"mtengo wolephela nyani, pusi sangakwele. tsabola wakhale mundiwo sangawawe" that's the real truth with African leaders then don't wanna step down even if they are failing dismally.
ndipo kudzakhala zivomezi zazikulu, ndi njala ndi miliri m'malo akutiakuti, ndipo kudzakhala zoopsa ndi zizindikiro zazikulu zakumwamba. LUKA 21:11 Ndipo pomwepo ambiri adzakhumudwa, nadzaperekana wina ndi mnzake, nadzadana wina ndi mnzake. Ndipo aneneri onama ambiri adzauka, nadzasokeretsa anthu ambiri. Ndipo chifukwa cha kuchuluka kwa kusaweruzika, chikondano cha anthu aunyinji chidzazilala. Koma iye wakulimbika chilimbikire kufikira kuchimaliziro, yemweyo adzapulumuka. Ndipo Uthenga uwu Wabwino wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi, ukhale mboni kwa anthu a mitundu yonse; ndipo pomwepo chidzafika chimaliziro. pakuti pomwepo padzakhala masauko aakulu, monga sipadakhale otero kuyambira chiyambi cha dziko, kufikira tsopano, inde ndipo sipadzakhalanso. Ndipo akadaleka kufupikitsidwa masiku awo, sakadapulumuka munthu aliyense: koma chifukwa cha osankhidwawo masiku awo adzafupikitsidwa. Pomwepo munthu akanena kwa inu, Onani, Khristu ali kuno, kapena uko musamvomereze; chifukwa Akhristu onama adzauka, ndi aneneri onama nadzaonetsa zizindikiro zazikulu ndi zozizwa: kotero kuti akanyenge, ngati nkotheka, osankhidwa omwe. Onani ndakuuziranitu pasadafike. Onani, Iye ali m'chipululu; musamukeko. Onani, ali m'zipinda; musavomereze. Pakuti monga mphezi idzera kum'mawa, nionekera kufikira kumadzulo; kotero kudzakhalanso kufika kwake kwa Mwana wa Munthu . Koma pomwepo, atapita masauko a masiku awo, dzuwa lidzadetsedwa, ndi mwezi sudzaonetsa kuwala kwake, ndi nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba, ndi mphamvu za kumwamba zidzagwedezeka: ndipo pomwepo padzaoneka m'thambo chizindikiro cha Mwana wa Munthu; ndipo mitundu yonse ya padziko lapansi idzadziguguda pachifuwa, nidzapenya Mwana wa Munthu alinkudza pa mitambo ya kumwamba, ndi mphamvu ndi ulemerero waukulu. Ndipo Iye adzatumiza angelo ake ndi kulira kwakukulu kwa lipenga, ndipo iwo adzasonkhanitsa osankhidwa ake kumphepo zinai, kuyambira malekezero a thambo kufikira malekezero ake ena. Thambo ndi dziko lapansi zidzachoka, koma mau anga sadzachoka ai. Koma za tsiku ili ndi nthawi yake saidziwa munthu aliyense, angakhale angelo a Kumwamba, kapena Mwana, koma Atate yekha. Ndipo monga masiku a Nowa, kotero kudzakhala kufika kwake kwa Mwana wa Munthu. Pakuti monga m'masiku aja, chisanafike chigumula, anthu analinkudya ndi kumwa, analikukwatira ndi kukwatiwa, kufikira tsiku limene Nowa analowa m'chingalawa, ndipo iwo sanadziwe kanthu, kufikira kumene chigumula chinadza, chinapululutsa iwo onse, kotero kudzakhala kufika kwake kwa Mwana wa Munthu. MATEYU 24:10-14, 21-24, 26-27, 29-31, 35-39
You inspired me very much through preachings in your muzik.Your muzik is Rich in uthenga.God bless you.
Approved in Zambia 🇿🇲 and we love it
Nthaw imeneyo alidi Phungu Joseph nkasa
"mtengo wolephela nyani, pusi sangakwele. tsabola wakhale mundiwo sangawawe" that's the real truth with African leaders then don't wanna step down even if they are failing dismally.
Great artist, watching from Zambian
He prophecy thru music, i call him a prophet
Yanyuwani mwaimbaija 4:28 mundi itane
Phungu nyimbo zake zimakhala ndi uthenga wabwino pano pa south Africa timamveranso nyimbo zake
Sure
Koma Nkasa ndi khani Zina palibeso 2020 fire
Nice madala nkasa we are proud of u....
