ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Uyuyu ma speach ache ngosonyezeratu zoti UTM adayituluka
Aaaaa mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pokuyikani nose wokhudxiwa pa ifa ya chilima
Zopanda ndi mchere omwe . Kodi iweyo ukupanga za chakwera ndi MCP? UTM inatulukatu mu Tonse nde ukukambazo is totally irrelevant
😅😅😅😅😅
Ndere zokhazokha.
Chikangawa 2
Nthiko uwo.
Palibe cha nzeru chomwe anganene manganya koditu akhaulatu ameneyu ku convention sakawina alira ngati gape ndithu
Kodi uyu Ali Mbali iti..odya zake alibe mlandu kapena chikangawa party?
Mauwa ndi opereka mtendere ndithu kudziko bola iyeso awonetsere kt ndi wa utm osati zomathawa thawazi
Weyo opusa siunapite kupita kukawona pamene panefela Chilima chikangawa
Manganya DPP Peter muthalika wa kuphudzitsa ulemu kupeleka kwa malemu Saulosi Chilima mbuyo mosemu nsongano umene umapangisa unavailable wawuza gulu kt akhare chete kwa second kwa 30 second iwe
Zaziiiiii
Koma manganya yeee kodi iweyo uzingolakhula za ndalama bwanji osapanga kampeni yoti utm ilowe mboma bwanji
Osamanvera uyu simunthu nsiyeni akuwona ngati awina ng'oooooooo angotaya nthawi
Wakupha iwe. Ndizimene umafuna
Uyu ndikape basi ....ussi kwasala pangono kufa
Palive point ndavapi apo
Kodi ulemu wa skc muonela Kwa peter kale unapangapo iwe yako mcp
Azoona usi amakwana
Koma abale musakoneze anthu
Panyooooooopoooooooo
Zaziii