Hahaha angozo mumaona ngati ikhala nkhani Ya nsapato kushop mupaka kumubweresela heater..... afana kushop ali bho amatha. Enjoying every clip. You have my back.
Hahahaha ....Angozo ati anthu amabadwa awiri awiri di😂😂😂😂😂 also black Nina wow wabhebhetsa...Asis amangoti ndikupatsa chilichonse...has the game in control....nice content....also don't understand why angozo is being too nice, so extra nkhani yake ndi ya nsapato yomweyi kapena Pali inanso🌚🌚.....Koma big up guys today's episode was perfect and so much fun to watch
I'm screaming.. best show ever😂😂🙌🏾🙌🏾
I wish likanakhaladi banja mumakhalana guyz
I love every bit of all the series Best show ever
Uli bwinotu ngozo muja
Akuthamagitsira muja ndimaona ngati. Uvuta pa ndalamayo.koma we are loving it
Ngouzo uli PA mavuto akulu 😅😅😅 mpaka masamu ukuletsedwa kuthandiza 😅😅
you guys never disappoint, big up
Mumanipanga last, from Zambia 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Akut azimayi amwene andifuna kale Nthawi yomweyi koma ngozo kkkkkk
Zopita ku Lilongwe zanthera faw basi😄😄😄😄😄😄😄😄😄😄😄😄
Hahaha angozo mumaona ngati ikhala nkhani
Ya nsapato kushop mupaka kumubweresela heater..... afana kushop ali bho amatha. Enjoying every clip. You have my back.
Kkk angozo akufunatu kupepesa Koma poyambila pa kusowa
Ine mayi Ngozo amandiwaza heavy 🥳🥳🥳
4 pin lunch plus 15 pin🤣🤣🤣🤣🤣
Angozo ati simuchoka Kmtu azimai alibeso pabwino mamuna asakhale pakhomo Km athu inuyo mandivetsa kukoma
Was busy watching American couples. Big up guys
Koma blackNina nd sister wake😂😂😂🙌🙌🙌
Amachita bwino osamulipila issssiiii
Chotukuko chimvutirapo nyumbamu ndithu kowerengetsera ndalama mwamuna asakhalepo
Tiyeni Ku Ntunda konko basi big up🍾🍾🍾
Zomwe waziona blackmina ndizomweso anaona brother wanga
Ati mwachenjera Darling 😂😂😂 Black Nina akuitha koma.
This Is Classic🔥🔥.... Mmakwanaa I Like Your Videos
forever my favorite people hahahaha keep it up you make us happy
kkkk Patricia and Gani..just like me and my sec sister
Anthu inuyo eeeee 😂 Nina wadya dolla ndi zinsisi zake😂😂
Banja kma ili, osati mkazi kungoyankhula pang'ono ndi mbama
Kkkk koma ndie kuwakhumatisa masten kungowauza kut ulula zomwe amapanga kwa amunawo afewelatu 😄😄😄 umatha khezen
Ndumachita kuona kuchedwa kuti ituluke
Kkkkk azimayi amakunyoza akudziwa kuti akufuna
Tufuna chinzukulu Ife angozo muchedwa kkkkkk
I hope project Ya bar sikhalaso bar lolephelekatu ndi Achina Ganizani ake amenewa
Koma zabwino zonse... Mumandisangalatsa kwambiri pitilizani kutero ndithu
Azimai ndife oseketsa.hahahaha
Big up Mr ngozo and Mrs. Phiri sangie kkkkkkkkkkk 😄😄😄😄😄😄🤙 we waiting next episode..........
Mulibe koyenda muyende apiksy
Episode 8 mwachedwa nayotu
akuti imbani nyimbo yanu yachipongweyo kkkkkk nice
Tikuziwa chomwe mukunyengerera😂😂😂😂nkhani ya nsapato tu siitha lero
Mposo 🤣🤣🤣🤣
Nice one guys keep it up
We're enjoying!
