That's true that Chakwera came into power through alliance which means the time alliance ended the same time Chakwera was supposed to step down and it doesn't make sense why Chakwera is still president of the country it's like Malawi has no judges, Malawi has no politicians and Malawi has even no one to lead the country
Palibe munthu angachotse Manganyu komaso asatule pasi udindowo ayi ,Ndipo kwatsala miyezi 9 basi kuti Manganya adzalandire chisamaliro chonse cha Boma kwa moyo wake onse .Ndikuti manganya Asatule pasi Udindo
Manganya anali mthira kuwiri pakati pa UTM ndi MCP, n'chifhkwa UTM convention yamukana. Panopa angozichepetsa kusankha kukhala member wa MCP kapena UTM. Zili Kwa a President kumusiya kapena kumuchotsa pa VP, si MCP ai.
@@MichaelHastingsGodfreyMvula Constitution can be changed in a broad day light. We saw it how 50+1 came about orchestrated by the courts. Same way, if the opposition was well united and brave, Chakwera can be ousted right now...
Choti adziwe a mcp , u president omwe iwo adatenga udali osonkherana,ngati ndi chomcho mcp so isiye udindo ,chifukwa munthu amene adapangitsa kuti mcp ikhale pa mpando adamwalira .nawoso asiye.kodi manganya amudziwa lero kuti ndi mthira kuwiri?manganya apitilize mpaka nthawi yake ithe
aMalawi anadziwa kale zochita zamanganya koma iye amazitenga ngati ndi dolo...mcp imayembekezera kt anyamula chipan cha utm kupitisa ku mcp koma zamlephera chikana mcp ikunena kt safunika kukhala pa u president...yah ndi zoona chifukwa utm inatuluka mgwirizano, 😮😮😮ayisova sunati
Zimene anachita manganya or mwana sakanapanga ,coz iyeyi ndikananakhala ine ndikanavomela kukhala vice president koma ndikanaona zimene chilima amachita kukhala vice koma ndikumagwila ntchito ndi chipani chake,
Manganya limuzunze ndi dyera lake baai chifukwa amaganiza Kuti sazavalanso miloga Ku tikuferanji chifukwa chake Za kumwalila Kwa chilima iye sanalankhule kalikonse
History tells us that Justine Malewezi was sidelined, Cassim Chilumpha was dropped, but maintained gheir positions constitutionally while in their homes till election's result day.
Mcp siyoyifera nde ndi zimenezi sidik mea anapita, SKC anapita lero ndinu a manganya ganizani bwino other wise mudzawona zimene anawina Chilima Mcp ilibe pabwino
Zaboza izi,,manganya si VP wachipani,,ndi VP wadziko osati chipani,,MCP imuuzabwanji kt ature pansi chikhalileni iye analowa pa u VP kaamba Ka malamulo,,,,zaboza izi..
Manganya wataya chingamu Chifukwa cha mtedza olawa😅😅😅
😅😅😅😅😅
😅😅😅😅😅
Onse atule pansi udindo. Boma ili linalowa m'boma chifukwa Tonse alliance which does not exist anymore. MCP is ruling illegally.
That's true that Chakwera came into power through alliance which means the time alliance ended the same time Chakwera was supposed to step down and it doesn't make sense why Chakwera is still president of the country it's like Malawi has no judges, Malawi has no politicians and Malawi has even no one to lead the country
Ichi chakoma ichi chakoma pusi anagwa chagada( this is sweet this is sweet cat fell upside down) yakwiya ndi mizimu. Asova
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 ndipo
😂😂😂 this is sweet this is sweet 😂
Amenewo ndi maganizo anu kapena akuluakulu amene mukunenawo ndi mbuli za malamulo. Sanasankhidwe yekha ndipo Manganya sangakhale kakasi muli kakasi ndinu. Kusapita ku Convention zikusonyeza kuti alibe pressure
MULUNGU tumizani MZIMU OYERA ku dziko la Malawi dziko labvunda, ndikunyozana, kusalemekezana ,kulankhula boza, kudana, miseche, kutukwana, kaduka, ndipo anthu tasiya kupembedza inu dziko lasanduka sodom ndigomola. YEHOVA tithandizeni kudzera mwa YESU KHRISTU kuti atikhululukire mphulupulu zathu nfi tumizani moto wa MZIMU OYERA unyeketse chonse choipa Mzina lanu YESU KHRISTU AMEN.
If Manganya was me,I was just start my own Political Party.
