BON KALINDO LERO PA 4 SEPTEMBER 2024 |

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 15 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 110

  • @ReubenNamfuko
    @ReubenNamfuko 11 วันที่ผ่านมา +8

    Mmmm ndipovuta kut angakhale akupitiliza, i hope atha kukhala ndimantha pazomwe zinamuchitikira mwamuna wakee

  • @PaulChafikirah
    @PaulChafikirah 11 วันที่ผ่านมา +7

    Mai chilima abwelepoyala ndikudziwitsa ntudu wa amalawi KT atsogolera chipani cha UTM ndinjila yokhayo tingazadziwe chilungamo cheni cheni chatsogolo la chipanichi km chonchi ai sizoona nkhope ya biyeni izasowa pansalu paja God bless you Mai Chilima

  • @user-gq9mh7se2e
    @user-gq9mh7se2e 11 วันที่ผ่านมา +3

    I support this idea....Mary chilima the game changer.

  • @bysongeorge3243
    @bysongeorge3243 11 วันที่ผ่านมา +2

    Bwana DC ulemu wanu ndipo ndimakunyadilani mukung"alula kwanu koma ya Mai Chilimayi Mmmm, ndakaika. Tisawakakamize ku Ndale isali mbali yao komanso akulirabe, amantha ndipo patenga nthawi kuti mtima wao ukhale pansi. Mwina asintha maganizo uthenga wanuwu akauganizira bwino...

  • @PaulKalambo
    @PaulKalambo 11 วันที่ผ่านมา

    The DC mwana ooooooophya kwambiriiiiiiiiiiiii ✊✊

  • @user-le7fb9cr8z
    @user-le7fb9cr8z 11 วันที่ผ่านมา +2

    I love you bon kalindo kuyankhula ndiye waesesa koma vuto ndiife amalawi

  • @yohanekipandula5197
    @yohanekipandula5197 11 วันที่ผ่านมา +1

    We love you DC,,ur really enlightening us

  • @PartceoTambala
    @PartceoTambala 10 วันที่ผ่านมา

    I support this advice

  • @OliveaMapanga
    @OliveaMapanga 11 วันที่ผ่านมา +2

    Ndili mbali Yako Bonie ( my young brother) ukuyakhuladi zoona cz mery ndamene akhonza kunyamula UTM pamwamba kwambili

  • @Paworo-h5r
    @Paworo-h5r 12 วันที่ผ่านมา +4

    Ngati muli wowona kuti chilima anaphedwa simungayankhulenso zoti Mary akhale president umenewo ndiwusatana,

    • @OliveaMapanga
      @OliveaMapanga 11 วันที่ผ่านมา +1

      Km kuyima kwa mery pa chipani kunthaso kuthandiza kuti okuphawo alandile chilango mosanvuta cz akankhala kunja kwachipani sangayakhule molimba ntima adaniwo antha kumupeza mosanvuta pamene akankhala nkati ankhala otetezeka kwambili

    • @MalizeniOliviaBridan
      @MalizeniOliviaBridan 11 วันที่ผ่านมา +1

      Kodiinuo mutaphedwa panyumba panu akazanu asiye nyumbayo kuthawa kuyikana kusiyila anthuwena atenge nyumba chifukwa choti mwafela amunawake

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 11 วันที่ผ่านมา +4

    The DC booooon kalindooooooo mwana owopsyaaa kwambiri inenso ndikugwirizana ndi fundo yoti marry chilima is deal to stand for president

    • @ModesterMbendera
      @ModesterMbendera 11 วันที่ผ่านมา

      The DC Bon Kalindo km umatha okumva wamva osamva akhare choncho

  • @EliaThomas-vp9jz
    @EliaThomas-vp9jz 11 วันที่ผ่านมา +1

    Chilima MHS continue.. To RIP opposes the idea of family succession politics he wanted change. Kalindo is of the view of old politics. I second the idea of Chilima that chipanichi ndachanu a Malawi sizakunyumba kwanga. The genius new that he will not be there forever.