Angozo being Nice😂😂😂😂
Akut muzit shop yathu🤣🤣 Koma black nina ase... big up guyz
My twin kudyera sister wako kumeneko
Komatu @blacknina😂😂🎂🎂
Hahaha unakapanda kuntumizila
Hahahaa achenjera lero azakufuna aleke
Bola isakhale mwatumiza kwa MG2 ndalamayo ngozo, Sangie masiku ano bale wakoyo ndamene amakupanga chipongweyo. Mukapusa mugwira chiphwisi kkkk
😂😂 Mwayesetsa kufuna kucheza nawo koma ayi ndithu
when is the next episode guys... kudikila kukumavuta tungobweleza ma episode kkkkk
😍😍😍😍😍 ndinu madolo
Koma amwene😂😂😂 black nina mbali inayi ngozo kwinaku
Akumana ndi nyambalo angozo
So nice
Ndisaimbe nyimbo😂😂😂😂
Gani ma project ali bwanji ?
Inavuta ndi nsapato 🤣 Ngozo akungoyenda olakwalakwa
Makwana ma guy,,🔥 ife tikufuna chi usauver cha 1hour
mmakwana koma mudziikako english subtitle nkhani zanu nizokoma
Zakuvuta Ngozo 🤣🤣🤣umasewera ndi azima
Kodi osangokwatirana bwanji?
Nice koma ikufupika talikisaniko nthawi
A shadow woyeeeee😂😂
Nice Series
Penatu zumakaikitsa za bar yomwe akumangisa achina sangie azazindikila bro wake wamudyera kkkkkkkkk
Sangie mr ngozo, amakwana
My favourites
Nayeso wa mushop kufuna kutamika chani? Azikhala sensitive osamangolubwa pa zlizonse ikanakhala nsapato sinawakwane nde sakanabwera kuzabweza?
Koma agulisa mma shop mukhalike ndinthu ngozo apa ndiye anathatu kkkkkkkkk
Pambuyo Sangie
Hahaha ati mundipalamulisetu
You guys makes me hahahaheheheheheheddeeeee but please notify me.
Always 🔥😂😂
Angozo mpaka kumuopsesa mwanw
😂😂😂😂abare zafika kumeneko
koma nkhani ya msapato tidakali nayo ndthu mpka apamapeto ubwino wake sangie sapupuluma kkkkkkkkkkkkkkk
keep fire burning Usauver on fire
Hahahaha ....Angozo ati anthu amabadwa awiri awiri di😂😂😂😂😂 also black Nina wow wabhebhetsa...Asis amangoti ndikupatsa chilichonse...has the game in control....nice content....also don't understand why angozo is being too nice, so extra nkhani yake ndi ya nsapato yomweyi kapena Pali inanso🌚🌚.....Koma big up guys today's episode was perfect and so much fun to watch
Nkhan yake ndi yansapatoyomweyo😂😂😂😂
Ndiwauza amuna anu zonse
Angozo ndi anankalizi mumakwana
Wakuda wangalusa ufuna umuulule sister wako zoona😂😂😂🔥🔥🔥
Guys you rock I love it ooooio
Keep it up
Kma 🔥🔥🔥🔥
komatu Sangie ndooneka bwino
Koma ngozi konseko kunseka pakamwa pati yo kkkkkkk koma nde ukaipa dziwa nyimbotu
Agozo mbolatu ase kkkkkkkk,,,pic up guys
Great
Mumakwna azibambo inuyo. Koma a shadow akanapereka ndalama. Wakuda zimuvutatu apa
Black Nina [chitseka pakamwa]😂😂😂
Zalowa mosavuta amwene
Black Nina ase.🔥
Ganizani sangajambule zinthunzi nthaw alibe😂😂😂😂
Aganizani mutu unazizizila nda amathu 😂😂😂😂😂
Ati ufuna juice Koma ma guy 😂 mwachenjera darling nso wathera panjira😂😂
😛😛😛😛😛😛😛keep it up
This shop keeper guy eeeeeeeh 🤗🤗🤗🤗🤗
Eeeee wakuda wangalusa uja walisira sistez uku😅😅😅
Akut amuna anu ndiwauza chilichose hahahahaha
Ati Basi ndiza nsapatozo😂🤣
Tikudirila Ina week into sonaturuke
Ukhala nd chisisi cha munthu nd bwino bwanj
Khezen achemwali ako uwapengetsa ayayaya 😂😂
angozo inu ndi one