Palibe munthu angachotse Manganyu komaso asatule pasi udindowo ayi ,Ndipo kwatsala miyezi 9 basi kuti Manganya adzalandire chisamaliro chonse cha Boma kwa moyo wake onse .Ndikuti manganya Asatule pasi Udindo
Zaboza izi muzichita manyazi unwinds wa manganya uli mumalamulo akulu aziko lino musanamize anthu .maganizo anga ndikuti ndiwe opusa ukuyankhulawe
Asiyeni chifukwa ana sankhidwa ndi president ngati vice wake wa ziko
A MCP zangowavuta, amaona ngati they will use Usi to get UTM back. Asova. Usi ndi vice president mpaka September 2025. 😂
true
Zoonad mpakana 2025 wooo chifukwa inali agreement
Mukachoka pamenepo mukadyera therere, pogonaso pachiguduli , nkhwawaso kumudzi kwanu , pamene mukumunenayo ndi bwana,
Make sikono akumudikira uku 😂😂 komabe malamulo akumteteza
Manganya.....amadzimva kt ...ndi dolo kumali ... amzake....
Makape muli ndi nthawi yambiri, osamangodya nsima ndikumakasanza bwanji?
Ndi vice president wadzikotu osat wachipani osamasakaniza khani palibe chingachitike pamenepo
Vice president wakewo anachita kukamutola mu msewu KAPENA adamupeza Ku UTM?
@@PrinceThom-pe6ieit doesn't matter...
@@PrinceThom-pe6iendiye zachipani zikugwirizana chani ndi malamulo a constitution yamalawi?
😂😂😂😂 basi abwelele ku tikuferanji
Kkkkkk azikayimba nyimbo mmasewero
Bwato sasisilana pakati pa nyanja anatero Manganya he will defend himself 😂😂😂
@@MonicaSteve-t5p happening only in Malawi.. because of lack of brave people with resources, in other countries zimatheka...
Mukusokoneza ameneo mau a late Dr KSC not manganya
Ndiwe wabodza hule😊
Mcp pomutenga manganya inali plano yoti adusileko 2025 ndicholinga choti mugwilizano nd UTM ukhalepo ndimene zatelemu mugwilizano walepheleka contract yathatso pati amanganya kusaganiza iwowa nali advice yanga kwa manganya apa ayenela kuwauza mwachangu kt nda joina MCP kt mwina atha ku dutsa mkuthamangisidwamu 😅😅😭
Ndizoonadii achoke coz his nt member of any paty, vp amaenela akhale wachipani chinachake. Mcp as killaz angomumpa bas !!
Ukuona ngati ngakhale atachoka pampando adzagona ndi njala ? Osamalimbana ndi munthu amene mulungu anadalitsa , ,
Ndinadziwa cifukwa anadzalankhulapo kumuza cikangawa kuti: acotse nduna zina cifukwa ndizimene zikupangitsa kuti cikangawa azitukwanidwa, nde nduna sizinasangalatsidwe ndi mawuwa ici ndi cimodzi ca zifukwazo.
Mbuzi zonse iye usi ndi MCP, tikuchosa 2025.
Manganya anali mthira kuwiri pakati pa UTM ndi MCP, n'chifhkwa UTM convention yamukana. Panopa angozichepetsa kusankha kukhala member wa MCP kapena UTM. Zili Kwa a President kumusiya kapena kumuchotsa pa VP, si MCP ai.
Constitutionally he is State Vice President and not for any party until Malawians vote in September, 2025.
@@MichaelHastingsGodfreyMvula Malawi is full of uneducated savages like me but it's sad to see well educated people behaving like savages 🤦
Umbuli kuchuluka kumango falitsa uthenga wabodza
@@MichaelHastingsGodfreyMvula Constitution can be changed in a broad day light. We saw it how 50+1 came about orchestrated by the courts. Same way, if the opposition was well united and brave, Chakwera can be ousted right now...
@@gracem-y8p well educated people are the ones taking Malawians to hell..there is ' Sense ' in 'Nosense'.
Tkhulukireni Tate namalenga tikhululukireni YEHOVA tachimwa tachimwa titseguleni maso ndi makuti a MZIMU OYERA AMEN.