  • @JonathanLimunye
    @JonathanLimunye 11 วันที่ผ่านมา +2

    Mr DC mfundo ya lero mokupemphani muike mu English and muiponye pa BBC NEWS kapena pa WORLD NEWS Kuti ma doners adziwe zimenezi za chipatalazi

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 11 วันที่ผ่านมา

    Ine ku queen Elizabet ndilibe nako mau
    Pa 4 April mwana wanga ampanga oparation
    Nditalipila 100 pin
    Chipatala chaulele chija mhhhh kobelekatu,
    Amati kulibeko siza akufuna akagule mhhhh

  • @HappyMunthari
    @HappyMunthari 11 วันที่ผ่านมา +2

    The Dc mwana woopsa kwambiri

  • @MervinMwambinga
    @MervinMwambinga 11 วันที่ผ่านมา

    I agree with you DC Kalindo. Honestly this guy is wise 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @user-sv5cq3sf7o
    @user-sv5cq3sf7o 11 วันที่ผ่านมา +1

    Wandisokosera mauling utamva, chilungami ndie ndichimenecho😊

  • @austinvincent1264
    @austinvincent1264 11 วันที่ผ่านมา +1

    I agreed this statement mary nde deal koma sitikudziwa kuti mary angavomele

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y 11 วันที่ผ่านมา +1

    Chakwera watikwana kwambiri ndipo watitoradi ife amalawi.Mayi Chilima akuyeneradi kukhala mtsogoleri wa UTM.Lazaroyu popanda SKC anali yani.Kanyimbi amene akutizunza ifeyu munthu opanda chisoni kumupha mnzake yemwe anamuika pampando. Ambuye kumwambako tikanthireni Lazaroyu.

  • @imraanJafal
    @imraanJafal 11 วันที่ผ่านมา +1

    ❤❤❤❤❤❤ Inu chilungamo simubitsa tiyamike kwambili boooon kalindo the DC president wathu

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 12 วันที่ผ่านมา +10

    mary -Chilima is the Right candidate for UTM

    • @peterchikwakwa8476
      @peterchikwakwa8476 11 วันที่ผ่านมา +1

      100% and ndiozindikira

    • @KikaImran
      @KikaImran 11 วันที่ผ่านมา

      As member?

    • @Suwedie
      @Suwedie 11 วันที่ผ่านมา

      Never... is that not same for the Muluzi's and Muthalika's?

  • @user-cv3zw9ic6d
    @user-cv3zw9ic6d 11 วันที่ผ่านมา +1

    Amai Chilima tipulumutseni tikudikira Inu mama bwerani mutiyankhule

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 11 วันที่ผ่านมา

    Mcp ikutuluka mbola basi afune asafune
    Mcp ndi yakhaza yokupha ndiye pano malawi 🇲🇼 yaziwa za chipani cha mcp

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 11 วันที่ผ่านมา +1

    Ndalama zingothera maulendo opusa basi ndiye namachende kunkuyu azibwera azitiyakhura zopepera, a Malawi anatiloza ife kaya ndi ndani? Anthu awa samayenera kubwelera boma mcp sichipani.

  • @OmegaSanjama
    @OmegaSanjama 11 วันที่ผ่านมา +1

    Ngat Panadol ku kamuzu central kulibe ndiye kumudzi akapezeke

  • @Moses51
    @Moses51 10 วันที่ผ่านมา

    The DC bon kalindo 🎉

  • @OmarManjawira-up3ns
    @OmarManjawira-up3ns 11 วันที่ผ่านมา

    The DC, this is what exactly happening in Malawi😢 I v
    Come from MHG and kwathu ku Liwonde kumakhala ngati ku Mangalande ife eni dziko kumayenda ndi mantha but our leaders 😢😢💔

  • @MwizaChavula
    @MwizaChavula 11 วันที่ผ่านมา +1

    Ndipo live marry yemweyo pliz.

  • @NancyNyelenda
    @NancyNyelenda 12 วันที่ผ่านมา +2

    Ndizowona wamisala anawona khondo HT DC🎉

  • @user-tq1ei8ls5u
    @user-tq1ei8ls5u 11 วันที่ผ่านมา +1

    Zomvetsa chisoni kwambiri, chakwera ndi anzake awononga dziko ndithu

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 11 วันที่ผ่านมา

    Mary Chilima is the right Candidate ✅️,
    The DC is always right ✅️

  • @MacdonaldNamphuwa
    @MacdonaldNamphuwa 11 วันที่ผ่านมา +1

    DC akunena zoona, a mary chilima tili pambuyo panu

  • @gertudebandah1758
    @gertudebandah1758 11 วันที่ผ่านมา

    Chilungamo ndithu koma chopweteka 😍😍

  • @FatimaUmali-pc8sy
    @FatimaUmali-pc8sy 11 วันที่ผ่านมา

    Mery mukasakha kukhala president nde akwatiwasotu nanga ore amakhala butcher kkkk❤❤❤

