetu patundapa😅😅
Munakatipha ndikudikila
Am dead😂😂😂😂💔💔💔danzi La gani latani
At bwenz ukumeta masiku angati...🔥🔥🔥🔥🔥team Ponyi mesa
Agwidwa mabataniwo asemphaninsa kkkkkk😂😂😂😂😂
Ikakuona litsiro kuthawa ku pub kukagwidwa kunyumba🤣🤣🤣
Watenga wapa decoleshion😅😅😅
Mutu wa Gani bwezi akumeta week yose 😂
Abusa kunamizila kupemphela
nthawi yachepa aaaa tikudikila kuti tione momwe zathela kwa hyphen
Ee! Koma Gani awene buyera wasanduka m'mponyi 😂😂 kuno...
Yeaaa kma guys mumakwana hvy ,, at mwanowo wapilila iweyo 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 angozo
Abusa mapemphero anji ovulira nsapato ndi sokosi??? Mabatani atasemphanitsa kkkkkkkkkkkk mmakwana guys. Dorica wainyumwa lero aphikilidwe basi kkkkkkk onjezerani ma minutes koma akulu akulu mmatisiya mmalele
Ndikuoneka ngati satan kwambiri 🔥🔥Koma patricia🤣🤣🤣😂
Very very great
Wine wa decoration 😂😂😂
U guys munabwera kudzakhala
Oh wow
Muthu wamulungu apa nde game yamukulira
😂😂 ndiphika ine nsima
tinakusowani gyz kkkkkk episode ili bho hvy
Koma ntebe ndiwe galu kwabas ati ambuye mudzionetsere nokha lero😅
Uncle p kathawika kamachepa heavy
Ati watenga wapa display
Following
Guys mwatisiya mmalele, ponyani Ina lelo 😅😅😅😅 mwaganiza bwanji
Ati bwez gani ameta masiku angat😂😂
Mtebe sanachenjere bwino 😂😂😂
😂😂😂😂Koma ntebe anakonza
Dolika uja izathera mapenate....
Musadzasiye nginiziii guys 😂😭 this is good!
Abusa apole moto lamba ayiwala kumanga bho bho chati ayiwalanso eish zovuta
Aaah kma ntebe ul ndchbwana😂😂
Eeeeish mponyi nzako wapezerera ma pemphero uko😀😀😀😀
Sangie ur good
Hahaha koma adah Busa wa fek
USAUVER Ili bho koma nthawi imachepa tamayesani kupangapo kakatali ndithu mwina kumaponyako every week😑
Busa wachinyengo yaaa kkk😂😂😂😂😂
Ngozo akuti mwano wokuti wakupitilila iweyo 😂😂😂😂😂😂
Hyphen ndi Dolo fana wapayize
Mumandimvesa kukuoma guys😊
Kma. Guys makwana🤣🤣🤣🤣 brother wake wa con chonde usatipase mavuto nyumba mo
ndipo brother ativuta uyu😁
Koma kwa Hyphen kutha bwanji😂😂
😂😂😂😂😂 muzithokoza kuti muli ndi dazi 😂😂😂😂😂
🤣🤣🤣nde a Mtebe mapempherompaka kusemphanitsa ma button, nsapato vuliiiii, hahahaha
Komatu ka m'busa akaa,, 😀😀
I love you @hyphen
Mponyi uli bho kwabasi😅😅😅
Mwachedwatu koma tathokoza
Ngozo magulisa ma ndinu ine😂🙌💔🚶
😂😂😂 translation iyi ilk nyatwa
Banja la Angozo ndi lowaza🤣🤣🤣🤣🙌🙌
Tinazisowa zmenez.ndkuwona m'busa wachnyengo zikumuipila panandpanand
Ngozi mponyi aaa😂😂usazamgulileso
Finally. Thank you
Pisky ndi Mai Ngozo pangani zeni zeni
Iyiyo ndi more fire guys,
Watengatu wapa display eeeshi koma azimayi ndi kabati 😂😂😂
Muzkoze paka mwez zooja
Wamwano wadabwa nazo 😂😂😂
The way Hyphen kept his cool tho 🤜🤛🙌🙌👋👋
Piksy and Sangie are a good combination 🔥🔥🔥
🔥🔥🔥🔥
Koma ka nthawiko kakutichepera khwambir please should be long if possible guys ❤❤😊😅😅
Extend the time plz atlist 30 mts
Ndipo inu aaaaa
Hyphen 😫🔥 mwabwera guys 🥳
Nice one, keep the fire burning from all angles🎉 loved every minute of this episode🔥