Pajatu manganya ndi ombwambwana ndiye idzi sidzodabwitsa abwelele ku tikufelanji
Anawonjeza kunyadiila imfa ya chilima mpaka Amkadziwa ndani kt ndidzakhala president 😂Mnzake atangofa kumene mmmm mzimu wa chilima wamuyendera ALAPE
ndipo inu Mmm
Dyera limuthere anthu amkamuuza kuti chipani Cha MCP sizithu
Zaziiii chibonyo
Nyekhweeee,,,, mwina agwilitsa mwanbi oti bwato satsitsilana pa nyanja 😂😂😂😂😂
Manganya ananenapo kuti anasiya zatikuferanji ndiza wakudya zake alibe mulandu olo za utm? Zokha ananena kuti sapanga nawo ndi zaupresident wa utm basi, ndiye pano ndi kabambe. Iye pano ndi president wa dziko lamalawi osati chipani chirichonse. Muzifunsako zammene amayendera malamulo adziko lino osamango falitsa uthenga wosonyeza umbuli wanu.
Waidziwano MCP bola unakhakhara Ku UTM kokuja kumamenya khondo relo wamutawako
Choti adziwe a mcp , u president omwe iwo adatenga udali osonkherana,ngati ndi chomcho mcp so isiye udindo ,chifukwa munthu amene adapangitsa kuti mcp ikhale pa mpando adamwalira .nawoso asiye.kodi manganya amudziwa lero kuti ndi mthira kuwiri?manganya apitilize mpaka nthawi yake ithe
Vuto la ku mcp kwachuluka mbuli zophunzira,iwo ali busy ndi kusakadza misonkho ya amalawi osati kukoza malawi okomera tonse
Iwe zomwe ukunena sizikuveka ameneyoo ndi voice president WA ziko not chipan
Aidziwe amcp amafuna amugwilitsentchito aziona
Manganya ndi munthu oipa guy's series munthu wabodza samalani a MCP akuphesani nose ngakhale mulizigawenga mulidzigawenga
Manga must pack and go to odya zake alibe mlandu crew
Nkhaniapa ndiyoti manganya mutuwake sugwira,muzimuwona nkhope munthu ngati kamutu nkotaya.komanso ndimfiti ameneyo.mzake kufa iyeyo kuthamangira udindo.ukoko yankho ndiloti akangopha kamanganyako.awiri ozungulira mitu sangayendetse boma.
Angolowa MCP yomweyo mesa zimene amafuna pomupereka chilima
aMalawi anadziwa kale zochita zamanganya koma iye amazitenga ngati ndi dolo...mcp imayembekezera kt anyamula chipan cha utm kupitisa ku mcp koma zamlephera chikana mcp ikunena kt safunika kukhala pa u president...yah ndi zoona chifukwa utm inatuluka mgwirizano, 😮😮😮ayisova sunati
Achoke basi pa u Vice president chifukwa alibe Chipani Ku UTM president ndi Kabambe
Mcp ili mugwirizano ndi wakudyz zake alibe mulanduno kkkkkk😂😂😂😂
Aziwon mesa amaona ngat usi angatengere utm ku mcp Nden aziona
Kabambe ndiamene akuyenera kukhala vp wa ziko chifukwa ndiwa Utm
Zimene anachita manganya or mwana sakanapanga ,coz iyeyi ndikananakhala ine ndikanavomela kukhala vice president koma ndikanaona zimene chilima amachita kukhala vice koma ndikumagwila ntchito ndi chipani chake,
Manganya angopitiriza kupanga masewero ake chifukwa ndale simbali yake
Manganya waziwona anamupusisa lero wapusa nazo wakhaura
Manganya achoke abwerere ku madirama ndiopupuluma
Amuthamangitsako chitsilu chimenecho sikusinja ndi gwenembe
Manganya vice president WA dziko mpaka 2025 wooooo qas per constitution of republic of Malawi.
Yes sakuchoka mpakana 2025 wooo
Manganya limuzunze ndi dyera lake baai chifukwa amaganiza Kuti sazavalanso miloga Ku tikuferanji chifukwa chake Za kumwalila Kwa chilima iye sanalankhule kalikonse
History tells us that Justine Malewezi was sidelined, Cassim Chilumpha was dropped, but maintained gheir positions constitutionally while in their homes till election's result day.
MCP dignatories are very wise to suggest booting out Manganya.He is not eligible to be .......and he is not empathetic either in UTM.
Palibe ali ndi mphamvu yochotsa vp ngati sanaphwanye malamulo
Asova munthu oyipa mtima manganya azípita kumasewelo ndiposo asiye kusokoneza utm muthu oyipa ameneyo
Mmesa about azisiya zaupredudent psno ndi.kabambe. Is kabambe complaining?
Mmmmm musamaname . VP Ali mmalamulo
Komaso a mcp nawoso akuyenera kuchoka chifukwa bomali linali la tonse alliance ndiye pano tonse alliance kulibe tikuyenera kuvotanso
WANENA DZIMENEDZI NDANI.... ??? BODZAA INU......MUKUNENA NDINUYO...MUSASOKONEZE ANTHU.....
