Ngati zipani izi zapanga mugwirizano ndi MCP it means all political parties are corrupt, don't trust them at all, mmene zinthu zilili ku malawi lero kamba ka chakwera ndi MCP munthu wazeru sangalowe ku MCP
Dpp my vote under the leadership of Apm osati chisilu chomwe tili nacho ....chakwera waononga ziko .....taonani mmene kwacha ikugwela pafupifupi tsiku ndi tsiku
Km asamaiwale kt msomba ikangoola imodzi bas zonse zimaola or atatenga zipani zonse muno Malawi km chongonva kt muli MCP palibe angavotele 💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙 my vote
Muluzi is not cruel but he knows that for the president to deliver he she needs to be running the government for the period of ten years that's what we Malawians approved in our pariament so let surpot him for the next five years that's when we can judge him as a fealier or not
Aaaah komaso awa HE Dr Joyce Banda munthu ndi former president nde azakhala senior minister koma anthu mwabalalika eti phikani nkhani yina iyi ndibwelela
Apite basi kuli chikangawa kumeneko akakumana nacho go no problem APM my vote ❤❤❤❤❤
All singapitilile pa DPP even dpp itayima pankhomo itha kuwona ngati angachose machine awowo dpp 2025 kuti bhuuu♨️♨️
Chakwera my vote
Kod UDF ife anthu akumachinga tinayitulukatu, kutero yapita yokha no supporters.
😂😂😂
Zoonadi apita okhadi
Munachita bwino
❤❤❤
Poti mwati aku machinga osati dziko la malawi
APM my vote
UTM,AFORD,DPP AND LEF MUSACHITE MANTHA ANTHU AMACHINGA SANGATEDWE KOTI AKADYEKO CHITEDZE AGANIZA MOZAMA.KULI KONSE KOMWE KULI OGANIZA SANGANKEKO KUMENE AKUWAKANKHIRAKO.IF DONE IN THAT WAY,CAN BE RATED MBUZI.
Let them make an alliance, ndipo tiwanyenyanyenya limodzi, we don't need MCP anymore
Aaah za ziii..chipani cha ndiwolotse nkakudyere pa tsidya cho...pitani muzaziona..azakutayani paliponse aChikangawa party wa..za ziiiii
Mmmm a muluzi apanga chani 😯😯😯😯😯 mzawo chilima zinamuthera bwanji kapena sakuziwa.
Koma naangati zili zoonadi a UDF mwazionongera mbiri komanso ma voti simungapeze alliance ya MCP yopepela kwambiri
Ah inu zamabodza zanuzo pangani koma keep Dr Joyce Banda out of it and leave PP alone mxiii
Ndipo leave HE Dr Joyce Banda ,zabodza zimenezo Ife sitili pa ubale wina uliwose ndi MCP, learn kumanena chulungamo
Zaziii dpp my vote ❤ sitikusamala aziwgilizana ndi chilimaso akagqilizana mwatendele , osaila zimayamba chocho ndeazizatililila Ife pasongolopa stop please
Vote APM ❤❤❤
APM my vote ❤❤❤❤❤❤❤forever
Ngati zipani izi zapanga mugwirizano ndi MCP it means all political parties are corrupt, don't trust them at all, mmene zinthu zilili ku malawi lero kamba ka chakwera ndi MCP munthu wazeru sangalowe ku MCP
Kwanukotu
Dpp my vote under the leadership of Apm osati chisilu chomwe tili nacho ....chakwera waononga ziko .....taonani mmene kwacha ikugwela pafupifupi tsiku ndi tsiku
Dpp, Aford ndi utm 💯spark💥💥2025
Zabodza zimenezo a Bakiri muluzi sangamulore Atupere kupanga phada ameneyo
Alliance yofoka ya anyamat ah MCP mupusitsa anthu aah mmidzi yakwanu to 🤣🤣🤣
Let them be akaluza that's the end of their political career