  • @80yami
    @80yami 11 วันที่ผ่านมา

    Kumene Mary Chilima nde joker, azinzake a SKC ofuna kudyadi zamasiye pano ayamba kuonekera poyera plus mma TV umu kufuna kuzigulira malo mxiiim

  • @ALEXAlli-ck8lj
    @ALEXAlli-ck8lj 11 วันที่ผ่านมา

    The DC ng'alula basi,mbambande

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 11 วันที่ผ่านมา +1

    Zoona amalawi tikanazuka tose kuchosa pule ndinduna zake . Akanakhala maiko ena bwezi nduna za Chakwera ndi iyeyo atathamangwisidwa kale. Ifa ya ngozi ilipo koma wosati ya anthu 9 yoyesa kukoza ndichifukwa akupereka statement zosiyana Mulungu wamoyo akuwaseka kumaso

  • @NoahPhiri-f7m
    @NoahPhiri-f7m 11 วันที่ผ่านมา +1

    Mary Chilima ndiokwana, chifukekwa alindikuthekera.

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl 11 วันที่ผ่านมา

    Chilungamo our president boooorn kalindo 🔥🔥

  • @user-qp5rc5bk8p
    @user-qp5rc5bk8p 11 วันที่ผ่านมา +1

    Mary emweyoo🎉🎉🎉

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 11 วันที่ผ่านมา +2

    Iiiiii Mary Chilima kungoti ayima aaaaa basi akanyimbiwa zawo zizadelathu

  • @AkibuMdala-sr1dy
    @AkibuMdala-sr1dy 11 วันที่ผ่านมา +1

    Uremuwanu the DC ❤❤❤👍🤝

  • @misoMoyo
    @misoMoyo 11 วันที่ผ่านมา

    Ndipo zoonadi I like it Mary yemweyo

  • @godrick-s6w
    @godrick-s6w 11 วันที่ผ่านมา

    I totally agree with you the DC . Mary can absolutely make it .

    • @rexnyalugwe4910
      @rexnyalugwe4910 11 วันที่ผ่านมา

      Bakili-Atupele. Bingu-APM. SkC- Mary...zakubanja ?

    • @rexnyalugwe4910
      @rexnyalugwe4910 11 วันที่ผ่านมา

      Chakufwa-Enock

  • @ErnestAllex
    @ErnestAllex 11 วันที่ผ่านมา +1

    Marry Chilima is key indeed

  • @Chikumbuso-l5m
    @Chikumbuso-l5m 11 วันที่ผ่านมา +1

    Ndizowona my chilima atenge uprasednt

  • @HarryKandani
    @HarryKandani 11 วันที่ผ่านมา +1

    Ndifedi opepela the DC sukunama

  • @NellieMsamala
    @NellieMsamala 11 วันที่ผ่านมา

    Ine ndimaona ngati asakhale koma kuli achinyamata enawa nda amene atasankhepo ngati tufuma UTM isathe merry ayi achikulire maso Ali pa iye nde mmm ayi

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 11 วันที่ผ่านมา +1

    The Truth bravo

  • @ernestjuniormbanga3370
    @ernestjuniormbanga3370 10 วันที่ผ่านมา

    Dc amatuma...Kma zoonadi ADC

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 11 วันที่ผ่านมา

    The DC mwayamba kukocha zipani?kkkkk

  • @CharlesKachipanda-jz9jv
    @CharlesKachipanda-jz9jv 11 วันที่ผ่านมา +1

    Iwe ndi machine

  • @JoyfulMbanda
    @JoyfulMbanda 11 วันที่ผ่านมา +1

    Chilungamo ndimwano

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 11 วันที่ผ่านมา

    DC umakwana 🔥🔥💪 💪

  • @KondaniPhiri
    @KondaniPhiri 11 วันที่ผ่านมา

    Bwana DC. Tikupepha kut. Mwezi uno usanthe. tamuchotsani ameneyu chikangawa yu. Komwe wapita iyeko akawone kofikila pls mabugwe lowelelanipo umboni ndiwokwanila pls

  • @HalimaShafie-q9k
    @HalimaShafie-q9k 11 วันที่ผ่านมา +1

    Really the daddcccc

  • @Patrick-s9d
    @Patrick-s9d 11 วันที่ผ่านมา +1

    Mary sangakhare president coz zitha kumukakami kt akwatire coz president sakhala butchara

    • @OliveaMapanga
      @OliveaMapanga 11 วันที่ผ่านมา

      Sankhala mbeta ,musaiwale kuti mery ndi nkanzi 😂😂😂😂
      Ndakunyadila kkkk

    • @HudsonMwafulirwa
      @HudsonMwafulirwa 11 วันที่ผ่านมา

      Chikomeni registered though amatenga amayi ake kapena abambo ake . Chikomeni anatenga amayi ake.