Zake izo awona apanga bwanji ife tikulika chilima
Kwasala kuti ampange chikangawa, akapanga makani
Manganya ndi chitsiru, how could he trust mcp?
Mcp siyoyifera nde ndi zimenezi sidik mea anapita, SKC anapita lero ndinu a manganya ganizani bwino other wise mudzawona zimene anawina Chilima Mcp ilibe pabwino
Apa bvuto palibe, vice president amasankhidwa or alibe chipani, so don't be jealous he is the vice president of Malawi
Manganya ndi nfiti,mwina enanu sumudziwA
Achitabwino ndiwausilu amuonesakupusakwake
Anya awona Manganya🤔🤔🤔🤔🤔 amuchita bwino Ku UTM sitikumufuna anatiphera Chilima ameneyo aziwona
Akachokamaganyandikuti map
nayoso yichoke muboma😮
A MCP asamukane,usi chifukwa tu paja anamulumbilitsa,ndiye kumusisa pampando usi akhala ngati ndani, Malawi tiyeni tizimvelana chisoni.
Hahahaha,muthudzuleni iiiya 😢
Zaboza izi,,manganya si VP wachipani,,ndi VP wadziko osati chipani,,MCP imuuzabwanji kt ature pansi chikhalileni iye analowa pa u VP kaamba Ka malamulo,,,,zaboza izi..
That's true 👍
Mbwiyanga manganya lero si izi lero chikangawa akukuthamangitsa km makani iwe
Mwaona tu baba manganya eish ,ichi cakoma ichi cakoma mwaziona
Kodi anasiya yozamayenda maOffice zija??kkkkkkkk anabweratu ndimoto
Anali matama chabe amene ajainu
Kape
Bolani pamenepo wapuzila kenakake kutengeka sikwabwno
Mayi Sikono akumufuna ku tikufelanji. Bwelera ku Tikufelanji Manganya ukayambilenso pamene unasiyila
Angomaliza nthawi yale inu amcp mnalinayo nganga kuti wakhale vice president msamde lero😂
Komatu mfundo zanuzi ndiye sizikumveka kaya mukuti chiyani pamenepa kaya?
Malamulo akumuteteze Usi kukhara Vp mpaka September 2025,,dispite kukhara opanda chipani
Basi amuchose pajatu choipa chimasata mwini apite basi abwelele ku Masewelo atikufelanji
Azanutu amaposita nkhan ndiumbon wake iwe umbon ulikut ?
Wakula watha azoona kti atani 😂😂
Eeeee komatu manganya ndi vice president basi or mutamuchosa zake dzilibwino kale analumbila kale
Kkkkk odya zake alibe mulandu apite kuchipani chakecho,
Kodi mmene amkadankha manganya samkadziwa kuti akusankha vp wadziko?mcp yayambapo kkkkkk amuyedzekatu akapanda kusamala
Ameneyo ndi munthu opanda makhalidwe abwino chifukwa anaonetsa mtima okonda ndalama, ku Utm kulibe chake
sizingatheke chifukwa ndi Vice president wa dziko osati ku chipani
Pamenepo
Good 👍
Achita bwino akulu akulu a MCP kuti apume manganya
Usi kusamva abweleleso ku madram azikavina ndi amake asiko
Amupusitsatu imeneyo ndi MCP
Azipita kumadrama kwakeko
Usi ndi dolo simungamuthe UTM ithera moyenda bola usi dpp makatani eniyeni dikilani muone zomwe akupangeni shoti usi mumva madzi sakuchoka muboma
Zoonadi ndaona convoy yake achepetsa magalimoto achitetezo ake
TILIBE NTHAWI YOPANGA ZA AMENEYO TILI BUSY NDI NKHANI YA MACHINE OBELA MA VOTE
Manganya asova Ku UTM kulibe chawo
IFE TINADZIWA KUTI IZI ZICHITIKA MCP IMAMUGEIRITSA NTCHITO MUNTHU NKUMUSIYA AZIONA
Awona Kuti apangabwanji manganya zamubwelera zimene amachita iyeyo akapange ubale ndi chikangawa😂
Umbuli ndi matendadi u vice President sugathe mpaka nthawi ya. Chisankho 2025 muonaso .
Komanso pamene amamusankha samaganizako chakwerayo penaso kumaganizat
Agalu Inu a chikangawa manganya ndi vice president wadziko not wachipani cha mcp
Ineyo si wandale koma umbuli ndi tchimo pawokha aaaaaa manganya ndi vice president wa dziko, dikirani 2025 September tizavote