If this is true then MCP ikutuluka boma becoz UDF and PP alibe anthu owatsatila kkkk Dpp ilowa opatsutsana naye
Hahaha bt politicians are very crazy,I can't even understand kuti masowa akumatsekeka ndichani.Ort let's wait and see
Aaa awa mabodza mene adaphela chilima pali munthu zadzelu angapiteyso ku mcp aaaa mwanyanayo a MCP
Kulankhula pang'ono koma action Tiyeni tikalembese kuti tizasankhe Atsogoleri omwe tikuwafuna
Dpp boma ❤❤❤❤
Mumafalitsa mkhani yaboza bwanji 😂😂😂
Km asamaiwale kt msomba ikangoola imodzi bas zonse zimaola or atatenga zipani zonse muno Malawi km chongonva kt muli MCP palibe angavotele 💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙 my vote
Exactly
APM my vote zinazi zitichedwetsa
mmmm ok zomvetsa chisoni kwambiri 😢
Adad my vote
That's good move, all the best
Bzija ayankhula Greece ching a bzaoneka poyela
Aaa zinazi atakumalizeni uyo mm koma mukakhara ndi maso awuzimu abale
Ngati zili choti no doubts MCP .pp.udf.azawinaso
Atupele, nankhumwa, joice apite okha amenewa ifeee amalawi tooonse ambiri sitingate ku chikangawa ku mcp aiiiiiiiii shaaaa koma iweyo bakili nankhumwa ndinu agalu eti PITANI NOKHA IFEEE TOOONSE AIIIIIIIII
Paja musaware kuti Grace chinga ananena JB joice banda za chipani cha mwazi😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Zaboza izi Kodi bwanji anthu mukasowa zochita basi... PP sikupanga alliance with any party... Piiiiiii fuel ngabwingambwi
Muluzi is not cruel but he knows that for the president to deliver he she needs to be running the government for the period of ten years that's what we Malawians approved in our pariament so let surpot him for the next five years that's when we can judge him as a fealier or not
Bingu deliveres in his first term once, are you aware of that.??
Yofooka ndi ya DPP
Well done ❤❤❤
Udf president osati masapota masapota ndi adpp ndi utm atupele mukathela konko ku mcp
Exerctly ❤
AFFORD kulibe masapota ake sangakwane 10
Tnanena kale kuti udf idadya ndalama
Kkkk koma avale UDF nde ndiyadyelatu mmm chonchobe koma Atupele uzalira naweso atakakuponya ku chikanga uona
Udf ndinu osemesa hahahahahahahahahahajajajajkodi atupele ndi mene muli mutumo siuzalamulako Malawi I bet u
Aaaah komaso awa HE Dr Joyce Banda munthu ndi former president nde azakhala senior minister koma anthu mwabalalika eti phikani nkhani yina iyi ndibwelela
Zakale izi maybe last year
Zaboza izi ine ndivela Kwa ntanyiwa osati zamisalazi zikambidwazi
APM 2025 boma osati nchewa okuphayo
Muluzi is clueless, very clueless, thats how he will lose his legacy as the champion of democracy, ndakwiya
Utm dpp afford my vote❤❤❤❤
A chair nanuso mumkatiuza zoipa zambiri za mcp lero mukukhatsera dovu aaaaaa zachisoni ife sitingabetse vote yathu kuvotela chikangawa
Atupele ollo anthu akumachinga anamutaya kale kale
Bodza linali lofunika maprophet kkkkk sizingachitike iziii
Zipani zadyera . Sakufuna kuthandiza anthu Koma kulemeletsa mabanja awo . Chauta simunthu mukwapulidwa nonse