  • @MoosaChirwa
    @MoosaChirwa 11 วันที่ผ่านมา

    Nkhani ya Mary ndi yowona coz ndi amene Ali oyenera kusogolera UTM manga ndi azake ayi ngakhale Kuti manga akufunisisa akhalepo yekha

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu 8 วันที่ผ่านมา

    Koma izi mukukamba ndi zoonz zenizeni

  • @JohnBandawe
    @JohnBandawe 11 วันที่ผ่านมา +1

    Dziko ilili eeeeh

  • @giftmakoyo1441
    @giftmakoyo1441 11 วันที่ผ่านมา

    Musiye Mary azilira mamuna wake wafa imfa yowawa chifukwa cha ndale ndiye iyenso apita pa mpando wa upresedent aaaaaaa Bon pena umayankhula zoduka mutu

    • @MalizeniOliviaBridan
      @MalizeniOliviaBridan 11 วันที่ผ่านมา

      Inundinu osaganiza sadzafa ndani kuchipanga chipani mkufika pamene chilili cha UTM ndintchito yaikulu asaisiye atenge ndichawo palibe vuto

  • @richardarmittage1693
    @richardarmittage1693 11 วันที่ผ่านมา

    Ndipo ndizoonadi Mary Chiloma ndipo atha kulamulira dziko la Malawi mosayang'anila Mtundu wamunthu
    Amalawi let's vote Mary Chilima kukhala President wa dziko LATHU

  • @ManganiStanley
    @ManganiStanley 11 วันที่ผ่านมา

    Totally agree Mary chilima should be come out and take party enawa abwera kuzangodyerera

  • @SEEJSHJEFFREY
    @SEEJSHJEFFREY 11 วันที่ผ่านมา

    Kumeneko ndiye kuononga ndale ...kungoti anali mkazi wa chilima ndiye basi atha kutsogolela dziko? Wafela chilima June yomwe mkazi wake mphavu azitenge kut zolankhulila?

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk 11 วันที่ผ่านมา +1

    Manjanjawidi kkkk

  • @felixtembo9602
    @felixtembo9602 11 วันที่ผ่านมา

    Koma asamale Mary yo ngati angatenge udindo wa late chilima.boma lilipo PANO ndi Mafia government

  • @Khumbom
    @Khumbom 11 วันที่ผ่านมา

    Mmmm ayi munthu adakalila mamuna wake

  • @DominicNkosi-iq9fh
    @DominicNkosi-iq9fh 12 วันที่ผ่านมา

    You have nailed, Born, that's 100%

  • @MaryMalemia
    @MaryMalemia 11 วันที่ผ่านมา

    Iweyo ndi amene wabweretsa cancer

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 11 วันที่ผ่านมา

    Mr DC mwayamba kupanga compane

  • @ShadreckHassibu
    @ShadreckHassibu 11 วันที่ผ่านมา

    Kalindo akuyankhula zoona koma vuto zipanizo zikatengera kuphya mtima ndicholinga achotse MCP pa mpando nde ndi izi tikuzunzika lerozi adapangira kuphya mtima a tonse including himself anali gulu limodzi kumamunena mutharika kuti osanva

  • @RaphaelKweve-u5s
    @RaphaelKweve-u5s 11 วันที่ผ่านมา

    Bon kalindo ukutanthauza chani za kuti Legacy ya Skc ndi kubanja angayikwanitse mu chipani cha UTM,,,,, ? Sitikufuna ndale zodalira kubanja komwe kunali President wa Chipani,,,Mary can support the party osati kukhala President as now ,,,,This is not Family Party,,,Maganizo opusa amenewo

  • @user-fy3yo5xy1v
    @user-fy3yo5xy1v 12 วันที่ผ่านมา

    You are saying truth

  • @rexnyalugwe4910
    @rexnyalugwe4910 11 วันที่ผ่านมา

    UTM is not a family party. Zomwe zikupha zipani ndi zimenezo zofuna akubanja azipitiliza chipani

  • @tchalosmulo
    @tchalosmulo 12 วันที่ผ่านมา

    The DC kuyakhula mopanda matha koma zopanda phindu

  • @JamesKalasa-s6s
    @JamesKalasa-s6s 11 วันที่ผ่านมา

    Ndimakuvera zoyakhula zako koma izi zomati mary chilima utm wadeya ndipo utm ndi chipani cha amalawi osati chakubanja. Akafuna akubanja abwele athandize utm not tisakhe wakybanja ayi. Mzeru zimafuna anthu a mzeru. Utm ndi ya malawi zipani za ku banja zilipo

