Kunavutatu ku Phalombe dance yomwe ena akuthyola kaya zitifikitsa patali izi chifukwa nde ndi ndale

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 5 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 15

  • @EstherZintambira-sq3yy
    @EstherZintambira-sq3yy 4 หลายเดือนก่อน +1

    Koma mauwo mmh. Ndiwe mchewa kossi

  • @PatrickGonagona
    @PatrickGonagona 4 หลายเดือนก่อน +1

    MCP ndi chakwera gule kwawo next year

  • @GenialaChalera
    @GenialaChalera 4 หลายเดือนก่อน +1

    Tv imeneyi ife sitizivera

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 4 หลายเดือนก่อน +1

    Agalu in ndithu zikuonekeran

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 4 หลายเดือนก่อน +2

    Chakwera 2025 kulibe chao

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 4 หลายเดือนก่อน +1

    Anyamata anafooka kwambiri ambuye ntengeni anawafoola mafumu awa zoona kumawasekekelera zoona

  • @samsonmtumbati4855
    @samsonmtumbati4855 4 หลายเดือนก่อน +1

    Amalawi tidzafera muwumphawi mmawombera mmanja zilizonse

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 4 หลายเดือนก่อน

    Malo mokweza aMalawi mukukwesa mavumu asaku vote rani mavumu omweo sachimba

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 4 หลายเดือนก่อน +1

    Mukhala mukusololoka milomo choncho akukudyerani masuku pamutu Iwo nkumanenepa ndi milomo yomwe ndalama zanu zomwe mxxxxxx

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 4 หลายเดือนก่อน

    Nanuso adpp nsanje mnawona atagona ndi njala kambani ina nkhani zisilu inu anthu asayamikile mzafa ngati yudasi chifukwa chansanje

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 4 หลายเดือนก่อน +1

    Za zii koma agona ndi njala makomo mwawo 2000 akagule chanino

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n 4 หลายเดือนก่อน

    Tiona 2025

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr 4 หลายเดือนก่อน +1

    That is politics akulemba mmadzitu iwowa akuona ngati mwera angaigwese!

  • @LukaAron-el5qh
    @LukaAron-el5qh 4 หลายเดือนก่อน +1

    Mazimfumu opanda uzimu amenewo zoona kuvina chifukwa chowakweza udindo pomwe anthu midzi akuvutika ndinjala Koma malawi sindikudziwa kuti akupita kuti

  • @AmandaConstance-fx8cr
    @AmandaConstance-fx8cr 4 หลายเดือนก่อน +1

    Mmmmmmmm koma kumalawi Kaya eeeeeeeee poverty yonse yiiii dancing for poverty