Number 1 mkasa he's one of my most favourite artist
Living legend
Good song Joseph
Mkasa the best musician keep it up
Inutu bwana nkasa, ndimataya kantengo really, Dubai,United Arab Emirates
GORIYATI ANAMENYEDWA NDIDAVID
My best friend, my favourite
Aaaaa inu ndi mfumu
How I loved this.
More fire nkasa
Keep it up i like it😊😊😊😍
Thanks 😄
Legend
Mmatha kuimba madala
Koma bwanji sakukaramba Nkasa?mmene ndinamusiyila alimomwemo😹😹don't for get to watch my prank videos..
Madala♥️
Estou a gostar
Super hit
ndipo kudzakhala zivomezi zazikulu, ndi njala ndi miliri m'malo akutiakuti, ndipo kudzakhala zoopsa ndi zizindikiro zazikulu zakumwamba.
LUKA 21:11 Ndipo pomwepo ambiri adzakhumudwa, nadzaperekana wina ndi mnzake, nadzadana wina ndi mnzake. Ndipo aneneri onama ambiri adzauka, nadzasokeretsa anthu ambiri. Ndipo chifukwa cha kuchuluka kwa kusaweruzika, chikondano cha anthu aunyinji chidzazilala. Koma iye wakulimbika chilimbikire kufikira kuchimaliziro, yemweyo adzapulumuka. Ndipo Uthenga uwu Wabwino wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi, ukhale mboni kwa anthu a mitundu yonse; ndipo pomwepo chidzafika chimaliziro. pakuti pomwepo padzakhala masauko aakulu, monga sipadakhale otero kuyambira chiyambi cha dziko, kufikira tsopano, inde ndipo sipadzakhalanso. Ndipo akadaleka kufupikitsidwa masiku awo, sakadapulumuka munthu aliyense: koma chifukwa cha osankhidwawo masiku awo adzafupikitsidwa. Pomwepo munthu akanena kwa inu, Onani, Khristu ali kuno, kapena uko musamvomereze; chifukwa Akhristu onama adzauka, ndi aneneri onama nadzaonetsa zizindikiro zazikulu ndi zozizwa: kotero kuti akanyenge, ngati nkotheka, osankhidwa omwe. Onani ndakuuziranitu pasadafike. Onani, Iye ali m'chipululu; musamukeko. Onani, ali m'zipinda; musavomereze. Pakuti monga mphezi idzera kum'mawa, nionekera kufikira kumadzulo; kotero kudzakhalanso kufika kwake kwa Mwana wa Munthu . Koma pomwepo, atapita masauko a masiku awo, dzuwa lidzadetsedwa, ndi mwezi sudzaonetsa kuwala kwake, ndi nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba, ndi mphamvu za kumwamba zidzagwedezeka: ndipo pomwepo padzaoneka m'thambo chizindikiro cha Mwana wa Munthu; ndipo mitundu yonse ya padziko lapansi idzadziguguda pachifuwa, nidzapenya Mwana wa Munthu alinkudza pa mitambo ya kumwamba, ndi mphamvu ndi ulemerero waukulu. Ndipo Iye adzatumiza angelo ake ndi kulira kwakukulu kwa lipenga, ndipo iwo adzasonkhanitsa osankhidwa ake kumphepo zinai, kuyambira malekezero a thambo kufikira malekezero ake ena. Thambo ndi dziko lapansi zidzachoka, koma mau anga sadzachoka ai. Koma za tsiku ili ndi nthawi yake saidziwa munthu aliyense, angakhale angelo a Kumwamba, kapena Mwana, koma Atate yekha. Ndipo monga masiku a Nowa, kotero kudzakhala kufika kwake kwa Mwana wa Munthu. Pakuti monga m'masiku aja, chisanafike chigumula, anthu analinkudya ndi kumwa, analikukwatira ndi kukwatiwa, kufikira tsiku limene Nowa analowa m'chingalawa, ndipo iwo sanadziwe kanthu, kufikira kumene chigumula chinadza, chinapululutsa iwo onse, kotero kudzakhala kufika kwake kwa Mwana wa Munthu.
MATEYU 24:10-14, 21-24, 26-27, 29-31, 35-39
Nkasa amatha uyuyu ndiwoimba
Komaso kuno tilikuno tikuva Bho. Beg
Bigman himself
Buluku mkasa udzikhala serious koma......nyimbo ili bwino
kkkkkkk mavalidwetu kkk
Kkkk nyimboyi ndiyakale and i think video iyiso ndiyakale angopanga upload pano...nthawi imeneyo anatchena apo
ZOONA VIDEO IYI NDIYAKALE ZIKOMO KWAMBIRI
@@MALAWIMUSICTV old pepper does not taste better that is true 😘
respect