  • @MaryMalemia
    @MaryMalemia 11 วันที่ผ่านมา

    Wasauka iwe ukufuna chi bans

  • @ElizabethMulinde
    @ElizabethMulinde 11 วันที่ผ่านมา

    Iweso mutu wako sugwila ntchito muntha akhala bwanji president munthu mamuna wake wafa pompano munaonako president opanda mkazi or mamuna cholinga chanu ndi chan makamaka ulibe nzeru kalindo

  • @CollinMkhonza
    @CollinMkhonza 11 วันที่ผ่านมา

    Anthu nose amene munatenga gawo popanga mgwilizano ochosa chipani cha(..) Boma ndi oti mundabadwa ma, 60s, 70s, and 80s... mukuziwa khaza zomwe chipanichi chimachita..... bwanji simunapange gwilizano ndi chipani cha (...)ndichomwej chinabwelesa Democracy? So yesesani chipanichi chichoke, coz chikazangowina 2025..chizagula anthu ose osusa Boma ndipo yemwe azakane azaphedwa... Ndipo ife Ana am 90s.....2000, sitizakwanisaso kuchosa chipanichi....chonde nose amene munasogoza chipanichi Boma...we need ur action sizomangolankhulazo, tatopanazo....pangani chimozmoz, Mene munapangila 2019,, Bakili analimbana ndi Fiti zimenezi ....inu mkuponyelaso komweko..... Munaganiza bwanji......😢

  • @AmosShadreck
    @AmosShadreck 11 วันที่ผ่านมา

    Cancer bola,tikutitu ozizilisa pofuna kukuchosa zino lomweli mzipatala mulibeee ati ukagule mkumati inu budget ija ku parliament mudaika ndalama kt zigule mankhwala zija zilikutiii?

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di 11 วันที่ผ่านมา

    M chilima zigamuvute akanakhala ndi mwana olo bro bola mai yu wawopsedwa ndi zomwe maunawake anapangidwa komanso Kodi Agathe kukwatiwa panopa? Mpovuta

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga723 12 วันที่ผ่านมา

    Kuba no1 kubakuba

  • @MwizaChavula
    @MwizaChavula 11 วันที่ผ่านมา +1

    Try ma demos DC

  • @ThomasMlowoka
    @ThomasMlowoka 11 วันที่ผ่านมา

    The DC

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga723 12 วันที่ผ่านมา

    Ng'ona party, wangakachi party

  • @AubreyChiyaya-ty8ge
    @AubreyChiyaya-ty8ge 11 วันที่ผ่านมา

    Mai chilima iloweni basi ...and tizavota tonse Malawi tizavotela inu pofuna kudziwa chilungamo pa imfa ya amuna anu ....tiyeni nazo ife pa mbuyo pano

  • @DeviLinya
    @DeviLinya 11 วันที่ผ่านมา

    💯💯💯💯💯💯❤️❤️❤️🙏

  • @KanjokaCh
    @KanjokaCh 12 วันที่ผ่านมา

    Zikhala bwino kwambili bola avomeledze chifukwa mmm

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 11 วันที่ผ่านมา

    Ayi inu a winiko .mmayesa inuyo munali limodzi ndi skc. Bwanji inuyo osaimirira kukhala pulezidentyo? Koma mzimayi yu ayi.mukufuna kuti adzaphedwe moopsya ngati mamunake? Mmene wafers mamuna wake.ndi andale ena a mcp? Musatero a baba

  • @douglasturner2992
    @douglasturner2992 11 วันที่ผ่านมา

    😢

  • @NdalamaJames
    @NdalamaJames 11 วันที่ผ่านมา

    Ndpo live

  • @mbelengamavuto2517
    @mbelengamavuto2517 12 วันที่ผ่านมา

    Dc kuyakhula mwamphamvu

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda 12 วันที่ผ่านมา

    🔥🔥🔥🔥

  • @user-ux9ik4zr5x
    @user-ux9ik4zr5x 11 วันที่ผ่านมา

    Unakakhala ndi nzeru sunakalora kuti munthu wazaka 90 akhale Presidential Candidate,achinyamata are ukunenawo ndiye ati?nchifukwa anthu amanena kuti ndiwe wamisala

  • @SolomonShaibuh
    @SolomonShaibuh 12 วันที่ผ่านมา

    Kuswakuswa