ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
OkSitinaiwalebe za chilima mwatipezaso tikudikila leport landege ana gwetsa ndani
Amzako anabwera kale ku msonkhano wa UN unali busy kupembedza America km Iran ndikuipempha ipitilize kuphulisa Israel wina azione
Astikali akuyasamula kkkk njala sanadye
Koma ndiye chanenepat kukoma misonkho yamalawi
Zose umakapempha kunjaku koma bwanji supempha akuthandizire kupeza chimene chinanagwesa ndege coz umaziwapokanthu
Tinene kut ndege imeneyi blackbox mulibe?? Nanga cockpit recoder???? God is watching.
His Excellency
Mr President, muzikhala ndi manyazi poyankhula. Chiyambireni kupita ku UNGA chinasinthapo positively ndichani? Only devaluation brought. Dziko lopempha pempha simatukuka, ndichimodzimodzi munthu opemphapempha salemera. Siyani kupemphapempha.
welcome back but i need report now for chilima don't forget please
Zaukape kulani ufit siyani kumaona zokamba kapena zoseweletsa
Guys mwakawona ka police mumene kayasamulila kukamwa kkkkkkk apolisi njala guys iiiiii angoyima chifukwa cha ntchito koma apolisi ali ndi njala kkkkk
Ai zikomo mwabwera kozekani yamanjia nkati timadikila iwe wafawafa
Chakwera my vote
Mutu
Kkkk mapwala wabwelera
Mbuzi yafika
Wabwera gurugunyinda 😏😏😏
Kodi ukati mafuso ndi angati limozi iwe ukuti mafuso radio basi ndi abs atolakhani ama radio ena alikuti zopusa
Mizimu ikudikilani mukumaithawa ija
Very shallow questions
Muzingovutika uyu akanali mpaka 2030 inu mukanali pa opp
Chikangawa wabwela 😂😂😂
Kodi zanjala tizingomvela mwela kumpoto bwanji samadya chitedze ulesi kuzolowela kulandila moyo wopemphetsa mulibe manyazi
Mulila misozi ya mamina fweee uyu akanali
Amaganiza sabweraso takulandila kuchitedze
Asilikali akulepheras kuponda perete bwanji dziko lomvesa chison ngt ili sndinalione
Aponda mwanji ali ndinjala akungoyasamula njala asikali nao akudya chitedze malomwa nyemba
@@JacquereenPereira mavuto adzaoneni
Mulungu alinanu
Anthu ovota 100 inu a pa wapo3 mu maka
Bola chikanafela komweko bwanji
Akukulatu munthuyi
Very unhealthy
Wabwerakodi wamoyo etiiii??????
😂😂😂😂😂
Sitinaiwalebe za chilima mwatipezaso tikudikila leport landege ana gwetsa ndani