Ngati atero ikhala team yabwino cz enawasangamake UTM ndiyogawana pamene Aford ndiya anthu ochepa choncho mgwirizanowa mcp,udf, pdp, pp ndiena uthakukhala wamphamvu
Bakili akuziwa wathakale nchifukwa wanyengedwa ndi joice banda
Noted but Mtanyiwa, Bakili Muluzi and The DC say the truth not you sir you seem to have less data with doubts
Osamafanizila kombola ndi bomba..Mama JB ndi katundu
Inu ndiwopoyila akanakhala Bomba sibwezi ataluza
Kkkkkkkkk koma anthu Kunama Dpp inakhawulitsa
Komatu masapota sangapite kumeneko iyaaaaaaa agalu awa
Iwe umantha daily usamale ikupanga chibwana UDF ichosemo
Tinkadsiwa ife bakili muluzi ndi mwana wawo afiti tere shanil muluzi uja anamugulitsa kupangila kt anthu asayikokekoke nkhani yakuchikangawa
Akunama inu UDF singapange ize
Komanso udf,pp pano sizipani zoopsya ngati zinayamba zapeza ma voti abwino chiyambileni kuvota mmalawi muno
Wabodza iwe Joyce Banda sangakhale nduna PP ikuima payokha
Akulota
Ndipo zowona zake
Nkhani zopeka izi koma anthu ena mulipachintchito cholankhula boza koma phindu lanu lilipati
Atupele wayiwala za ng'ona kodi
Udf tilibe nayo ntchito inatha kale koma mulungu akuona mavuto amalawi mmene akuvutikila
Zabodza izi sindikuzikhulupilila mkutheka dzakalekale
Chimwendo Mesa chifukwa ukuba kwambiri mimbayako galu
Kkkkkkk bola zokha 😂
Where is Manganya now😮😮
Amalawi tiyeni tithese asogoleli ozikonda ndi adyela monga amene apanga mugwilizano waku mcp
Anthu awa akupasidwa ndalama kuti ayipisa UDF
Aaah ofunikira enawo apemphere kwambiri
Peter adanena kale sangawine..... Olo munthu atamwa ambuye tengeni sitingavotele aluzabe
Zosatheka kuwina mcp komaso kupanda nzeru kothani munthu oti amapita kuchimbuzi akavotele mcp
😂😂😂😂😂 sazawinabe atupeleyonso azamupha
Adzachita manyazi ataluza poyela
Apm ikuwina opanda opikisananawo
Asakupusisen uyu ,UDF sangapange ubare ndi mcp
N̈ext it will be lake Malawi not Chikangawa for Atupele
Tadzigulitsani nkhani zenizeni zomveka bwino kwa anthu osakhala bodza
Izo ndiye zoona bg agluwa
Koma bdaseka,MCP anthu angaivotere chifukwa choti apanga ngwirizano ndi udf,pp,odp?mukunama zimenezi sizingapangise kuti MCP kuti ingawina mukunama,zapanga zipani zimenezi ndizomwe zipangise kuti anthu insewa ade kukhosi kooya,
Amenewo ndi maganizo ammutu mwanu
Kwatsala a Usi nawo ali mnjila akupita konko
Mwana wa a mululzi abambo Ake Amati MCP ili ndi magaz mmanja nanga Ichi ndi chan
Tidikila official announcement from UDF and PDP itself not this fake stories
Anyatu nawo a UDF komaso akondwani Mesa amaziona ndalama akwera kwachakwera agalu anthu
Zovesa chisoni ndithu pomwe dziko Lili Pano basi munthu wazeru kumapanga mungwirizano ndi MCP Kumalawi mavuto sazatha sure mwanguchulusa dyera kufuna Kuti muzikapakura Koma mulungu atimenyera nkhondo Bora pasazakhare smart Matic basi adadi azangodusa mopanda vuto lililose
Mcp my vote
Mcp Ikuzawina 2025 boma🎉🎉🎉🎉
Atupere anangokula chimutu opanda mzeru
Ndipo sikuteketseka sangawine
Ife ndi ana adadi bas
😂😂 maloto achumba
Komatu mukusowa zochita leave Mama JB alone
Mcp boma 2025 woooo
Zabodza manyaxi mulibe polengezapo